Heavy flooding hits Malawi

Advertisement

Malawi has once again been caught unaware! Reports reaching Malawi24 newsroom indicate that most parts of Blantyre have been flooded because of incessant rains leaving many properties damaged.

More details to follow…

If you are in the affected areas, please send us a message or images on Facebook or through email: [email protected]

Malawi Floods Malawi Floods (2) Malawi Floods 1 Malawi Floods 2

 

Advertisement

237 Comments

  1. Whch part of Blantyre has been hint by floods? Osamatinamizapo apa kodi ife timakhala kuti? Kambani kuti nyumba zina zaonongeka cz of heavy storm. Storm & floods r 2different things..wagwan ć u?

    1. Do you even know Blantyre? Those are pictures of Limbe just before pa hardware. Limbe is in Blantyre if you didn’t know. In case you are trying to get technical, a place is flooded when it is submerged in water and I dunno about your eyes but those cars are half way submerged.

  2. Mwayiwala kuchikwawa anaziona kale anthu,ziweto mayimba adapita pano mukuona ngati zachilendo.ngakhale maiko olemela nawo ma floods alipo .

  3. Chofunika ndikukhala wochenjera chifukwa ano ndimasiku omaliza. Komaso yesu ananeneratu zamasiku omaliza. Chonde zinazi ndi zizindikiro za masiku omaliza.

  4. This has also happened in Mzimba; The reality is that we are ignorant of who to involve to help us out. Stop fighting one another & let God’s intervetion eradicate such an overwhelming problem. Politics have got nothing to do with this! Be knowledgeable to avoid unnecessary perishing!(Hos 4:6; Isa 5:13)

  5. Amalawi tizasiya kupusa liti mwagundika kuphoda ma profile pic flag ya france manyazi mulibe?? Nanga ku france akuziwani inu aphude aliyense opeperanu mwafasa kupenta ma profile anu kumbwambwana mxiiiiieeeew

  6. some people are wondering what the limbe flooding has to do with dpp.Sukulu siitha. Pse read this with great understanding: The cause of the flooding has been established to be bad drainage. Every construction project is supposed to be inspected by gvt inspectors, and unless you tell me otherwise, we still have a dpp gvt. As simple as that.

  7. Force majoure (acts of God)no one can completely avoid it zimaonetsa ukulu wake wa Mulungu kupanda izi kuchitika we can easily forget HIM nyengo ndiyake anayikhazikitsa kale no suprise to HIM Jesus prophecy of last days osati iyayi mitengo kulibe,amanga kuphiri , just imagine first rains only more disaster its Elnino rainy year more is to come

  8. Deep concerned about the victims but not surprised, I invite you to come for exemplo to kanengo in area 28 and look at the drains, all are blocked with rubish and city council do nothing about it.
    Last year we had a lot of property damaged because of that and this year more can be expected … if no action.

  9. Blantyer is almost a plateau than the lower shire, why the floods? Change of times – People from lower shire should donate relief items to the victims in Blantyer as the bad weather is not predictable; Last year it biow off roofs of Lilongwe’s Area 49 Dubai area; Lets kneel down & pray for God to protect us during the rain season;

  10. hahahaha inu limbe mwaidziwa lelo chaka chilichonse pamenepo ikamagwa mvula pamatelo ndipo sipokhapo in limbe pali malo angapo,mmalo moti muudze anthu asamale chilengedwe mukukamba za ndale,mvula imaononga kumene MWABADWA LELO KODI?

  11. Well……….am after BCC, they, with their friends frm the police, were busy burning fuel all day everyday chasing pple doing illegal vending, all in the name of cleaning the city, well u forgot abt making the city safe. Poor drainage i hear is the cause of the floods?*
    GOD is with us

  12. Koma umbuli winawu mvula ena akutchula chipani zosagwirizana ndi pangono pomwe.I think it is high time Malawi has been on bench,its our turn now face the real our friends faced

  13. Froma geographical point of view phepo ikuchokera cha kumvuma tiyembekezere zazikulu pa 18 onwards now iz bt nsanje ipumeko ku disidwa!

  14. Thank you JEHOVA GOD that you h’ve blessed malawians with water to drink unlike other countries that are currentry flaminng with the heat wave that is bringing disgrace and fear to the people.

  15. Many places are being visited by earthquakes, fire as well as flood, so that we may see that GOD’s judgement is @ hand.. Chofunika ndikuchita chifuniro chake… Yehova akutichenjeza & kutilalikira kudzera mChilengedwe chake..

  16. Many places are being visited by earthquakes, fire as well as flood, so that we may see that GOD’s judgement is @ hand.. Chofunika ndikuchita chifuniro chake… Yehova akutichenjeza & kutilalikira kudzera mChilengedwe chake..

