Demos against Government set for tomorrow

Billy Mayaya
Billy Mayaya
Mayaya: Demos on tomorrow.

The Lilongwe City Council in Malawi’s capital has given human rights activists a go ahead to hold demonstrations tomorrow, Tuesday, 27 October 2015, Malawi24 has learnt.

According to a post on Facebook by Billy Mayaya, the demos are slated in a bid to demand good governance and improved service delivery in the health sector.

This follows incessant reports that Malawi24 has also been carrying about miscellaneous economic woes and lack of resources to man hospitals in the country.

For example, Machinga hospital has fallen short f food such that patients’s daily meals got reduced, a development that has also hit Mzimba hospital.

Reports say the activists also want President Peter Mutharika to address various governance issues including the recent controversial trip to the United Nations General Assembly (UNGA).

According to Mayaya, the demonstrators will converge at Parliament roundabout at 700 am.

“From there we shall proceed to the Capital Hotel roundabout make a uturn and proceed to the traffic lights turn left to the civic offices where a petition will be read and delivered.” Mayaya wrote on his Facebook profile.

The demos will see all people dress red or black.

The last time pressure groups was in January this year, protests which were driven by the controversial financial scandal at the National Aids Commission (NAC), a scandal christened Nacgate.

The demos were however marred by low turn out due to heavy rains that hit the country.

Advertisement

341 Comments

 1. i don’t like politics,but concening about this issue called demons… i have to step in ‘n’ say something.demonslations demonsla ……………… anthu inu mulibe nzelu simukukumbukila kuti azanu anataya miyoyo chifukwa chama demons… Pezani solution ina yothesela mavuto osati such nosense soluton.

 2. lets remember the death of victims people who died on 20 july…lets my relative am not apolician jst wana advice,u wil start and ending loosing lives of people later u wil say that govt has killd people…its ur choice doing or nt but thnk twice.

 3. Winayu amakhala fodya, Billy Mayaya mukuyang’ana anthu oti akafe basi, aja apa 20 july sadakwane??? Ine zanga phee kudya Nsima pa den mukamaliza munena, muzipanga tsikunditsiku hop mankhwalawo muwapedza!!

 4. sindiri mbali ina iliyonse koma nkhani ndi yakuti, akuluakulu tisaiwale zomwe zidalembedwa kapena kutsindikizidwa kwa mau m’mbaibulo kuti matsiku otsiriza ogula sadzakondwa nde mavuto sadati ndipo akubwera oposa amene tikukumana nawo lerowa chofunika ndi kuziyang’anira wekha ndi moyo wako kuti uli bwanji ndi Mulungu wako, chifukwa zinazi ndi zopweteketsa mutu komano mau a Mulungu amatonthoza. Popanda mavuto pa dziko lapansi nde kuti Yesu sangabwerenso ayi.

 5. Amayaya pezani chochita cha nzeru,muputsa nazo izi,wona wakalamba

 6. Malawi gained independence in 1964,bt still remains the poorest country.Rich countries hve bn helping Malawi since then,bt still no change.The money that Malawi gets 4rm doners does not help 2 build Malawi,rather it helps 2 build greedy and selfish so called top bwanas in government.That money wz supposed 2b used 4 building institutions and infrastructures.Your demos wl do nothng 2 change Malawi,it wl jst worsen the situation.Plz stop playing blame games it wl jst waist our tym.You olwys find fault wth evryone,even if we choose u 2b the president,these problems wl still b there.If u got nothing gud 2 sei abt someone u betta kip quite.

 7. Tisaopyezane pano akati madem sikuba kapena kuononga katundu ai, komaso osati kuomberana ai, ku madem saumilizana osafuna asapite ofuna apite, zonse zimatengera ndi mene ukuzionera zinthu zikuyendera.

 8. Otsamurekerera president opanda chifundo ngatiameneyo komanso amalawi taziona zotoreratora mumati wabwinondiameneyo timakuudzani kuti ameneyo tsimmalawi ndimunthu wakunja mmakana makamaka adzathu akumwera mwaziwonela nokhananga mutengerepo phudzilo ndingakondwere zikanakhala ngati 2012 dzikamchitikilanso naye kutiamene alikowo nawonso atengerepo phudzilo

 9. Amene ali ndi nthawi apite. Ine ndangokhala busy ndikanapita. Mbuzi imeneyi ingotula pansi udindo. Dziko lathu likufuna munthu oti athandize anthu osati azikalipira anthu ovutika mpaka kumenya tebulo?? Bigup mayaya, I think ku malawi kuno kukufunika anthu olimba ntima ngati inuyo kuti zinthu ziziyenda bwino.

