Donors thanked for suspending aid to Malawi

Advertisement
Dorothy-Ngoma

The National Association of Nurses and Midwives in Malawi (NONM) has applauded donors for suspending aid to Malawi.

Executive director for NONM, Dorothy Ngoma, said the action by donors to suspend aid to the country needs to mark a way for setting priorities and transparency.

“It is very embarrassing that you are helping someone to have a shirt but the person is using the money to drink beer, how can donors come in to help if you are not setting priorities.”

Dorothy-Ngoma
Ngoma says donors opted for a good decision.

“There is no food for the patients in public hospitals and the government says there is no money and the same government is spending millions of Kwacha to buy luxury vehicles while people are dying in hospitals,” Ngoma told the local press.

Ngoma further said authorities need to stop taking money from the public purse to buy luxuries.

“Those who need cars should wait this is not the time to buy cars, whatever is there should be directed to important sectors,” added Ngoma.

Several of Malawi’s donors cut off aid to the country due to lack of transparency and accountability.

Advertisement

261 Comments

 1. Ngoma you are very true, go a head with constractive critism.a foolish president

 2. Its a shame that the reporters of Malawi 24 look half baked,,,, all who are commenting find out her live speech what she had to say,,,,, not this twisted information. Malawi 24 b professional ,,,

 3. Mayiyu ndi chitsiru, alibe nzeru or pang’ono. Anaipa ndi mtima omwe. Akutichititsa manyazi ma nurse fe. She is nt fit to b our leader, she is more of a politician nt activist. She must apologise to malawians for the nonsense she has said. Alibe chikondi ndi amalawi. Munthu oipa iwe, mfiti

 4. mayiwa alakwa chani kut muzingo atukwana? kod nkhaniyo mwaiwrrenga modekha kapena munakali ndi ma hang ovr ?enanu ndikuvananu chisoni mukumadziona ngat owoneka bwino kuposa maiwa pomwe muli onyasa kuposa manyi,,,,,,muziganiza polankhula ,,,,,,stupid……ine siwachipani koma maiwa sindikuonapo chomwe alakwa kut nkuwatukwana ……agalu…

 5. How can aid suspension be something that a Malawian can be happy about?
  That is being unpatriotic.
  If this nation sinks, then we will sink together. Let us wish our nation well. God gave Malawi to us .
  We don’t have another Malawi else where.

 6. osamakonda dziko lanu bwanji who is going to sufer after all si a chazimbuyanu kumudziko who is not someone insane can rejoice on such punishment kupanda nzeru zaumunthu uku anthu akufa chifukwa chosowa mnkhwala njala ndi zina wina nkumaombera mmanja shupit!

 7. Malawianz lets love our selves,ur applauding donors 4nt givng aid to malawi who wil suffer if not poor ppo, if u hav evrtng in ur homz som1 out there z struggling to find ameal once aday! What a shame

 8. Dont jst comment musanamvere wat she said. A malawi 24 mwanama. If u don’t believe it, tune in zbs friday evening amapanga repeat pa program ya tiuzeni zoona. Mumve zomwe Ngoma anayankhula.

 9. Mayi mwayankhula mwamzeru ndlama zilipo evryone knows koma taonani ma Mp boma akungogawana amalawi inu ma donner athandiza kwa zaka zambiri koma simukusintha vuto lake mukawiner u Mp mumafuna kulemera enanu amene zakubhowani i know kuti u dont know the meaning of this report ur just DPP supporters if the country was well gorvened ma donors sakanasiya but due to poor govrnment ma donor apita this will help,boma lisia kuba ndlama i think zimawachulukira

  1. STUPIT ZACHARIA. Dorothy is right how can government spent lots of money on cars while there is no drugs in hospitals? your a BIG FOOL like amalume ako a Pitala kkkkkkkkk

 10. Inu azungu asakupusitseni, kodi munthu uli ndi nkhuku koma ulibe ufa ,mbale wina akupatse ufa ndiye kuti iwe usaphe NKHUku nkudyela chifukwa wapempha ufa? Ndalama zao timapangila zomwe akufuna zathunso tipangile zomwe tikuona kuti nzofunika osati alamulire zao ndi zathu zomwe.no no no no

 11. kodi maiyu walakwitsa chani? ndalama sizikubedwadi monga? magalimoto mesa agulidwadi?, kodi y do malawians hate chilungamo? ma doners ati topeladi nanga chifukwa cha mbava za Boma, THE GOVERNMENT OF FULL OF ELDERS BUT WITH EMPTY HEADS

 12. Oh mpaka pamenepo komatu mayi musayakhule mopusa with de aim kuti akutameni. inu2 simusowa kathu kukhomo kwanu, amavutika ndi wakumudzi amene amapezako ka mtendere ndi tindalama tonyenyeka tomweto 4rm ma donors, MAYI INU I NEVER THOUGHT DAT U THINK STUPIT LYK DIS!!

