Queens Central Hospital for sale! Government to privatise public hospitals
…Kamuzu Central Hospital put on auction

Malawi government has set up plans to privatise all public hospitals, Malawi24 can reveal.
President Peter Mutharika made the revelation that his administration will soon start auctioning public hospitals into private hands in an exclusive interview with BBC Hard Talk’s Zeinab Badawi.
Mutharika said the plans, likely to draw a public wrath, was hatched to address the current drug shortages which he said started with donors’ decision to withdraw aid from Malawi.
“We have no medicines in hospitals. We are trying to bring private sector into hospital management and we hope it will work” Mutharika told BBC Hard Talk.
The president did not clarify how putting hospitals in private hands motivated by profit will improve accessibility of medical services.
Malawi24 reported earlier this week that some public hospitals in rural areas exorbitantly charging patients over K25 thousand.
1,909 thoughts on “Queens Central Hospital for sale! Government to privatise public hospitals”
Comments are closed.

zikanakhala zothandiza kwambili kukanakhala kuti atsogoleli athu zi mbava ! koma apa zikuonetseratu kuti ,mukufuna mube zambili chifukwa ndalama zimenezo sizizagwira ntchito potukulila malawi koma kuzangokhala kutukula atsogoleli omwe akuyendetsa dziko,,, gulitsani zipatalazo ife tizikagula panado pa shop motchipa chifukwa ndalama zopitila ku chipatala cholipila tilibe!!!!!!
Tithawa muno mmalawi
zachamba,amphawi a zitani omwe alibe ndalamaaaaaaa?
Ingogulitsani tonsefe muchuke ndinu mukagulisa zipatala osaukafe tizingofa mukhale ndinu olemelanu
nyapapi
No1 Ayamba kugulisa manda abingu bwanji osati kuti gulisi zipala zanthu zosauka kale makhwalazi. NO 2 kodi njala ikavuta pabanja njira yonthesela njala ndikugulisa ana mbanjamo izi ndizopanda sogolo a malawi ndi a uphawi sangakwanise kulipira mitengo yama privet. NO 2 ngati ukuziwa mano atha suswa phale ngati zaka wina zamchepela kungosazi ka wakumuzi
Malawi iwe dzuka ndikale lomwe unayamba ku gona!! Why?
palaboma lamutondani ntchiwemi thulani udindo mdziganizila anthu ndalama waitole nkhuni masuzgo yachali malawi ganizila wanthu iwe.
Ena aja zimayenda bwanji KO’d …ndekuti zativutatu
palaboma lamutondani ntchiwemi thulani udindo mdziganizila anthu ndalama waitole nkhuni masuzgo yacha
Mkulu ameneyo amadwala mwela kkkk
Koma mtundu uwu eish kodi osatenga ma tillion omwe apanga kalewo tsono akagulitsa akuti osauka azitani? Too selfish iye ndi abanja ake amapita kuzipatala zakunja tsono akumudzi. Ingotiphani tonse mutsale ndinu mwamva
State houseis next to be privatised wait nzagula ndine kkk
Nanga awawa azakwanitsa zolipilazo? azimayi uyutu sim’malawi adabwera kuno kuzakumalizani.
Nanga awawa azakwanitsa zolipilazo? azimayi uyutu sim’malawi adabwera kuno kuzakumalizani.
Chitsilu Peter Mutharika.
BWANJ AKANAYAMBA WAGULITSA CHIPANI CHAKE CHA DPP? PVT CLINIC KUT MUKHALE MANKHWALA AKUMADALIRA ZABOMAZ AKABAMO MANKHWALA AKUMAKAGULITSA KU PVT CLINICS.NDMAONA NGAT NDBWNO AKANATHETSA ZPATALA ZOLIPIRAZ.ASAGULITSE ZNTHU NGAT ABWERA KUZAKHALA MBOMAMU AYI NDPO AYI!ASAEREKEZE NDTHU.
gulitsani ifenso mutigulitse ku lraq
Let him build his on hospitals & sell them himself. This is stupidity readership Mr President.
Dziko ramukulira wina koma ndigalu ndithu amenei bwanji aa