  I understand pa july pipo were killed but that is not a an excuse to hinder good governance, Demonstrations will be there for lyf. Even it means ineyo dying for the innocent malawians koma they shd benefit at the end

 10. kodi mumasangalala anthu ena akamataya miyoyo yawo?oyambitsa mademostrations sakapezekako akhala ali kunyumba kwake ndiye ndi mtsogoleri otani ameneyo musathetse mtundu wa amalawi tinazolowera kuvutika ife

 11. inu ofuna kupita ku ma Demo just go don’t persued others to join you since to them the Idea is not Ideal;As for you who dont want to go fro Demostration reamin quet don’t talk much or dont persued those who want to go to stop going…we r n Democracy where by we r free to participate mma Demo but if nt intelested to join simulanduso …so just let it go…..

 12. Mbuli zili paliponse guyz maso alinawo koma sawona palibe nthawi yolimbana ndi demo apa omwe anatenga gawo la chuma cha ziko lathu mukuwazi ndipo mumawazi koma mukuti timatche ngati akutuman mukawauze kuti ati mutipwetekesa thphedwa ndizinthu zopanda ntchito ngatinso ulindiulesi

 13. Hello…… We are a lovely family from United Kingdom and we are here looking for a serious worker in our home and in our hotel like a serious Driver,Nanny,Housekeeper,Home Nurse,Private Teacher,Security,Au Pair, Waiter,Manager and so many worker like that are needed in our home and our company needed urgently. If you are interested in our job offer and kindly contact us directly to our email contact address…… [email protected] so that we can tell you what to do next on how you can come over here and process all your traveling document to come over here. Hope to hear from you soon.

 14. Dziko akuliononga ndi eni akumipando tangoganizani zambia sakaniza anthu kugula zakunja pano zambia latukuka kuposa malawi chifukwa chozikonda amai ambiri amakaoda zitenje kma akupeza mavuto pa boarder malo moti anthu akamatenga katundu wakwina zinthu zimaenda bwino ndalama zimapezel bwanji congo dziko loti akulandira katundu wamaiko ena pano ndalama alinao nanga ife kadziko kake kameneka malamulo thon wakumseu basi tikufuna ma bisnes anthu aziyenda osati zomativutitsa pa boarder nanga tikamakwatirana akazi okha okha tiberekanso ngati?

 15. I used to respect mr mayaya but I was wrong, where were you when the jet was sold, when the maize was taken and the government claimed the maize got rotten, and most importantly during cashgate!!! Don’t waste our time Mr mayaya,ok!!!

 16. kupita ku school sikuti uzakhale bwana kokha komaso kuka chosa umbuli nde zikuchita kuwonetselatu kuti simudapite ku school poti amati ukamalimbana ndichitsilu naweso umakhala chitsilu nde tikusiyeni poti ndinu zitsi lu pitani moyo simuwukufuna

 17. First Ov All Mayaya Atenge His Son/dota Up Front Then His Wife Beside His Grand Pa/ma Osat Ife Tipite While The Above Mentioned Subjects R Enjoying La Mkaka Ndi Uchi Ali Khuuuma Mminyofunyofu Yonga akhala Pa Madzi. Failing Which Buckoff!

 18. Demonstrations are not a bad gesture dear Malawians, the only bad thing is that we have misinterpreted them for violence,shoplifting and all sorts of immoral act, so in return, we get killed, th CSO could have find better ways of negotiating with the government. people today are afraid of demos, not because they do not want to, but simply because they do not want to risk their life, we are afraid oc HISTORY REPEATING ITSELF(2011,20 JULY). let the CSO learn the value of Diplomacy and the skill of advocation n negotiation in sensitive issues like these.

 19. Ngakhale tili ku GP nafenso tipanga nawo poti zimene akupanga Peter zatikwana. Timaganiza kuti mwina mmmm koma ayi it’s too much

 20. Demos are part of democratic life.Even the president isn’t against this.If you hate them,then go back one party state or join Islamic states.

 21. forget about a gun,demostrations its not about fighting with government you stupid people, let piter hear what people think!,,,,,,its free world remember

 22. Billy Mayaye ngati pakhesedwe mwadzi mawa lino ndinthu uzakhara pa mutu pako,amalawi ife imkutiyesa chani phindu la ma demo pa malawi pano sindimaliona kupatula kubedwa kwa ma shop kutentha nyumba za a police komanso kuphedwa kwa anthu mmmm billy mayaya uzayakha

  ine ndale sindipanga ndipo nthawi ndilibe

  A malawi chonde chonde lekani kulota

  byee

 23. Ma Demo achiani? Za ziii. Mwasowa chochita eti. Inu a Mayaya muli president mingathe kulamulira inu? Kuyendesa boma muyesa ndi masewera eti. Amalawi ifetu tinachenjera sitingothamangira zilizonse. Uyenda wekha uwona.