 13. She is right, imagine you buy vehicles when there are other vehicles on presidential fleet as well as those of parliament.
  You Malawi24,why dont you publish my post of Thomas Sankara of Burkina Task for people of Malawi to appropriate how that selfless patriotic TRUE son of Africa did for Burkinabes?

 14. Inu a Malawi 24 you didn’t listen to her speech and now mukupeka nkhani so anthu should blame nurses. Did you know that nurses marched last week to deliver petitions in various districts so that the government should invest more in health? Muzitha kukana akakutumani to report zabodza

 15. amalawi anzanga muzanyoza dorothy ngoma kumati woipa mtima komatu amalawi 24 sanamvese bwino speech ya mzimaiyu, inali pa zodiak tiuzeni zoona, ananena kuti ma donors apanga freez aid yawo becouse our leaders are spending recklessly, and or mutakhala inu m’bale wanu mwamupasa ndalama wamwera kenako kukupempha fertliser mumupasa? She was clarifying the reasons for the withdrawal of the aid and she said the reasons are enough and not neccessarily thanking them, malawi 24 ndiodanisa

 16. am nut a fun of dolophy ngoma,,,,, she is a shit ofcoz but the reasonin in ths story i like,,,,,,, hw cud ths so cod gvnt spend such hug money on cars whn the country has no money?

 17. mai inu ndinu wopusa, kodi azungu ndi anzeru zedi pochotsa Aid kuno ku Malawi?
  Azungu ndi kapasule simudziwa amafuna aliyense akhale kapolo ku ndalama yawo, inu mukuyamikira anthu wodanitsa amenewa? siganiza olo pangono inde amalawi ena akuba ndalama koma bwanji iwo akuthandizana wokhawokha pamene kwawo katangala akuposa wa Malawi???

 18. Mulomo udzakupeza samala polankhula kwandutchuke nanthambwe anazitengera tisakumveni mukunsa kukweza malipiro akutumani eti?

 19. Ofcos we need donation, but of what use is the donation if it is not serving the masses. Zikungofanana ndi kupepha yandiwo kwaneba basi kenako madala nkuzatenga yopempha yomweyo nkukagula yawo mnyumba mulibe chokudya chilichonse

 20. Donors thanked for withdrawing aid? Ha ha ha ha! Is this woman a Malawian? Is this the reason why ur sister JB is still in exile to plead with donors not to resume aid? What a bunch of heartless women u are!

 21. So people went to school to get educated but turned out to be dump,how can you applaud donors from suspending Aid.we understand the situation but also at the same time feel pity for those that need the Aid.

 22. Kuganiza mwa umbuzi konya pomwe ikudya uku mkodzo pwatapwata!Munthu wokonda dziko lake sangafike apa ayi,chifukwa chotumikira maganizo kaya ndale kudzipuza yekha.Kuganiza nkumati unyandulapo ndani?.

 23. Kd mzmaiyu n’nda?ndpo amakhalira kt? ntamtumzira anyamata anga akamuongole#Boko haran,Isil n’ Al_Qaida

 24. Kd mzmaiyu n’nda?ndpo amakhalira kt? ntamtumzira anyamata anga akamuongole#Boko haran,Isil n’ Al_Qaida

 25. Dorothy, simkumvetsa inu mwakhuta mowa wa DPP , she is making a very good point, the country has big crucial problems yet ur so called pres is buying expensive cars by the way who made him a president?

 26. Plz plz guys- Let me withraw the statement of this senseless woman- ‘Donors resume your Aid in Malawi because we need more posh cars for our politicians!

 27. Plz plz guys- Let me withraw the statement of this senseless woman- ‘Donors resume your Aid in Malawi because we need more posh cars for our politicians!