  17. m sorry to all concerned families….God should see u during your hard times….WARNING…A escom chonde musapezerepo chifukwa apa..paja simusowa ponamila

  18. Uku ndi ku Limbe pomwe panadusa nsinje walimbe ndi pa bridge pomanga nsewu sanapapange bwino, pamenepa ndekuti limbe anasefukira

  19. God z so merciful. He does hear our cry. lets just come together and pray for our country. God z gonna hear us. kutukwanizana siphula chili chonse. know that mvula yidakali mawa udzakhala uli iwe. pepani kwanonse mwakhuzidwa ndi ma floods amenewa.

  20. ii chronicles 7 v 14 if my people who r called by my name will humble themselves n pray and i will hear from heaven and heal their land. so dont waste time pointing others mistakes. be careful n judging others. we all sinned n fall short of Gods glory. lets unite n pray 4 our land

  21. Nkhani Ya Ngozi Za Madzi Sizikugwirizana Ndi Zandale.Kodi Mudzasiya Liti Uchitsiru Anthu Okokoloka Nzeru Inu. Apa Palinso Kugwirizana Kwanji Ndi Andale?
    Yehova Anakupatsani Udindo Wosamalira Chilengedwe Koma Mukukanika Kusamala Nokha Ndiye Ndizimenezo Anthu Akutaya Zinthu Zofunika Mpaka Miyoyo Yawo. Pokha Pokha Anthu Ayambenso Kuchita Monga Mwa Udindo Wawo Ngozi Zachonchi Sizidzatha Ayi.
    Nonse Mwalumikizitsa Nkhaniyi Ndi Zandale Ndinu Nkhumba.

  22. PaFb simalo oti tizipangapo za ndale. YESANI kuchenjera polankhula. Tiyeni tisatukwane Chauta pamavuto alionse. Komanso mafloods sikuti kusonyeza kuti Malawi ndi Ochimwa pamanso pa Chauta, ayi. Iwenso ukulankhula zonyoza Malawi, Zikufikitsani kuti. Lekani Tiyeni tikonde Malawi. Zikomo.

  23. If not mistakeni, it was last week when we heard that Disaster what what Management was telling the nation that they are more than ready for floods or whatever. Just waiting to see them how they gonna help Bt and those in the Mzimba who affected by storm afew wks ago.

  24. kod zikugwilizana bwanji ndi ndale anthu mukunyoza why kod ndi amene agwetsa mvula mulungu dziko analilenga lokongola lelo taliwononga mmalo mosamala zabweletsa kusintha kwa nyengo tibwezeletse chilengedwe tisanayambe kutukwanana ndikumupempha ambuye atipase mvula yabwino coz ndi amene amagwesa mvula ma churh amkhala ndi anthu ambiri sakutengapo gawo lakuphunzitsa anthu za kusamala chilengedwe cha mulungu siwudindo wa boma lokha kapena mafumu chifukwa anthu onsewa amathanso kukumana ku church ndi njila imodzi yofunikila kwambiri kut tigwilizane a malawi pakubwezelesa chilengedwe chathu ma church asakomedwe ayi koma awathandizeso anthu za moyo wawo watsiku nditsiku thats christianity

  25. Ku malawi kwagwa vula yambiri yaononga zithu mukuti we have sin against God, ku south Africa vula siku bwela misinje yauma mi popi madzi sakutuluka akutiso its punishment from God. Eeee munthu alibedi pabwino.

  26. Did we take advantage of the 12 months since the last devastating flooding to heal our soil, plant trees, build swales, mulch our fields, build water harvesting tanks, dig banana pits, construct check dams, and diversify into seasonal cropping systems which include both water-loving species as well as drought-tolerant ones? Or, did we continue to cut down our trees, burn the landscape, hoe up vegetation, and ignore our compacted, depleted, and sun-baked soil just waiting for the rains to monocrop another wall-to-wall crop of chemically-dependent maize? Humans have a moral responsibility to be good stewards of the earth. When we learn how to care for our Mother, we quickly discover that she takes care of all our needs.

  27. Thank you almity God that you have given malawians water to drink in other countries there total flames of heat wave which is bringing disgrace and fear of their lives.

  28. Ndikamati namalenga sakugwilizana ndi ulamuliro wa ulipowu ndye muziletsa yetu amatha kulanga ana chifukwa chamakolo ndinena ndinu munasakha zolakwika inu

  29. Malawi blessed country no war no fighting God blessed us with rain don’t worry about floods this is a blessings

  30. even south Africa many people are homeless because of storm let us pray for them and wish them well because tomorrow it will be us or one member of our family. when people are affected by natural disasiters dondt mock even laugh them moto umayaka kumene kwasala tchire Mulungu akukuona.