 24. Zomwe ndimadabwa ine ndizoti,mmalo mokatula nkhawa zathu kuboma timalimbana ndikuthyola mashop,ndikumaotcha mateyala mumseu,kodi mashop ndi miseu ndizomwe zikuchitisa kuti zinthu zisamaende bwino mziko muno?Ine nde simundionako kumeneko

 25. Kkk John iwe kutumiza uthenga kwa ena iwe osapita wekha bwanji?ukuopa Chan ?i gues the solution is to pray than demonstrations,where is Malawi going ?

 26. Something will change after Demo, osamakhala ndi mantha ngati akwangwalayi ndipo ambiri amene akususana nazo ndi a Dipwipwi onyamula pic ya president komanso ovala zojambula chimanga kunsana koma akuyendera ufa wa walkman daily ndipo sangakondwe nazo zimenezi poti ndi chipani chawo chili Boma,, ngakhale chikuwazuza,, inde tilipamavuto osowa ndalama koma atsogoleri akumawononga ndalama mwadala monga “kunyamulana ulendo kwa America chigulu cha anthu opanda chokachitako”,, ndikumva kuti Boma lagula galimoto 4 zokwana k300 million zongokwera anthu owerengeka amene alinazo kale. Bwanji ndalama zimenezo kuyika ku subsidy program kuti anthu osauka apindule nawo mkuti panopa mwalandila makoponi ndipo ndi angati chaka chino? Poti nthawi yatha, Njala ya mphweeee! Ilikonso chaka cha mmawa,,nde ngati pali njira yolitutumusa Boma ndi ma Demo zovuta ndi zambiri zoyenera kuti Boma lipange komanso lisithe,,,,,

  1. Ine Ndi Wa M C P Koma Ndati Ndisuse Ku,izi Zomwe Achita Abilly Mzosamanga Malawi Ngati Dziko Pamodzi!! Kodi Adali Kuti Pamene Awa Amzathu A Dpp Ankatenga Boma.. Ngati Ndi Ukadaulo Womwe Ali Nawo Wolamulira Sadaime Nawo Bwanji?! Ife Ngat M C P Sitizalora Kuti Wena Atiputsise,tigwira Limodzi Ndi Boma Ngati Chipani Posatengera Zabwino Zomwe Achitira Speaker Wathu.. Ndimati Ndipemphe Kuti Uyu Puluziyu Nkuti Mayaya Asakusocheleseni!!

 27. this is very retroprogressive,why on streets and leaving work behind?have demos ever been fruitful before?mayaya,dont waste our time.shut up ur mouth!

 28. I totally support the demonstration so that change can prevail rather than just seeing things falling apart.Some are saying those who want to demonstrate are against the government,i don’t agree just coz what they want is that the govt shud always be conciuos when doing its business and not just mere rhetoric so lets all pliz work with one goal to promote democracy and development.

 29. Kodi Gulu La Achina Billy Mayaya Osayambisa Chipani Chawo Bwanji?! Ndikuzapikisananawo Pa Chisankho 2019 Ndikubweresa Kusintha Muno If They Think The Have Pontetial!!! Boma Lilonse Basi Alongolole For Nothing?! Axatiphere Anthu Chifukwa Chomenyera Ufulu.. Amzawo Omenyera Ufulu Anamwalira Kalekale Iwo Ngati Alimunthudi Womenyera Ufulu Bwanji Xasowa Kuti Tizawakumbuke!!!?! Zaziiii

 30. Kodi amabungwe mavutowo mwawona mu ulamulilo wa DPP basi? Nthawi ya PP munapangapo chani poti ndalama zathu za misokho anthu anayika matumba mwawo palibe chomwe munapanga zopusa basi, musamatitenge ngati sitimaganizo inu wofoyila pitani nawonu uku ma Demo anuwo musatinyasa nawo mwamva

 31. Ma demo ma demo chani apa? Tinawona ma demo ife pa 20 july. Kuyamba ndi kumaliza kwa ma demo kunali komweko. Awa ndimacheza kusowa zochita. Pitani mundipeza.

 32. Kodi mavuto akukupitisani Ku nseu ndi oti chani. Ngati ndalama ulibe ndibwino kugwira ntchito mmalo motaya nthawi kulimbana ndi boma.

 33. billy mayaya ndi john kapito asamatipusise coz kumbaliko amamwera chikho limozi pa ichi mademo sangathandize kusintha zinthu

 34. Akusowa chochita amene alinazo bizewo. Tikumangomvutika ndikumvota palibe kusintha. Ma presedent onse palibe yemwe anapanga zofuna anthu dziko muno. Opanga ma demo asiyeni angozuza moyo wawo, kungozimvomeleza, ngakhale atabwera presedent wina simuzaona kusintha.