 28. Kodi akudyetsa chisikono kukamwa kwakoko?azimai timakupatsani ulemu km apa pokha ulemu tiwusiye apo iweyo ndiwe galu

 29. Kodi akudyetsa chisikono kukamwa kwakoko?azimai timakupatsani ulemu km apa pokha ulemu tiwusiye apo iweyo ndiwe galu

 30. Zoti mfiti yaikazi ndiyoopsya kwambiri ,ndakhulupilira pa maiyu.Malankhulidwe osoweka umunthuwa tikumatenga kuti? Tikuyenera kudziwa kuti pulezidenti sakuvutika ndipo ma donors amatithandiza ife osauka akumudzi

 31. Zoti mfiti yaikazi ndiyoopsya kwambiri ,ndakhulupilira pa maiyu.Malankhulidwe osoweka umunthuwa tikumatenga kuti? Tikuyenera kudziwa kuti pulezidenti sakuvutika ndipo ma donors amatithandiza ife osauka akumudzi

 32. It is very unpatriotic to take pride over suspension or withdrawal of budgetary support by the development partners. We are likened a people sailing in rough waters and should the ship sink, we will all perish. So we need to be careful as a people who love their country to be very positive about our country

 33. amalawi tiyeni tikonde dziko lathu tisasemerane chinyau tokhatokha kodi inu amene mumazitenga kut ndinu anzeru kmanso ophunzira bwanji simunachita kanthu kt zinthu zisithe mdziko muno kusiyana ndikumanena malipoti onyazitsa dziko lanu lomwe chot mudziwe nchakut sionse amene ali ochita bwino muzunzitsa abele anu kumudzi mukutsekeleza madonors chonsecho ndalamazo akakupatsan mukumaba kut muoneke ngat anthu ayi mutipeza ndimalankhulidwe anu ankamwa mosatsukamo tokotan mmene mungathele zadziko lanu km mawa muzazindikira kt sibwino kuzinenera wekha choipa

 34. Dorothy wayamba ndale! Chifukwa choti boma la JB anamupatsa udindo zizakhuzane ndi NONM cz ma nurse si andale……..ingotulani udindo mupitilidze ndale bx

 35. thats the more reason why i dnt comment some of the issues here,read the whole story before you start shouting at Dorothy,get her points before you act.Dorothy is quite true,munthu akupatse ndalama ukagule shirt iwe kukamwera mowa,pali dzeru?the doners give us money,we spend the money by buying things that can not help us,wake up malawi,sinthawi yomapita kunja ku misonkhano spending millions yet people are starving out there.

  1. beggers have no choice,mind you.its too pathetic that when doners are giving us money,the first priority we do is to cashgate the money instead of helping the needy.with our situation now,its time to reduce the number of vehicles each minister uses,reduce the motercade the president uses,reduce the trips abroad where the expenditure is always more than the benefits.wake up malawians

 36. Chimene akufuna kutanthauza ndi choti ngakhale ma donors atapitiliza kutipatsa ndalama a malawi sapindula kanthu chifukwa ndalamazo sizigwiritsidwa njira yoyenelela. I fully support you D ngoma

 37. where are the leaders ?people are dying busy spend money in moving what are u looking for as u say that we do not want donors,no person is an island,buying luxury cars why not to buy food and medicine for the need,where is country milk and honey

 38. Iwe zimai iwe ndikuchotsa ntchito bwanj sukuyagana kutsongolo ngat iwe unalemera kwanu koko sizintheka ineso ndine womphuzira kuposa iweyo

 39. Off course we are on the path to economic freedom. Those who applaud donors for their aid withdrawal, yes, tell them to withdraw their embassies as well so that you are more than happy. You are leaders of a corrupt group and we know your silly master.

 40. Ifenso tikuthokoza kuti ma Nurse ambiri samapedza mabanja kapena kuti samakwatiwa vuto lake mwalidziwa …….. Kkkkk anthu openga mwapanga bwanji kodi.

 41. Afunseni anamwino akuuzani bwino za mai ameneyu. Woyipa maganizo kwambiri. Akapitiriza anthu amuchotsa mabele

 42. Kodi maonekedwe kapena kuti nkhope ya munthu imatha kufotokoza mene uliri mtima wake.Kuipa nkhope ndi mtima womwe.Mai ameneyi ngwakumidima ndithu,ali ndi abale ameneyi,samalani pofuna kulankhula mai.Even walls have ears.

