Chiukepo Msowoya wins big at Super League awards

Advertisement
Chiukepo Msowoya

Big Bullets forward Chiukepo Msowoya won the Malawi Super League player of the season award and was also the joint top goal scorer along side Innocent Bokosi of Red Lions with 14 goals a peace.

Chiukepo Msowoya
Msowoya: Smiled all the way home.

Msowoya, who pocketed K425 000 in prize money, was recognised for his role in helping the peoples team to defend their Super League in record-breaking fashion in 2015 season. In the player of the season category, he overcame Yamikani Fodya who was favorite to claim the award.

The former Escom United and Orlando Pirates forward revived back his career following a disappointing season at Pirates and Platinum Stars in South Africa.

In other categories, Fodya was voted best defender of the season whilst Stainley Sanudi of Mighty Wanderers was voted the most improved player of the season.

Blue Eagles shot-stopper John Soko was voted the best goalkeeper of the season with Civo Service United midfielder Nelson Kangunje being voted as the best midfielder of the season. Overall, league champions Bullets dominated the awards.

Full list of winners:

Super League player of the season (K300 000): Chiukepo Msowoya

Best Defender of the season (K100 000): Yamikani Fodya.

Most Improved player of the season (K100 000): Stainley Sanudi.

Best Goalkeeper of the season (K100 000): John Soko

Best Midfielder of the season (K100 000): Nelson Kangunje

Top Goal Scorers award (K125 000 each): Innocent Bokosi and Chiukepo Msowoya.

Best Technical Panel of the season (K100 000): Blue Eagles.

Best Managed team of the season (K100 000): Big Bullets

Fair Play teams of the season

1. Civo Service United

2. Azam Tigers 3. Fisd Wizards

Most Improved teams

1. Mafco FC 2. Mighty Wanderers FC

Most disciplined supporters

Big Bullets FC

At the awards, longest serving players in the top flight were honored by sponsors.

James Chilapondwa, Jacob Ngwira, Rodrick Douglas, Mapopa Kaunda, Mabvuto Khozombwa, Gerald Mkungula, Josephy Kachule, Charles Ngosi and Lameck Thindwa are some of the longest serving players to have been honored.

At the end of the ceremony, Bullets were handed the trophy plus a dummy cheque worthy K15 million.

The Blantyre based giants won the league with 66 points, becoming the first team to win the title with such margin.

Advertisement

279 Comments

 1. The organisers saw that Chiukepo was the best & acording to their criteria, he deserved to be the best. What is your problem Malawwi24? Kusowa zolemba? Haa? Ngati muli ndi ndalama organize ur own Award giving function & give ma Award kwa olepherawo! Musatisokosele apa. Boma litivutitse inunso mutisokotselenso apa! Mxiew!

 2. eti ka malawi 24 kusowa chochita! tianthu take topanda nzeru,kd palibe mutu wina oti anthu nkupanga discuss apart from this silly one? inu mumafuna awine agogo anu? kupusa eti,ndasiya kuwerenga ka page kanuka

 3. Mwachidziwikire walemba nkhaniyi wadana nazo koma ndikukhulupira kuti asanasankhe player of the season amaunikira Kaye. Tisadane ndi opanga sponsor league ai fwa akasiya makampani tikuwaganizirawa simudzawaona akupanga sponsor. Azilephera kuthandiza matimu kulibwanji league? Tidziganiza akulu akulu tisanaposite nkhani poyera ngati apa

 4. Amalawi 24 tell dem dat,asiye kudana ndimatimu a army komanso ma refu asiye kukondela matimu omwe zitavuta maka sangafike mu top 5.asiyenso kudana ndi ma player omwe amasewera timu za army,ku army kuli ma playerz ambiri omwenso atha kupita ku timu ya dziko lino eg mwambene.koma kantima ka nkhwidzi basi,kupondeleza luso la ana anzanu makape inu.ngat apitilize kutero kuluza mkosayamba.atnm alibwino hevy

 5. MMMMM! ZINALI BWINO BASI COZ OR TINENE KUTI KOMA FODYA ASANKHA KALE KOMA TIPEMBE ATNM KUTI AWONJEZERE NDALAMA BASI NDALAMA NDIYOCHEPA KULIGI

 6. Ine ; ndikuona kut bola akanasankha iweyo #admin,coz ndwe wansanje koopsa mu season iliyonse….whether; politics,sports,entertainment…u r alwayz against some1-yet that1 he/she is far above from you. #mutu_oolawo.

 7. hahahaha iweyo you are against Chiukepoz being nominated player of the season I guess, you don’t know what football is all about…..tamangolembani zandale basi

 8. Ndinaona maplayer eti zoona guys kulephera ka suit ka 17 pin ka china komweka koma kuvala ngati wapachiwaya #Kangunje ndi nzeke uja sanavele mwamwambo muzitengera zisanzo anzathu abullets aja munaona player wawo fodya uja mmene anavalira komanso chiukepo?nafenso amatimu ena titengerepo phunziro

 9. Ngakhale mtola nkhani safunsidwa mafunso koma ine ndikufunsa; mafunso nawa: iweyo maganizo ako ndiotani? Komanso iweyo umafuna kuti asankhe ndani kupatula Chiwukepo ndipo chifukwa chani?