 35. Mizimu mnathila nsembe thawi ija yasiya kugwila ntchito pano mufuna ina shupiti katengeni ana ambuyanu
  A reason person amapita Ku ntchito
  ma satanic inu
  Thawi ya cash gate simunathamange msewu bwanji
  kawuzeni akutumaniwo kuti mlungu akuwenelani zomwe mupanga

 36. osamangoti mademo chosecho mkufuna kuphyanya achopu shoot 2 kill igwire tchito apolice anthuwa ndiakuba akufuna akhare mahiro kumanda

 37. Ngati pa 20july panamwalilanso anthu 20afterwards chimene chinasinthapo ndi chani ?mutengerepo phunziro kuti palibe amene angasithe ganizo la president kumalawi kuno kunja ndidzotheka.

 38. Amalawi kupusa! Anzathu ku zambia zithu zavutanso ayang’ana kwa Mulungu Namalenga, ife tikuti mademo, tipindula chian? Pali nzeru apa? Inuyo ma big amademonu bwanji osabweresa solution yoti dzikoli liyende bwino? Musavutike this z signs of de tym! Mwana wa Mulungu watsala pang’ono kubwera, tieni tikonze mjira zathu zoipa kuti adzatipeze tili oyera!

 39. What If Malawi Should Rise In Production And Export,can We Suffure These Things Any More? No For Sure,ndiyeno Amalawi Tiyeni Aliyex Angolingalira Njira Yoti Apeze Money Yochuluka Zose Zisitha “but This Can Happen Only If We See The Vanity Or We Make Our Mind 2 Change Our Daily Life Expirience,what If We Sit And Discuss How We Can Make Money Thawi Yama Demoyo,komaso Trust In God Who Send His Only Son,he Never Fails!!!!!

 40. I am here to report dead people to BBC world TV tomorrow. Kafeni bwino komaso wa Mway I we, bwerako bwino ndi katundu obedwayo. Amavutika ndi amalawiso omwe akupanga timabizinesi. Tsoka ukugulisira mtawuniwe, Chifukwa mawa mpamba wonse utha in the name of demonstrations. Bwanji osapita ku state house komweko?

 41. Zamanyazitu izi coz ine sindimadziwa kuti mawa kuli ma demo!!
  Angapiteyo ndie kuti alibe chochita ndithu!!!!!
  Tieni a Malawi timuthandize president wathu kupeza njira zothana ndi mavutowa kusiyana ndi umbuli ukufuna kuchitika mawawu!!!!!!!!!

  1. ukamat pulezidenti wathu kt chani stupit…uziti pulezidenti wa mako aja ankakhala ku bala aja asakuona kuvutika ndikukweredwa ndi amuna osiyana ndie munangozolowera nanga bambo anu muma waziwa inu foolish!!

  2. u r very stupid…..ukuganiza kut ma ideas a ine waku grassroot akafika bwnj kwa iyeyo APM wa2yu…i mean timuthandiza bwnj….by the way ali ndi cabinet yake yomuthandiza…….jst go to hell with ur primitive ideas….mesa mumakondwa amalawi tikamavutika….mxieew….

  3. u have to think b4 write ua coment,aZanu ku south afrca amagwirana manja ndikupanga protest zinthu zimasitha taona last wk za mafee aku university sizintheka kapenatu inu zikukuyendelani eti wake up and stand up 4ua country mr gerlad mavuto

  4. Limbikira kugwira ntchito ndiponso azikudula msonkho wambiri mapeto ake uzafe mphawi pamene msonkho wakowo akugulira ma galimoto a 400 million. Do you call that kukonda ziko. Tiyeni titseguke mmaso a malawi. Inapita nthawi yongokonda muthu coz ndiwakwathu. Lets start reasoning with our little brains

 42. my fellow youth members don’t join that shirt coz u will fall in troublistic and terrible life and u will behorsted

 43. Mavotavota awa akuononga dziko, munthu wogwira ntchito za u gay angakhale ndi mzimu wabwino woti nkuyendetsa dziko bwino. Agubilidwe ameneyo awonekere poyera kuti ndi wolephera.

 44. Mantha sapezetsa zabwino, zionetsero ndi zabwino tiyeni tonse tikagwirane manja pitalayo adziwe kuti adavoteredwa ndi anthu, akaziwe uchitsiru wake. Zonse izi ndi mavotavota opanda pake.

 45. I think billy is a #mmmmm#. Do u want cheap fame? Malawians know that u ve been bought to organise that. Ok, go ahead wth the nosense demos coz u say its ur freedom. But if u and ur sympathisers bring chaos, the guns are ready to go blazing!

 46. Azeru akuwoneka pomwepa wopandaso zeruso aluwoneka. Amalawi tisarore kuti tiwononge ziko chifukwa chamantha, tizakhala tikupanga zimenezi mupaka nariti?

 47. Azeru akuwoneka pomwepa wopandaso zeruso aluwoneka. Amalawi tisarore kuti tiwononge ziko chifukwa chamantha, tizakhala tikupanga zimenezi mupaka nariti?

 48. Amene anabadwa ngati munthu sapita nawo kukaguba nzoona tisiye ntchito zathu tikagube eti peter achoke.Bwanji tifunse amene tinamuvotera kuti munthu wathu ali bwanji?