 43. mayi ameneyi akuyenela kupepesa kwa mtundu wa amalawi,,

 44. uku ndiye kulankhula kwauchitsiru. Iyeyo akamanyadila ndiye avutike ndani. Yemweyo akumakatenga ma injuction kumapanga protest kuti sakuwalemba ntchito ndiye akuganiza kuti ndalama zake zizichoka kuti akawalemba. Pakuti anthu omwe akuwanena kuti awachita bwinowo zao zikuenda akunkela akulemelelabe. Ndipo ameneyi wandipyesa ntima akadakhala pafupi ndikanamupasa kuti audye pakuti adazolowela kuona zilonda ngai nyama. Munthu wanji osakonda dzikolake, asamalankhule ngati atamupasa 1 month kuti ayendese dziko angakwanise

 45. Dorothy Ngoma watsala ndi masiku owerengeka kuti ufe.bwanji kuyankhula ngati ukuyankhulira #kunyero??? Kuyankhula mopusa chonchi bwanji?? Abale ako onse ndiochitabwino moti akadwala kamfuno akhonza kupita kunja?? Usandiyankhulitse pambali wa #satanic_iwe,kagwere uko. All in all dziko liziyendabe,kaya mwapendapenda only God Knowz

 46. Nonse amene mwayika makomenti anu apa simkudziwa chimene mukuchita/simkumvetsetsetsa nkhani mwangowerenga mutu okhawo mwasiya thunthu lankhaniyo chonde!kumamvetsa bwino nkhani osapupuluma polemba makomenti A DOROTHY NGOMA AKUNENA CHILUNGAMO CHENICHENI

  1. Man,kodi munthu akaphedwa pamsewu munganzindikire bwanji?? Mesa mumaonera nkhope?? Nanga nkhope imapezeka ku mapazi?? Mesa ku mutu,anthu apanga comment molinga ndi mutu. Ngati pali zolakwika,ndekuti alakwitsa ndi amalawi24.komabe palibe chanzeru chimene maiyu wayankhula.

 47. in malawi to day this to morrow that fuck u now, try to depend in on your own, use if u sit down and doing nothing waiting for some one to give u sothing every day you will be making head lines lyk that, wake up and do somethings to be proud shame on man!!.

 48. Stupid association of nurses and midwives. everyone knows that malawi cant survive without donor aid. for their own information Kamuzu college of nursing which trains nurses here in malawi its fees were raized from 55 000 to 275 000 due to lack of donor aid as if many parents could afford that.

 49. mxiii doners thanked for suspending aid and someone is happy about this so who is the victim here selfishness and lack of patriotism

 50. Hahahahaha.Mpaka federal system yidzatheke basi.Cashgate is evil.Andale ndi azitsogoleli athu aphunzire kutumikira anthu wosati kumawaberanso munjira ya katangale,ziphuphu ndi kashigeti sikando.kkkkkkkkkkk.

 51. The opposite is true,”Government suspends the recruitiment of nurses and midwives due to lack of donor funding…Shame on all nurses&midwives”

 52. chison alibe ma nurse ndi anthu akhanzadi she knws that she cant suffer at all olo zitavuta muzipatalamo poti iye ali ndiwaulemu wake akeee….aganizile anthu omwe ndi ovutika pot iye amadya amakhuta bas aziyankhula mopepela choncho ….amphawi apumila kuti abale aaa zinazi koma foolish woman

  1. #memories….am comenting wat i hav heard not wat i hv nt heard…i cant even hv issues about ndani saziwa kuti manurse ambiri amakhala ankhanza not all are cruel but sam lyk this ngoma chison alibe wazionesela poyera kuipisisa kwake….she ia there to help pipo not kuyankhula fundo zake zopanda mutuzo azipwetekesa chabe anthu osalakwa

  1. usalimbane ndi bwampini zake zinayela kale. Ovutika ndi iwe ndi ine, mai wakoyo walankhula ngati anadya bibi ndipo sizodabwisa bcz madotolo amatha kumaliza munthu paja

  2. Jealousy is always bad for development,chifukwa chake Malawi amangokhala malo amodzi.keep hating but when we start reaping the fruits don’t wanna hear u say fre!fre!,

  3. Kodi guyz ine ndangofunsatu.winawe nde ukuti za bwampini zinaera kale,musapuse atate ndalama sizikwana munthu.komaso funso langa ndimafusa MALAWI 24,Nde ndudabwa kuti inu mwasanduka MALAWI 24?

