Malawi still welcoming Mozambican refugees

Advertisement
Mozambique refugees

Malawi continues to offer refuge to stranded Mozambican nationals who are fleeing conflict in their country.

The Mozambicans are staying at the newly established Kapise ll camp in Mwanza district as fighting has intensified in their country’s Tete Province.

The current trickling in of refugees follows another pour in of more than 700 people into Malawi in July after RENAMO fighters had carried out two attacks in Tete province, and refugees say they continue to flee atrocities and killings by militias.

However, Kapise II is already home to more than 2,500 refugees and the current situation will likely worsen living conditions at the camp.

Mozambique refugees
Mozambican find a second home n Malawi.

According to media reports, the refugees are facing difficult weather conditions due to lack of shelter and they need food, water, sanitation, and social support.

Some of that social support will have to be provided by villagers who live near the camp but they are worried about the refugee influx.

“We are staying with these people in the village, yes, but we are living in fear because we believe that in time they will completely run out of food, they will start stealing from us in our homes,” says William Mitiwe, the headman at Kapise ll village.

The villagers also fear some of the refugees might have run with weapons that can be used against them.

Mozambican authorities reportedly said those fleeing into Malawi are either thugs or lazy people. But refugee Jaleo Bernaldo denies this.

“They cannot say we are lazy people who are leaving Mozambique for free things at a refugee camp in Malawi. Here at the camp there are all sorts of people, including children, adults and the aged,” says Bernaldo. “Do they mean they are the ones who have been feeding us all this time?”

Malawi government authorities say they are trying to work with their Mozambican counterparts on how best to address the issue.

Meanwhile, international bodies are helping out. Doctors Without Borders is providing medical help.

The United Nations has provided some tents and has established a children’s counselling centre, where children also sing songs to help relieve them of trauma due to running away from home.

Malawi previously hosted Mozambicans who fled a 16-year civil war between 1977 and 1992. The current conflict between government soldiers and opposition RENAMO forces followed a disputed election early last year.

Advertisement

205 Comments

  1. Iwe Mozambique usayesedala kudzandiyandikira !! kungokugwira while here in Malawi eeeeeeeesh ndikugwira ukapolo uja waaaanyooooo!! ndipo ulakalakanso kuthawiranso kwanu komweko phwanga!!!!!! wandizuza mokwana!!!!

  2. They abuse us wen we go to there country en they dnt show respect so does it mean kut ife ndi asamaliya a chiufundo tu hell wth yu

  3. koma guys amalawi ndi chani?kupusa kapena chifundo?anthu oipa awa,,samationa ngati anthu amaiwala kuti akayamba kumenya first option kothawira ndi kwathu,,guys tikamakumana nao tiziwasecha nafenso,,asatizolowere

  4. Kod nkhondo idakali maona ngt zakale2 mh tawalandila amenewa koma njala kuno acibale akufa ndinjala kundende uko nde kay awa tiadyexa cani kay

  5. Ndipo ine kuti ndingopeza mwa m’modzi wa moxo m’dziko lathulo ndingamuonetse zeno,anthu ameneaja nthawi iliyonse ndikamabwela komaso kupita kutheba amativutitsa kwambiri,panopa kuteleku ndikamadzabwela adzandivutitsa

  6. Lets welcome them although there r clazy people, to much kutibela m’ma border mwao tikamadusa. Ndiye ukhonze pansi pa mtengo umva wakonzela president m’mutu anyway tiyeni tiwalandile we r one image from one God.

  7. Boma lawo likuti anthu omwe akulowa muno ndi zigawenga kapena anthu aulesi chabe. This just shows that there stupid government ain’t appreciating what we are doing for their people. Bwanji tiwagogomese azivaya?

  8. I have been with these mozambicans for a while but all they know are bad manners and ill treating malawians since malawi is peaciful nation let them hide and provide all that requires never do tit for tat so that if they have senses they should learn something from us malawians but dont let them behave like animals here in malawi they should learn how to respect human diginity with positive mind as we do if they will fail to live in hamony with the locals they will be unwelcomed too actually too much liniency sometimes is not good all they have to do is to coply with our rules and respect them………!!

  9. Although we know Mozambicans to be bad people in general, let’s still help them for the sake of ‘loving thy neighbor as you love thy self’. Just remind them that we do burn thieves here.

  10. Guys anthu amene amativuta mdziko mwao siamene akuthawa nkhondo lerowa akanakhala asilikali ndikanati asapatsidwe gawo kma amene tikuwatsungawa zimenezo sidzikuwakhudza, tionepo bwno pamenepa

  11. Alandilidwe koma azimai samalani…sizoti akamazapita kwawo azakhale atasiya tiana mbwembwembwe kuno ai..ndikuwadziwa anthu awa pobeleka chitute weniweni

  12. Malawi ndidziko la mtendele ndipo la chifundo koma maiko enawa akuzuza anthu ochokela Ku malawi kodi iweyo malawi umatengambo mbaliyanji pa anthu ako omwe akuzuzudwa kumaiko RNA?