 10. ife tikufuna a FAM athetse contract ndi TNM ndipo league ikhal yama sponsors ambiri kut ndalama zichuluke. Tikachotsela ma expenses pa 28 games home & away timu yotenga chikho imapezapo ndalama zingati? pabwele partnership yama sponsors osati a TNM kutipatsa closed contract kut palibeso wina opanga sponsor super league, ma company ambiri amaifuna league yi koma vuto ndi contract plus ma conditions anapeleka a TNM.

  1. Ndikugwirizana Nanu! Zoona Zokhazokha, Mgwirizano Wawowo Uthesedwe Basi. But I Smell Kachinyengo Kena Pamgwirizanowo.

  2. maganizo abho komano ma company munenawo anali kt mmene super league imkasowa sponsor?fam agreed to that contract because of the situation they were under

 11. Samayeneradi coz si player woti ndi best player mu season ya 2015 chifukwa sanakhalepo man of the match ngati wachitira Yamikani Fodya mukuwona kwanga amayenera kupikitsana kwambiri ndi maplayer atatu awa 1.Stanely Sanudi 2.John Christopher Banda 3.Yamikani Fodya awa ndiakatundu womanga ndi mawaya womwe atumikira mwapamwamba mu season imeneyi

  1. akulu inu Nsanje kapena msanje??? ngati mukutanthawuza msanje ndi simukuyidziwa dala tnm ndi imene ikuwononga mpila ndalama ndiyochepa panopa ngati team imodzi ikuthandizidwa 103 million season imodzi nde chikho azitenga ndalama yake yonyenyekai???

 12. Ndi achikulire ameneo sanalakwitseso pamenepa. Enao azilimbilana kukhara nomber 4 komweko km kwabwinoku ndi kwa matate ,amdzakazi ,ammikhatheya, madolo, maigwe, km NBB ndi dilu

 13. Nanu amalawi24 zinazi musamakambe zikumapepusa news zanu ayi sikhani yoti anthu ayikepo manganizo awo tabanganizani timakhala pano kamba kainu kma sizi ayi

 14. Nanu amalawi24 zinazi musamakambe zikumapepusa news zanu ayi sikhani yoti anthu ayikepo manganizo awo tabanganizani timakhala pano kamba kainu kma sizi ayi

 15. zidakhala bwino ku blets zimenezi mwina akhoza uphunzilako chikhalidwe ngati cha zawo anyelele amene amabvoleza zinthu zikalakwika,adziwe kuti awandimasewela oyambitsa ubale osati nkhondo mmasewela ampila ayi! zidalabwino kwambili a tnm apitilize mwina kuno kwathu ku malawi tidziwe kukankha chikopa, good pa good a tnm,

 16. ine ndikuti super l inanyenda bwino koma angani zire mpuleyer kunkhani ya ndalama kuti pakutha kwa l player azingulako kathu kooneka kuti akamanena kuti ine ndikusewera mpira musuper l nya malawi aziroza koma pano season yathuthu koma osa ngulako ngalimoto koma conseco mpuleyer wathamanga nthawi yayitalipa ground efe ogonera ndi amene tikungula nglimo sorry malawi.

 17. Ndingothokoza a TNM chifukwa ndamene mukulimbikitsa kupititsa mtsogolo masewero amiyendo mdziko la Malawi,pitilizani kupangitsa maligi ambiri kuti masewelowa apite patsogolo

  1. yemweyo madala,yemweyo mnyamata?kkkkk nde ndioopsya bwanji chiukepo kuposa step up transformers ku kapichira power house kkkkkkkkkkkkkkkkkkkkkk km abale hahahhahahahhahahahahhahahahahahahahaha

  2. Ujk..doloyu..amasakaniza chikopa booh..alibe limit..sasekelera ma golo boyi..nah nkhani yogwedeza ukonde..aliponso wina

 18. Palibe chulungam chifukwa zikhozos zapita ku BBkokha zochepa zokha matimuena awili kapena chifukwa yanyamula ligi koma aaaaakunena chulungamo chukepo yamikan and fisher naga ku BB AMENYA BWINO BASI OSATI ZISELEKWETE ZINAZO

 19. Nokha mukuziwa kuti padalibe chilungamo mkana mwatifunsa kuti mutipale mkamwa???Mundifunsireko award ya mbaleyu idayenda bwanji??Apo bii ndimasha waku state House andiuze bwino,mbale ali pansiyu.

 20. Keep Quite If U Want Perekan Photo Kwa Anthu Omwe Amakonda Kupereka Comment Mwachangu U Always Like Controvesis Why U Think Zimatisangalatsa We Hve Alot To Do Try Bring This Which Can Make This Country Move Ndale Kapena Usawiii

 21. Panalibe Kuchtra Mwina Kma Chiukepo Yemweyo Tangoganiza Mu Super Lig Dzna Ndlake Ku National Team Chiukepo Yemweyi Akukwana Mwanayu!