  4. Kodi guyz ine ndangofunsatu.winawe nde ukuti za bwampini zinaera kale,musapuse atate ndalama sizikwana munthu.komaso funso langa ndimafusa MALAWI 24,Nde ndudabwa kuti inu mwasanduka MALAWI 24?

  5. Ndalama sizikwana yes komano sikuti ali monga ulili iwe ndi ine, sindkuziwa ngati munkhaniyi alankhulamo za Bwampini. Kulankhula mau onyoza sizingabwelese chitukuko pamalawi. Komabe timakumvesani anzathu akumpoto kuti kunyoza kutukwana ndi sankho ndiye nkhalidwe wanu. Nkhani yabwinobwino mumafuna mpaka munyoze anzanu. Anthu ambili omwe amakonda kunyoza pa fb ndi akumpoto kutanthauza kuti khalidwe alibe ndiye ngati simusintha ndithu muzakhala chomwecho ndisankholanulo anzanu akupita pasogolo

  6. Kikkkkk Walani Pepa ngati ndakulakwira.mwina anzathu phindu mumaliona.koma ineyo mmmm nsaname.komano zikusiana pati?usalimbane ndi ku mpoto,paja sikumalawitu.uone wayambitsa mau oti bwampini munkhaniyi siwakumpotoso.munangodana nafe.

  7. I tend to wonder what the heck is the so called bwampini has to do with the above article? Nthawi zina uchitsiru ukakhodzokera munthu amalankhuladi zosemphana ndinkhani! Mr kumbu chithira nyirenda this will take you nowhere! I am sorry to call you very stupid!

  8. I accept to be called stupid thats what i am,but that wont even make me smile seing heartless people squandering funds that were meant for the poor Malawian who is suffering out there.You can say whatever you wish to say but ‘YES BWANA’ will take us nowhere.

  9. Mayiyu siwada ndi kumatako komwe ameneyu?? nanga pamenepa umunthu uli pati?? ndiye aziti tilembereni ma nurse eeeh koma zakudya mzipatalamu!! chimthakati ichi sichiri patriotic ata 1 shame!!

 53. Is there something to thank for malawians? Are we saying we are bewitching our country ourselves? What is really going on through your mind? Is it the end result of your downfall? Thank God you have produced your ideas and we have known them!

 54. koma ngati mai iyu analankhuladi mau amewa eshiee dziko lanu simulijonda mukufuna kusangalatsa ndani ndimalankhulidwe anu opanda mzeluwo dziwani ichi zisankho zinapita ndipo APM ndiye president chotsani mkhwiyo wanu kamba kazisankho ovutika ndi ife osauka inu mumapita ku Garden City ku South Africa , Mwai Wathu komaso yanbani kupemphela muchoonadi dziko ndilithu ili

  1. #clement ,analankhuladi kwa kazembe wa dziko la germany ngakhalenso wa britain mayiyu mutu mwake mulibe nzeru mpang’ono pomwe ,munthu wa dziko la malawi kuyipisa mbiri ya abale ake ,ayi ayi ayi mayi mfiti uyu

 55. Good keep clapping we will see who is gonna be laughing when the economy of the nation goes on its knees and your salaries can’t be paid but your bills scream for attention, think before you talk. Amalawi openga mwapanga bwanji?

 56. ha,difficult to understand,happy with what?happy to see malawians suffering,I cant honoudifficult to understand,happy to see malawians suffering,you are not loving your country mama

 57. Kungowina Chakwera mavuto onsewa azatha ngakhale zomangotaya anthu chisawawa omwe afa pangozi zidzatha chifukwa Macard komaso ambulance zonyamula anthu zizakhala zikupezeka paliponse ngati momwe zinalirikale MCP ikulamulira.Talira mokwana God is just looking one day will answer

 58. Mayi uyu dzulo amangozikolakola yekha ntolankhani akuwapanga interview ,zomvesa chisoni kuti mayiyu kuyamikira kuti ma donnors achita bwino kuimika thandizo,eeeeesh nzimayi wanji uyu

 59. anthu opusa kwambiri who will suffer bwtn the President or his government… & poor Malawians omwe aliphe kumudzi ///anthu openga inu///osangosiya zintchitozo bwanji anzanu alowemo

  1. Amako anakuphuzisa zopusa ndithu komanso m’dala wako ndiwakabanga kuvkwana ngati mfiti pagulu? Opanda manyazi ngati banbo ako ndipo m’mutu mwakomo mulibe bongo. Katukwane amako amene anakuphunzisa osati pagulupa shame!