 49. Mukufuna kuphanso anthu ngati mmene munachi masiku ammbuyomu,apa mukukaniza kuti ma demo ayi ndi cholinga choti anthu akachita mudziti amphwanya malamulo ,kodi ufulu wa anthu amenewa uli kuti dude motherfucker kodi akati Malawi ndi inu nokha kapena ndi wa inu ndi ine

 50. Mwayiwala abale adafa 2011? Analitu a Mayaya omwewo akayenda. Why kulimbana ndi Mamutharikas only? Mudali kt nthawi ya amayi ndalama zikangobedwa ngati mango muja? Mayaya munthu opusa zedi galu okonda ndalama chidude chamunthu

 51. May the good Lord, God of our forefathers,God of Abraham, Isaac & Jacob, my God, forgive this so called Billy Mayaya..& aliyense behind this kind of thinking..! kupanga ma Demo nkosaletsedwa ngati atakhala kuti is done in good faith (which is not the case here!) Ndakhala pa ka nthawi ndisanatuluke kunja kwa dziko lino kotero kuti sindinamvepo kuti a Billy Mayaya akonza zokambirana ndi boma kuti apeze solution ya mavuto amene tikukumana nawo ngati dziko, sindnamveponso kuti a Billy Mayaya alepherana kumvana ndi boma ndiye achita involve amipingo kuti akhale nkhala pakati..! yes, ndi udindo wa boma kuonetsetsa kuti aMalawife tiri ndi zofunikira mmoyo wathu eg. chokudya,madzi,mankhwala etc komano sindinamvepo kuti a Billy Mayaya ngati Mmalawi akonza ulendo wandawala pofuna kupeza ndalama zogulira mankhwala ndi chakudya ma patient achimodzi mwa zipatala za m’dziko muno. Mbanja mmodzi akalakwa ankhonswe a olakwayo samapita kwa olakwilidwayo mkumakamuwuza zoyipa zokha zokha za olakwayo koma mmalo mwake amakankumbutsakonso olakwiridwayo mbali ina yabwino ya olakwayo ndikumpepetsela olakwayo.. ine sindinamvepo kuti a Billy Mayaya ngati munthu okonda Malawi akagwada kwa ma Donors kuti atipatse second chance. Ndiye kuti bomali palibe chabwino linachitapo mbali ina coz sindinamvepo a Billy Mayaya akuyamikirapo boma! Pena ndikumadzifunsa kuti ma CSO enawa ndi zipani zotsutsa boma zinazi anthu ake ndi a Malawidi? Ndichifukwa chani amakondwela ndi njira zophwasula than kumanga Malawi ? in “Billy Mayaya’s wisdom” ma Demo is the solution!

 52. paja apolice awagulira zida zatsopano2…ndye kuli ma bomba a nuclear,teargas watsabola uja…mmmm bola ndkafele pamunda mawa!..mbava zonse panseu koma half wammanda agulu.

 53. Kugona kwambiri amalawi maiko ena zomwe zapangidwa akuchita atsogoliri akunozi apanga ma demo mpaka zithu zasitha koma siife amalawi kupusa ngati nsima yotsala dzulo fotseki tidzagalamuka liti ife okhala mzika za dziko kumakhala ndi mantha dziko lathu lomwe oooooooooooooooooo! Mudzionera ma dstv plz zomwe akuchita maiko anzathu pakusagwirizana ndi zinthu ngati izi.

  1. Iweo odzukawe pita! uzatipeza! ngati kuli kusauka osamangolimbika maganyu bwanj? ukutengera zapa dstv? ali ndma dstv ndiangat ndipo akaonera apindura chan? Amnzanu mnzeru zkachuluka amayambtsa chpani chao ndkusapikisana nao pazisankho? we voted for APM and he is in power ife tikumuvetsetsatu.. what are you up to? you thnk Malawi is a playing ground wth stupid people dat tizipanga mademo chfukwa cha Billy Mayaya?? who or what is he? If u dnt lyk APM koma he is your Leader basi!

  2. Pitani mukawapangire chumacho a mayayawo! kodi demo imeneyotu ndi fund raising yawotu ngati simukudziwa! onse amene mulibe zochita tiyeni nazoni. watulo aoneka konkonso.

  3. demo singabwezeretse ndalama za cashgate. nde poti mavutowa akuti gwero lake nlimenelo choncho pitani a Mayaya alemere. Kuchenjera kwina ngati ngumbi zongotsatira kuwala kulikonse osadzwiwa kuti akawadya kumeneko.

  4. Kumeneko Ndiye Kusowa Mfundoko Mmalo Mofufuza Njila Zothesela Mavutowa Chilichonse Tizingoti Cashgate.Hahaa ndataya nanu chikhulupililo.