 22. Ndkudziwa kuti ambiri mwalankhula apanu nd a team ija ya anthu olongolola kwambiri mukawina dzko lonse kusowa mtendere, kma ndkuuzeni musakomedwe nd ka sponsor kanu ka ndudu za fodya kaja ayi ndipo sitikutekeseka nazo zmenezo tikumana kutsogoloku.

  1. mmmmmmh nthawi ijayonso mumatero inu!! Koma kupita pa Ground kumachita kumenyedwa ndi Mzun mpakana 3 kwa chilowere!! Asakuziwani inu ndi ndani wanu ndiwapakamwa basi

  2. Kutsogolo kwake kuti?Tinakumenyani 1st round mumkati chani?Tionana sec round,Tinakupunthani sec round.Pano mukuti kutsogoloku,Tolani maplayer amayinawo ife sitisamala tidzakugagadani maina alimom’mo kuti mudzavomereze kuti ndi team yafuko.Next season BB ndi more fire.Forwardever backwardnever.

  3. Inu amalawi24 chomwe mungadziwe anthu omwe amapatsidwa ma awards including Chiukepo amasankhidwa kudzera m’mavoti,Sikuti anachita kungoloza,Komanso mulungu simunthu now chala chikaloza munthu mndaninso kuti akadane nazo,Tiphunzire kufunira anzathu zabwino pamene achita bwino,Tsankho,Nsanje ndi Kaduka izi ndizomwe zikulepheretsa dziko lathu kupita patsogolo.

  4. Plz Malawi24 phunzira kulemekeza komanso kuyamikira pazomwe ena achita coz munkhani zina zomwe mumatumiza zimakhala zongofuna kudzetsa mpungwepungwe komanso zoti zilibe umboni.Gwilani ntchito mwaukadaulo osati zomwe mukuchitazi.U will never prosper

  5. Mbuzi yamano kunsi ukufuniranjinso umboni wina team ya Bullets Pa Malawi palibe size ka team kakoko kanali no ??? Pomwe MA KING OF SOCCER kukhala pa top kumatsatidwa ndi timu yoperewera mapoint 16 inuyo nkukhala pa yanambala two shame on you

 23. amwene! dzinalibwino kwambiri,kapena munkafunakuti award ya chiukepoyo ampase watimu ijayi????kkkk inu a Malawi24 mwaganidza bwanji poyankhula maganidzo amenewa??tudziwa sidzinakusangalaseni,komabe ng’ooooooooo!! mwagwanayotu.

 24. As a Bullets Fan Yamikani Fodya deserved to be player of the season and most improved team was Mafco ndiye poti anasankha iwowo awoooo zikhale choncho ndikusafunira zabwino ena

 25. Congrats chiukepo ngakhale amakunena kuti ndiwe was mankhwala its all hard work you deserve all the accolades

 26. malaulo!! malaulo!! kkkkk do’t talk to much about silver azanu tinatenga motsogozana 4times ndie kawili kokha mutilowe mmimba paja ndinu mavenda paja venda akaona ndalama phuma eeishp!

 27. malaulo!! malaulo!! kkkkk do’t talk to much about silver azanu tinatenga motsogozana 4times ndie kawili kokha mutilowe mmimba paja ndinu mavenda paja venda akaona ndalama phuma eeishp!

 28. Akanakhal chiukepo yokha poti ali ndi advantage kuti timu yake yatenga chikho,zimatelo kwinako nde poti chizungu ndi top goal scorer zikhale choncho koma kwa ine player of the year ndikanasankha Fodya wamenya mpira wa pamwamba kuposa wina aliyense(silver fan)

 29. We are poor guys.I agree today.Player of the year pockecting K300 000.Eeeeeish but Mr President is buying a toilet seat of K 16 000000.

  1. kkkkkkkk Shutup toilet 16million Aaaaaaaaa!!! its bigmantu kkkkkk Afunazathu zikazaza tizikathandizikila koko ndichachikulutu kkkkk taganiza 16m iiiiii!!!kkkkkkk.

 30. #Geof anzathu aja amawerengera kuti wapereka ma ‘assist’ ambiri ndi ndan. For eg Mu EPL Ozil ndi Walcot akhoza kumaliza league ose ali matop goalscorer ndi zigoli 20. Nde amaona kuti paawiriwo adathandiza anzake popereka pasi yoti mzake adachinya ndindan. Apereka kwa ameneyo.ife kuno tilibe ma video statistics a zigoli zonse za redlions/ BB.

 31. Correct me: How come one season to have 2 goal scorers? On 2010 world cup there were more than 3 players all of them they scored 5 goals but only Thomas muller awarded, so may be in malawi we have our owner football laws apart frm FIFA laws?

  1. Though Malawi hardly enough equipment like camera’s and so on but the best way to choose one between this two is to count fr how many times he has been atop goal scorer,how many brilliant goes being scoredtp than making 2 number 1 its not fair

Comments are closed.