  31. Change your profile and support MALAWI and the people of blantyre…. eyetu ndizomwe tikupanga amalawi kukopeka zanthu zayambapo apa

    1. r u forced to change ur profile?we hav done according to our choice.leave us kaya ndife otengeka kaya ayi that’s none of ur business.remember every 1 has his/her own choice.

    2. kkkkk zikakhala kwa zungu ndiye kumati tichinje profile koma kuphedwa kwa mafrika ndiyekosa onetsa solidality? West gate pa kenya,boko haram pa nigeria komaso alshababu pa somalia

    3. Its a flood. Not a terrorist attack during an immigration crisis. Dont be so full of yourself. When isis comes to malawi during an immigration crisis and shoots up your most important, multi cultural, and equal city killing 120 people. Come complain again

  32. Mvura ndizandale zikugwilizana bwanji? Penapake tamapumani ndiza ndale plz,kulephela kwa zipani zanu simathero azonse.pitilizani kulota mwina 2019 zizayenda,pepani ife omwe tidawasankha adawina ndiponso tikuyang,ana kusogolo for another victory,its very pain kuvotera chipani then chipanicho ndikuluza very shame.mvura ya dis year its ablessings for mlw nation u wil c end of aseason ppl wil harvest bumper yields mark my word.

  33. Imagine here in Bangwe people constructing the houses mphiri,mitengo were all depleted therefore the runing waters are demolishing houses on their way,fences are falling down.Its indeed pathetic,Escom ndiye atiuza chiani kaya.

  34. what does this have to do with DPP is dpp your God does dpp controls the rains, i think the one who accusing mbendera must be very stupid #climate-change havent you heard about this term koma ndekuti mumakhala kumashamba kwenikwenitu mukadali muumbuli

    1. i thought pipo who use fb are learned person but now aaaaahhhhhhhh pachuluka ana othawira pawindow ongodziwa #this_is_my_nose kkkkkkkkkkkkkk

  35. Komatu Odziwa zanyengo tilinao. Bt why??? this is to show that Gods Knowledge is mans he? Now I know. Malawi needs to humble urself b4 Almighty God. We hav sinned against God! We need to ask 4 forgivnes. Machimo afika kumapazi kwa Mlungu. Wakwiya. Tichitileni chifundo Yeheva.

  36. Dont blame rains but your poor engineered drainage System

  37. ooooo!Tatiyeni tiwone chimene chikumatsitsa dzaye kuti njovu zizithyoka minyanga tisangokhala chete.Mipingo tapemphelerani dziko lino chonde madzi asanafike mukhosi

  38. ‘Government is assuring Malawians that it is more than prepared to deal with El Nino effects’. Jeremiah Mphande, spokesperson for the Department of Disaster and Preparedness said in an interview (Nyasa Times November 12, 2015)

  39. Dziko lathu la malawi linadzadza ndi mbuli dzokha dzokha nabiliva ine sure kugwa kwa mvula pali chifukwa chozondera achipani apa.??? Kkkkkk zikang’a zanu mwamva.??

    1. .#Symon,uziyankhula mwanzeru komaso mozindikila,ukati ziko la Malawi linazaza mbuli zokhazokha ndekuti iweoso ndi mbuli mapeto pamozi ndi achibale ako ose coz u r also a Malawian,check ur mouth b4 comenting!

  40. Wait a minute… I find this reporting to be sensational. Heavy flooding…really? Let’s be careful how we report please. This one is a haven storm which has brought flash floods…, please please let’s inform people in the right way!!!!

    1. kkkkkkk. ..flash??????..i hope u will change ur statement to floods after being a victim…..just wait mesa zangoyamba..

    2. Well, the trajectory of reporting then should state what is the state of affairs now; when it comes to the HEAVY FLOOD level, then the reporting should state so. I’m not seeing my statement changing really after the fact, it will have been so anyway. In any case, I think it was more significant to report about the devastating storm than the water flowing because of poor engineering in Limbe. The many houses that have had their roofs blown away, not washed away, should have been the center of the story. But I’m not a journalist anyway

    1. What does dpp have anything to do with floods. Thats the problem with you people, first ones to blame someone else. When you are part of the problem. Did we take advantage of the 12 months since the last devastating flooding to heal our soil, plant trees, build swales, mulch our fields, build water harvesting tanks, dig banana pits, construct check dams, and diversify into seasonal cropping systems which include both water-loving species as well as drought-tolerant ones? Or, did we continue to cut down our trees, burn the landscape, hoe up vegetation, and ignore our compacted, depleted, and sun-baked soil just waiting for the rains to monocrop another wall-to-wall crop of chemically-dependent maize? Humans have a moral responsibility to be good stewards of the earth. When we learn how to care for our Mother, we quickly discover that she takes care of all our needs.

