Malawians will not starve- ADMARC

66
ADMARC

Maize is enough at ADMARC depots.

With 2.8 million people in the country expected to face hunger this year, the Agricultural Development Corporation of Malawi (ADMARC) has assured Malawians that it has enough food to feed people in the country.

“We have 55 metric tonnes of maize of which 30 thousand tonnes was bought from Zambia whilst the other 25 thousand tonnes were accessed locally,” said spokesperson for ADMARC Agness Ndovi.

Ndovi added that the corporation has distributed maize to various depots throughout the country in order to maintain price.

“At the moment we are distributing maize in small market outlets of the country through our main markets,” she said.

Ndovi has since asked ADMARC staff to always alert the cooperation whenever maize is not available in their depots.

Share.

66 Comments

 1. Ngati Kuli 2.8 milion tones, bwanji ku Gawanani admark ku machinga anabweletsa 90 bags yokha? ndikutha isanakwane 10 koloko? mukunamiza ndani?

 2. Ndili ndichisoni pomva izi chifukwa ku admarc chikabwera chimanga akugura ndima venda ndpo truck yomwe yanyamura chimangacho sifika komwe amakachisitsa kwina ndpo ineyo maumboni alipo maka kumachinga nde zanyanya

 3. I would rather they starve a bit. They should know that stealing, corruption, overfishing, overpopulation, and all the other things malawians do have consicueses . Aziwe kuti mukaba ndalama, mukasiya sukulu muzavutika. Palibe atagawe chimanga. No country does that. Amalawi aphunzire kuganizila za kutsogolo, and know the consicueses of what they are doing on the present day.

 4. Amalawi ndalama zogulira chimanga azitenga kuti popeza bwana pita anasakazira ulendo waku usa? Ngati azigawa chaulere ndiyekuti sitivutika.

 5. Mmalo muti muzizazisa madepot akumizi mvula isanayambe mkukhalira kuzitama. Nde mvula ikayamba magalimoto yazapitisa chimanga kumadepot akumizi. Azikaunjikana mmadepot amtauni ngat kwawu kulibe Admarc. Zitsiru.

  Chimodzimodzi mene amapangira feteleza wamacoupon. Pali ali phee koma akudziwa zoti mvula ikubwera. Nde azizanamizira mvula. Makhuluku amenewa. Zitsirunso

 6. chimanga chombwera dzulo kuyamba kugulitsa lelo kutheratu ndiye. akumakhala ma tones angati?so should we trust u , kapena akumagula ndi ma vendor tifatu kuno!!!

 7. Tumizani chimanga chambiri mmaADMARC kuti anthu asavutike osamangolengeza kuti tilinchimanga chochuluka pamene mukumabweretsa chochepa,revisit ur systems

 8. Horses starve while grass grows so too Malawians are starv’n while d silos ar full with d grain,ADMARC is 4 vendors not 4 poor village pple.U sayin Malawians will not starve while d ar already starv’n.

 9. How are you going to feed them? Are you going to go village to village and house to house to see if the people have food? You’ve got a humongous task on your hand if you don’t want the people of Malawi to starve.

 10. amangwetu!!okana 20Kg ali ndi chimanga chambiri ameneyo,kuti ugone nayo,ndikuti ugule 20kg chabwino ndichani.kupita ku admarc ukapeza chimzere chaanthu kufuna 20kg-yo. #as_for_me_im_flapping_my_gums.
  #DPP_ADMARC_WOOOOOOOOOOOOOYEEEEEEEEEEEEEEEEEEEE

 11. Ndakwia nanu 20kg inu ophutsa ndikumakwela muthengo kulengeza mithu ngati ziboliboli
  ……makhamakha amene wayambitsa ndikufuna ……..nditango menya ……Rivekere dzikolotse woooooooo……Nchibagela.kuti….
  Tii? mano……onse out kulibe

 12. Bola Kumachitumiza Kumalo Ofunikirawo.Osati Tidzizamva Kuti Chimanga Chaola Mma Silos Pomwe Mma Shed Ammudzi Mulibe Chimangacho.Yambiranithu Kumachitumika Mfuna Mvula Ibwele Nde Mziti Misewu Yaonongeka Sitingafikire Mmadela Akumidzi.

 13. Ndi zoonadi chimanga chiliko ku Admarc, koma akumagula ndi mavenda pamtengo wa K6000 m’malo mwa mtengo ovomerezeka wa K5500.

  Amene muli ndi number ya ACB, tipatseniko kuti tiwatsineko khutu pa zomwe ma buyer akuganga pogulitsa chimanga.

 14. “Malawians will not starve?” Malawians starve even if admarc’s silos are full with maize. At least if you said the price of maize will drop not at your sky rocketing prices. Actually your prices are saying “there is nothing for the poor”.