 60. esh Koma boma lagula magalimoto abwino komaso odula ndalama za mlimi zonse akuziwa ndi ambuye kaya chonchobe masiku osiriza no solution to current up until jesus comes back koma muzalipira oneday mulungu akuona

 61. esh Koma boma lagula magalimoto abwino komaso odula ndalama za mlimi zonse akuziwa ndi ambuye kaya chonchobe masiku osiriza no solution to current up until jesus comes back koma muzalipira oneday mulungu akuona

 62. sorry madam, think again! if you are there happy that donors stopped supporting malawians then you better step down. Your character is always questionable. may be you are part of this club that says jews should pack and go! No wonder our nurses behave like rabid dogs.

 63. Izi ndizomvesa chisoni kwambiri…let us jst help the gvt by payin taxes so tht we cn gt reach the needy!

 64. Big up to t ndie timve kuti akupanga za u g*y tiyambanapo komaxo amalawi sizoti tipite kumademo ai taziyamba tokha tizimalize basi kkkk koma nyasaland bolaxo gebuza

 65. Working under instructions from jb she also wants to use nurses to put government to pressure she is not patriotic madam loud mouth are you not ashamed?

 66. Ineo zakhala bwino coz ndalama zimangothera mmatumba mwao first muyambe mwaona kaye kuti asia why coz ma nurse samalembedwa koma donor alipo kumalandira ndalama zochepa koma azitsogoleri kumazikundikira .

 67. kodi munti galimoto ,,zilikuti simutionesa,, aid was frozen during period,,this is aftamath of c~gate,,whoz to blame,,its zodiak ,,kamlepo,,dorophy ngoma,,,chakwera,,dpp,,

 68. Ndiye tisakumveni mukulira kuti boma silikukulipirani kapena silikupanga recruit ma nurse.anthu osakonda dziko lanu ngati inu mudzafa imfa yowawa

  1. Iwe nde opepera ndlama zoinse akugula magalimoto zija sizikanathandiza taganizani bwinobwino osangoti poti ndinu aDpp

  2. Iwexo uzafa imfa yowawa @ Enock. Out of all wat she said munangofuna kukamba za ma donors basi @ admin. Talk of ma patients kudya kamodzi, mankhwala kusowa, ma ambulances, recruitment of nurses, doctor, lab tech, clinicians. Mwaxowa zolemba eti

  3. timakutengani ngati anthu anzeru koma mwatikhumudwitsa,madona akapele mumasangalala ndinunomwe,kumakhalako ndi umuthu nthawi ina.

  4. Zawonetsa kuti ngakhale ndalama zitabwera zambiri azingodya okha.sikuti manurse ndiopanda mzeru,koma mmalo mothandiza mavuto akuchipatala ndizina ndalama ndikumakagulira magalimoto?This govt z very stupid.

 69. Donors stopped their donations long time ago before the coming in of this government. They stopped during PP regime. These Non-Govermental Organization are just there to enrich themselves

  1. Mmalawi opusa iwe #kondwani sungatchule munthu kuti bwampini pamene bwampini ali iwe sichinthu cha nzeru achina #DOROTHY_NGOMA uyu ndi nzimayi omvesa chisoni zedi ,dzulo ndinamvera interview yake koma zoyankha zake zosagwira mtima

  1. @john nde wapindulanji by kutukwana?…so u av satisfied ur self by saying that?…..do u feel it is appropriate to show ur anger and foolishness on a public platform like this?

  2. Eti zamuwawa bwanji?? Pamtumbo pako iweso wamva. Panyero pako namachende iwe. Our parents r suffering in villages coz these donors cut their aid and you r hape.?? U r crazy. Go in villages and c even some pipo in town r n troubles. Mbole yako iwe wamva. Shame on uu!

Comments are closed.