  13. Anthu amenewa kwawo alibe mkhalidwe pofunika adzibwelela kwawo.

  14. Koma matsenga awo omasanduka afisi mkumaluma amalawi chonde tisazione, komaso chonde asecheni palipose asalowe ndi akasinja kut azithyolela zitseko ndikumaba katundu. Pomaliza akumbutseni kut timaotcha munthu akapezeka ataba choncho asunge mwambo

  15. Zowona ndine m,modzi eni mzmbque ndizowona ngakhale anuwakefe timazuzika ngati alendo moti tikalowa m,malawi timapanga zinthu momasuka komabe tisungeni anthu owopa mulungu inu

  16. Si anthu awa njoka izi kwao amanyada kwambiri agalu awa kudutsa miseu yakwao ali ndi zimalamulo ngati sanavutikepo

  17. Mutafusa akut kwawokuno kwatan chfukwa kuno kulbe kapena amenewo akuthengo km muno kulbe nkhondo kkkkkkkkkkk mmmmmm ayooooooo

  18. We know that mozambicans,hates malawians but malawians does not hate them.We always welcome any individual despite,colour of skin,race,religion or nationality knowing that, we all belong to one creater(JEHOVA GOD).

  19. Bwinoni ndi anthu amenewa. Ngankhanza ndithu. Ku Nsanje anawaletsa kukalima minda, moti sakhalitsana bwino, chikhalireni amaoloka ku Malawi kukathandizidwa mankhwala kuchipatala.

  20. Alandireni koma asiye kutizunza mminsewu ya kwawoi, makamaka pa chamano boarder ndi pa tete bridge.komaxo zoti tikapempha madzi akumwa asiye kutipatsa othira mchere .

  21. Koma a Malawife aaaaaaah ifenso ndiye kaya! Inu Ziko la mozambik likukaniza njira yoti sitima ifike pa Doko la Bingu! Inu ndiye mukuwavomeranso amenewa kuti azitithera ma resources athu??? Nkhondoyo taiyambisa ndi ifeyo kodi??? Anthu amenewa amatipanga chikuwawe siomawasekelera amenewa ayi

    1. Aaaaah za zea! Masiku omaliza kulibe konda mzako monga uzikondera kkkkkkkk! Thus y a Malawi tizakhala anthu osalira mpakana kale kale! Iwe usanamepo apa! Masiku ano chasala ndi konda Ndalama monga m’mene uzikondera!! Mukanakhala anthu achilungamo mukanapita mukawalalikire a Mabungwe amene alolera kuti inu a Malawi muvomereze mathanyula chifukwa chokonda Ndalama! Usataye nthawi yako ndi kuti undilalikire ine wamva?? Cz Masiku ano chakula ndi chinyengo!! Ikakhala nkhani ya ma refugeese yi isakuwawe awowo ndi maganizo aine nawenso uli ndi ufulu ongonena maganizo ako not kundilalikira

  22. Malawi dziko la anthu opempheradi komaso okonda mtendere.. Dziko la Mozambique anthu akuzunzika kuti adutse kupita ku Zimbabwe or RSA.. Kumawalipiritsa anthu ma R50 ena R100.. Ena akachitikanso tsoka akumamenyedwa ndi Asilikali awo.. Ndiye mukamati akuthawira ku Malawi aaaaa God Bless Malawi..

  23. What Malawi Gvt is doing is like playing with Lions or snakes l know these people they don’t have manners at all Villages near them at total mess believe you me. l have stayed with these people around the boarder anthu amenewa amazunza kwambiri and sayamika you caint walk or travel in their land freely without them tip off their authorities to abuse or detained u. My four years of stay with these people lived in hell. because of our parents and ancestors let them stay

  24. azipita kwao ndikuti zandiyipira ,,nnaona akuwakwapula amalawi pa dzobwe chifukwa choti anapanga overstay ku rsa zosagwilizana ,azipita ndikuti

  25. Let them in,. but they have to learn about life this time as Africans n neighbors,, we don’t have to be hard to forgive, let God bless Malawi as a peaceful nation

  26. Eish am abit nervous how to go back home through there roads these Makambaraza are hard and heartless…..imagine just to pass through there boarders what they ask is 1,000 Americano dollar( kkkk yet they dont knw its value)and you wonder why since i got all documents right.But never mind dont punish them back they are still our brothers and sisster…..keep them though its not first time,pray for peace in there country and more freedom and peace in our country so that we can keep them in time of bullets like ths.

  27. okay. welcome malawi, km mumwele ndi chakunya chanu musapatse mavuto ena president tikulila mavuto anjala sono mukutawa kwanu mukufuna mumalize ndla zakumalawi pa mundimbela ndalama zanga ena pamene ndi kapita

  28. Poti Malawi ndiwachifundo ndi anthu obwera,,,, km akanakhara kuti amafikira nkhomo ndi nkhomo ine ndikanawakana coz awa pa chimano border amavta heavy

  29. M’malo moti muthandize anthu anu akufa ndi njala ndalama mukukathela ma tchangani ozolowela nkhondo kwawo iwowo angalandile ndani ndinkhaza zawodzo!!!!!!..