 54. Zopusa mwasowa chochita a2 14million apange zofuna aliyese? M C P mumat misokho U D F umbava kuchuluka D P P(bingu) kwacha wasowa DDP second tme mwayambatso chomwe mungaziwe palibe okomera a2 onse

 55. Am not a politician but NGOs which president do u want?kapito anavuta nthawi ya bingu atabwera JB anavutaso ndiye sopano mkut uyu achoke mkufuna ndan? Why Malawi is struggling its bcoz of cashgate,JB is woman but she is not suppose to b in politics

 56. May the good Lord, God of our forefathers,God of Abraham, Isaac & Jacob, my God, forgive this so called Billy Mayaya..& aliyense behind this kind of thinking..! kupanga ma Demo nkosaletsedwa ngati atakhala kuti is done in good faith (which is not the case here!) Ndakhala pa ka nthawi ndisanatuluke kunja kwa dziko lino kotero kuti sindinamvepo kuti a Billy Mayaya akonza zokambirana ndi boma kuti apeze solution ya mavuto amene tikukumana nawo ngati dziko, sindnamveponso kuti a Billy Mayaya alepherana kumvana ndi boma ndiye achita involve amipingo kuti akhale nkhala pakati..! yes, ndi udindo wa boma kuonetsetsa kuti aMalawife tiri ndi zofunikira mmoyo wathu eg. chokudya,madzi,mankhwala etc komano sindinamvepo kuti a Billy Mayaya ngati Mmalawi akonza ulendo wandawala pofuna kupeza ndalama zogulira mankhwala ndi chakudya ma patient achimodzi mwa zipatala za m’dziko muno. Mbanja mmodzi akalakwa ankhonswe a olakwayo samapita kwa olakwilidwayo mkumakamuwuza zoyipa zokha zokha za olakwayo koma mmalo mwake amakankumbutsakonso olakwiridwayo mbali ina yabwino ya olakwayo ndikumpepetsela olakwayo.. ine sindinamvepo kuti a Billy Mayaya ngati munthu okonda Malawi akagwada kwa ma Donors kuti atipatse second chance. Ndiye kuti bomali palibe chabwino linachitapo mbali ina coz sindinamvepo a Billy Mayaya akuyamikirapo boma! Pena ndikumadzifunsa kuti ma CSO enawa ndi zipani zotsutsa boma zinazi anthu ake ndi a Malawidi? Ndichifukwa chani amakondwela ndi njira zophwasula than kumanga Malawi ? Lero ndikamamva kuti in “Billy Mayaya’s wisdom..” ma Demo is the solution.. ndichifukwa chake ndagwada kupempha Ambuye kuti achilitse ndikudalitsa dziko lathu la Malawi komanso awakhululukire a Billy Mayaya..!

 57. Mwadya zonona uko mwakhuta. Then calling hungry people to join you. Akakayamba ku phwanya ma store a eni ake. Be ready to answer. Though some how idont understand. Do you think doing demonstration is asolution? Ithought you have got a btter ideas to solve malawis crises. Dialogue, ithink can help you yield fruitful results. Koma zinazi palibe chomwe zipindule.

  1. Brother Romesy!, demonstrations r not solutions indeed & u r right!! Bt question might b “Y pple com up with such point?” Ine ndimayesa kodi timaenera kutero kuti mtsogoleri azidwziwa pamene zinthu zisakuyenda? Iwe ukuonapo bwanji pamenepa!!!!

  2. Dziwansotu kt anzathu ku SA akumapanga mademo kaamba ka zina mwa ngati zomwe zikuchitikazi! Do u think that they dont knw the solution of dialogue? So, Y did they demostrate!!?

 58. Haha….poor malawians really…..ntchito kudandaula kma akati ma demo busy eeh sindikapanga nawo…..malawians mumakonda peace mwauchitsilu…iwud rather die fighting for my country rather than afool idle in my home

 59. This s pure nonsense! Go to thoz countries that u say r rich they hve their own PROBLEMS…..THIS s a global crisis…. Not only Malawi s facing this…Just work hard in silence…..akutaitsanipo nthawi apa

  1. But to tell you the truth Malawi is facing more problems than any other country in Africa. You’re just siding with the government while surely people on the ground are facing a lot of troubles physically, materially and financially.etc

  2. That’s tru # Foster M Ndalama Msisya….we all went thru the same bt with help 4m God n hardworking…..life s moving…..matenda aakuku;inferiority complex

 60. Nkhani iliyapa siyawumbuli ma demo amapana anthu olemela iwe kapokangolo ukupanga matama ndiwe osabeleka kape iwe mawa kuma demo amene akunyo ndiwe mbuli no comments

 61. inuyo atsogoleri ama demo osayiwala kuzasogoza your sons & daughters patsogolo mwayiwala ana aanzanu ku mzuzu pa 20 may mademos si solution alaaaa

 62. Ngat Demonstration Kuli Kutukwana Nanuso A Mw24 Mukangomuza Demonstrationyo Kt Mapaz Ake Chifukwa Chimenecho Ndi Chamba Akufuna Apheseso Anthu Osalakwa? Komaso Mukamupeza Wosogolera Demonstrationyo Tel Hm Dat Heshe Very Stupid Cz Akungofuna Aphese Anthu Osalakwa Kuwonongesa Katundu Wa Anthu Iweso Wa Mw24 Ngat Wasowa Nkhan Yochita Post Ungolemba Iyi : #ubwino.olima Chamba.com
  Ndakwiya Nanu Tamalemban Nkhan Zomanga Osat Zosokoneza Ziko Lathuli.