    2. Lonjezo Bande, your msg is clear but put it in local language for the masses to understand the situation on the ground.

    1. Ndikukonzeko pang’ono galu iwe, unene kuti pepani bambo anga and then upitilize zakuthako zakozo, mwana opusa onyoza bambo ake iwe but the problem its not you but you fucken bitch-mum thats a problem #fuckYou

    2. Iwe azungu after ma floods amakhala mabwana koma ife a Malawi after ma floods ndi umphawi okhaokha basi amene amalemera ndi kumipandoko basi chifukwa cha thandizo lomwe limabwera kuchokera kunja

    3. Mulungu amalangiratu munthu opanga zosayenera ali moyo, ndikukuuzani ndipo zikutengerani nthawi kuti muzindikire chimene ndikunena, Mulungu akulanga Malawi ndipo akanalanga, ndabadwira ku Malawi ndakulira ku Malawi koma phazi langa silidzapondanso Malawi kamba ka ulamuliro wadyera omwe uli m’dziko la Malawi. Koma popeza agalu ndi agalu basi mukhala mukuimbira m’manja agalu omwe akukulamuliraniwa mpakana mudzafa. Zitsiru

    4. Iwe galu iwe za ine amakamba ndi anthu kuti ndiyambe kukamba ndekha uona ngati ndikunyada, ndipo oloko Mulungu atangopserezeratu Malawi sangalakwitse a Malawi akuvutika kwabasi, wamva mwana wa hule iwe, nanga kuti udye amako achinditse ndiye kuti pali nzeru!!

    5. Iwe ndi manyi eni eni,zoona ukumanyoza kunyumba kwanu chifukwa kwa a neghbour mwadyera nkhuku yomwe kwanu simumayiona?ukumanyadira dziko la eni kunena kut kwanu kuno suzaponda phanzi?iwe ndi ine lero uzandifunse ngat chaka chikuthere kumeneko.amayi,abambo,ana ndi ambwiyako zikang’ka zili tho! ndiponyera pomwe,koma iwe osawathandiza,umvekere mbendere…fyotokufyoku….undilankhulitsa pa mbali,ndikanakhala kut til live i swear ndikanakupambaza.Chifiti,chopanda nzeru,buluzi,panyak ndikambi kuti busu lenekuleneku……

    6. bt to sae the truth adzathu a ku joni awa kawiri kawiri mitu yao siyigwira bwino ntchito ndaonera mbudxi yomwe mwayimangirira apa iyi how can someone anyoze dziko la kwao chosecho amayi ake akuvutika ndi bonya uko am a broad of course bt i can’t compare any country with malawi hw can i i love malawi zandikhudxa kwambiri

    7. Zili m’Baibulo kut Mulungu adzalanga Malawi? Jon ngakhale yatentha anthu kupha kuisiya malawi ndye yolakwitsitsa. The Bible says we’r living in the last days Mathews chpt 7; chpt 24 not only in malawi bt the whole world.

    8. Chancy pokhalira pa amai ako wamva!! Am not staying in RSA, iweyo ngati watopa nawo umphawi ndi abonya akowo zako izo, ndanena kale kuti zaine amanena ndi anthu ena ndimakana zomati ndikukulalatirani akapolo a Malawi ngati inu, kumavutika koma ndikumaona ngati mukusangalala. Malawi still on fire from now until God’s judgement day

    9. When u argue with afool people wl not see the difference ,they wl regard you both as fools.my fellow poor malawians you can leave this guy he won’t help us in anyway.nokha mutha kuona mmene akuyalukila apa do u thnk he is well to do?arich man has self respect aswell as respect for other people.yes he might be abroad koma mwina akugwilakn magobo uko.kuvutika chimodzi modzi bolanso ife….Lets Join hands and pray for our country..lets not argue with this good for nothing.ntchto zolemetsa zamukwana akufuna aphwesele zakezo pamenepa.

    10. Lamwa, zaine amakamb ndi anthu, ndipo kuti ndizichedwa nawe ndikukufotokozera zaine ukhoza kuona ngati Mulungu amakonda ine ndekha ndipo iweyo ndiwe bonus ya anthu padziko lapansi lino, kungoti nanga si amphawinu munthu akangonena yekha m’mene iye aliri mumati akunyada ndiye ine ndimakana dzina lonyadalo, ngati uli ku Malawi dziwa kuti ndiwe kapolo wa akapolo onse padziko lapansi. Mbuzi ya munthu @Lamwa

Comments are closed.