  30. Malawi akutukwanidwa leloyu kutj overpopulated nkhani yake ndi anthu amwnewa nkhondo ikatha safuna kubwerera kwawo mxiieew! Olo kuwathamangitsa kuwaudza kuti Malawi naye alibe chakudya komanso ali pamavuto adzaoneneni iunkhani ya chuma… Anationapo ife tikumenyana? Koma akuona ngati ife tilibe pulobulemu? Nooo timakana zimenezi zoti tizizazumzika m’mayiko a eni ake. Nkhondo yawoyo ikazatha asazakhare kuno azakumbukire kwawo asathe malo kuno…

  31. Koma chisoni chinaphesa nkhwali anthu amenewa ndiwovuta ngakhale kungodusa mdziko lawo kupita ku Zimbabwe kapena ku Jon amatizunza mpaka kuti bela ndiye zitakhala kuti zativuta kwathuko mkuthawira kwawoku angatisamale???

    1. nthawi zina tisamangolola zilizonse, anthu amenewa osalephera ena akulowanso ndi mfuti mdziko muno as a result securitywise, we not safe.

    2. nthawi zina tisamangolola zilizonse, anthu amenewa osalephera ena akulowanso ndi mfuti mdziko muno as a result securitywise, we not safe.

  32. I hate the Mozambicans, very self-centered people, heartless,full of hatred.These people have got no mercy,they don’t take fellow people as humans. It’s a shame that they are seeking refuge there.When we are going to South Africa or coming back home,they treat us as animals not human beings.

  33. Ntchito yabwino imeneyo osabwezera choipa kwa wochita choipa. Anakhomelera doko lansanje. Amalawi tiope Mulungu azatitukula

  34. Mistakes has no master, ndi abale ndi alongo tiyeni tiwalandile m’mene tinawalandilira maburundi chifukwa mphamvu ya Mulungu siinama, welcome to malawi the warm heart of africa no xenophobia here stay with peace

  35. Pankhani ya nkhondo ngati mwai wapezeka mkupulumuka chonchi mmmmmm yamikani Mulungu ndikuwauza kt azikhala ndi mtendere wawo kuno mku Malawi welcome.

    1. mpake ine andifusa akuti mwini wake wa passport yanga Ali kuti ine ndati its me akuti nanga bwanji sunavale zovala zili pa passport cholinga a ndichose ndalama

    2. Mmmmm #George..zimene amapanga anthu amenewa sindimatha kuzimvetsa kuimitsa ullendo akuti aone galimo ngati sikutaya oil kupa kuti uwadettsela mseu wawo.#Nyirend,anthu amenewa akamakupanga search amakhala ngati akupeza kale ndi Vuto

    3. Athu ankhaza kwabasi takhala masiku 5tilikubwezedwa pa bridge limene lili ma roadblock awiwri. Koma poti ndife antendere asungeni basi.

    4. Awatu afera zaweni, even mu boarder akwathumu alimo akhalidwe oterowo, umayamba kusupa pa mwanza pomwepa, nde amenewo akhululukireni basi alowe.

    5. Alandileni mwachikondi kuti adziwe ndife anthu amtendere. Ngakhale ndikudusa mudziko lawo ulendo wa ku SA ananditsitsa mgalimoto kukandilimisa mmunda kamba koti ndinalibe R3000.

    6. ndipo amwene simunama a2 oipa kooopsa. amapanga nkhaza ngati kuti tifuna tipephe Malo pomwe ulendo wanthu umakhala wautali.

    7. Kma ndiwanthu ozikonda bad kuposanso anthu akomwe ukupitako sindikuziwa kt mdaliso ukadakhala mziko mwao ndibwemzi amalawi akuphedwa angat per night kapena kt zinthu zikanakhala bwanji?

    8. #Mr Chisinga,tiri pamavuto anthu awa akangokhalitsa muona ayamba kuonetsa khallidwe lawo angati momwe amatichitila muja tikamadutsa mu Dziko lawo akuthawalo..

    9. zi anthu zakhaza kwambili nanji akava kut ndmalawi eshiii or apolice awo asawone #plet ya galimoto ya malawi sikukakamila kwake

  36. Amenewo awabweze kwa kwawo coz last week apolice anayimisa galimoto yomwe munali amalawi amwe abwela kuno ku south africa ndikuwamenya anthu kenako kuwalanda ndalama.one of them ndi bale wanga so faz imeneyo ndiyoipa izipita kwawo.

    1. Uyu sanalakwe ayi, wanena bwino zedi. Anthu aku Mozambiki kunyasa too much amakhala ngati sitinawalere kwa nthawi yayitali kuno. M’malo mophunzitsana kukhala a ulemu iwo amatipangira nkhanza ku dziko lawo la nkhondolo. Iya abwerere lkwao konko

Comments are closed.