 63. a mayaya ndi anzanu tabwerani pa public mutiuze kuti mukanakhala inu president mukanatani kuti mavutowa athe, timve mzeru zanu mwina tingasithe maganizo ndikukupatsani u pres inuyo, apo biiiiii zikalimani fodya uko za ziiiii ngati ndinu odziwa apa. mxiiiiiii

 64. Billy and ur friens u talk on behalf of ur families and needs not Malawians. go demo may be u,will be given more funds. why dont u,use ur money to take care opharns and in less privileged. stop nosense.

 65. hahahhhahahaha anthu enawa amalaka laka kuvotera O bama pa Nyasaland… Eniakewo ma Pizza tima drinks enafe milomo mbuuu chimbatata chootcha plus madzi a k10. Pangani mutiuxa chitukuko chomwe mawalo mupange.

 66. Bingu anafa chifukwa chosowa mtendere chiphere ana osalakwa. uyu ng’ono wake wolepherayu sangayelekeze kubweleza chiwembu chotere.

  madokotala, ma nurse, aphunzisi tiyeni pa nseu mawa

 67. Mind u,boma silolimbana nawo since one party era….umafa ngati kamwanapiye okupha osamuziwa..anthu amakulira koma subwereranso…for this organisers for demos,chitetedzo chawo ndichokwana musawatengere u wannar regreat.thanks

  1. Ukadzachiona chitawerama udzathawe sichitsa chimenecho!! uwu ndi moyo wa mantha woyenera khwangwala yemwe makolo ake anamuuza mawu ndanena poyambawa!! Ndipo anchina John Chilembwe akanakhara ndi mtima ngati mulinawowu,sim’bwezi ufulu tikuunenawu ulipo lerorino!!!

  2. Ooo! kodi inunso ndi john chilembwe! a john chilembwe ena anafa 20 aja chifukwa cha mademo omwewo chinasintha ndi chani? bola john chilembwe timamulemekeza mu history ya dzikoli, nanga 20 enawo akulemekezedwapo? kodi ankapanga john chilembwe ija inali demo? kodi kamudzu analimbana ndi asamunda muja inalinso demo? nanga kulimba mtima kwa bakili ndi ansembe pobweretsa multiparty inalinso demo?? kutseri kwa demo kumakhala zowawa zambiri komanso simasinthitsa zinthu. eish!

  3. Sorry! nthawi ndi ndalama bambo! kuti munthu utukuke ndi kutukula dziko lako ndi kugwiritsa ntchito bwino nthawi yako. ukalimbana ndi za mzii umangozibera nthawi yako.ukalolera kugwiritsidwa ntchito mzamzii nde umphawiwo umenewo!

  4. Zitsanzo muli nazo zambiri inu mukuziwa kale.kapangeni ma demo wo,following with interest.mwina tiwona kusintha ngat simusinthidwa ndinu

  5. TIYAMIKE NAWENSO NDIWE OFOILA CHILEMBWE ANATIONONGERA ZIKO PHUMA NDI KUTHAMANGISA AZUNGU ZIKO LATHU LISANATUKUKE ZACHAMBA BASI

  6. NDALAMA NGATI IKUMAGWA MPHAMVU DOLLAR NDIYE INU MUKUT CHAN MUKUONA NGAT IFE TILIMTULO SITIKUZIWA MENE ZIKO LAPANSI MENE LIKUENDERA?

  7. My tears r still fresh upon the death of my xulment Robert chasowa’due to his death,i leant alot.make sure muli ndi chitetedzo when comes to ague the government.thax

  8. Ma demo mwapangawo what changes?kungotaya nthawi basi…khoswe pa khate sapheka mind u.liwu la kapolo silizamveka patali zimenezo muziziwa

  1. Don’t just stay idle kudya mango anzanu akubelani ndalama zanu nkumadyela buledi,nyama achina pizza basi inu nkumadya mango phee koma zikuyenda?Tiyeni kunseu tikawauze ma fosha amenewa asamangodya ndalama zathu,kkkkkkk……

 68. I thought this one is against our donors for telling our former lady president to give away our jet or against donors for withholding aid or against the slow execution of cashgate cases?

 69. mwatha maplan amayaya stop doing useles thing who toid u that doing demo is asolution lets look into almighty god he wil help us

 70. m.palibe m.mawa tikapana khoko
  ndazilondao peter utumize amene ….umadalilawo ifeyathu ndi miuta ………..no miter kuocha ngati m.mene mukuonelamu …….m.mawa 6.00 a m paseu ………
  ……Nyoooooooo? zaunsilu ……..
  …ife tidzikala mwamantha ……
  ..chifukwa chanchi Nsilu china

 71. Wat kind of ppo r u anthu osalapa antundu wanji munthu ukaluze moyo dhifukwa cha sku limodzi tamuzeni billyo akhare president atapange zanzelu iyeyo osamafa mitu ngat nonse mayanu ndamodzi mukamatcha nde zti zisinthe ndalama tizingotora coz mwamatcha

 72. Apa Bola Wamboni Amene Savota.Mayoooo!!!! Ndikanaziwa Ndikadalawila Kumunda Osati Pa Line Kukavota Kunyowa Ndizaziiii!! Mwaiwala Kale?

 73. Dear mwanawanga chonde ndisamve kuti wapita ku ma Demo sinnakuberekere kuti wina akusandutse Hillo pa imfa yochita kukomza wina kuti atchuke udziwe kuti pelibe chomwe chingasinthe moyo wathu kupatura kudzilimbikira tokha popeza dzikuchitikazi baibulo linaneneratu ndatha ine kholo lako SIKADZA KOKHA

 74. ZA ZIII ANZATHU PA ZAMBIA APA AKUMAPEMPHERA IFE NDIYE TIZIKAYENDA PA MSEU NDALAMA ZOPEMPHAZO BWANJI OSAKAPASA AMASIYE BWANJI? MUNTHU OPANDA MZERU NDIYEMWE UKAKHALE NAYE KUMENEKO, KAPENA MA DOBADOBA ,UKANABWERA NDI NKHANI YOMVEKA KOMA IYI AAA EHEEE #MANYAKANYAKA

 75. 4 What Purpose? Mesa Boma Atisilemba Anthu Job Caka Cino. Lets Pray Hard To Our Beloved Papa,GOD Creator Of All Life And Lifeless Thingz. Am Out

 76. Ngati mwaona kuti amene akupanga zionetsero ndi zitsiru mukawatukwana mukufuna kuti uchitsiruwo uthe kapena ai, kapena mufuna kuti tidziwe kuti nanunso tinzeru tabwino munali nato tija takutherani mmalo mwake mwakhala opanda nzeru kapena kuti mwapenga kapena ndinu zidempete ndikunena ndi inuyo mukumatukwana anzanunu ndi olemba news omwe mukuwatukwana zimenezi ndiye mwati ndi nzeru tsopano ngati muli anthu opemphera mukatukwana Mulungu wake ndiye uti amene amakuzani kuti mudzitukwana anthu osaganiza ndikuchita zabwino? Mudzifunse kuti mukusiyana pati ndi olakwitsawo

 77. Mayb Mr President isn’t know that things are going wrong almost each & everyday!!! So, we better do something indeed 2 express ur anger!!! Ine ndikugwirizana nazo!!!! Zikapanda kusintha!, tivotanso tione ngati angawinenso!!!

 78. Sazapezeka olungama chfukwa zikamalakwika wina aliyense amane mzake amene analipo pa udindowo m,mbuyo mwake, go 4 demoz, bt wth care, otherwize u wl come on ambulance whch iz bad.

 79. Amalawi Mantha Ndi Chifukwa Chake Tikungongala Anthu Osauka, Timaonerera Pamene Muthu Akusokoneza Ndi Kutibera Komwe Ife Timangomvetulira Timvekere Ndife Atendere

 80. What we will benefit after having that demos? My fellow youth, lets refrain from this . Our memories are stil fesh on what happened on 20 july 2012. If you are not happy with this regime wait until 2019.

 81. peter apange chani?inu simukudziwa mavutowa kuti adzandichani?cash gate,floods.xenophobia zatenga ndalama za malawi,solution ndiyakuti free hospital more challage ,,,,stop your nonsese

  1. like ua c0ment br0da peter z duin enythn 2 help malawianz bt an2 sakuxwa ine0 ndaona painternet ambiri abt pr0blmz wl malaw wub facing bt peter akupempha maik0 ambiri kt amuthandixe including hea in southafrica bt zonse czingabwere nthwi im0dzi

 82. Poti ine am based in south malawi koma zimene muwaonetsele aboma zikhale izi: kukwela kwa renew driving licence,misonkho ya anthu apantchito,misonkho pamalonda ndikusamva ma dandaulo anthu omwe anavota apo bbii ndibwera ndekha konko mxiweee!

  1. Yes akungolakwisa iwe sukuwona tym zinazake kumaziwona zithu bwinobwino posatengela chipan chosatila how many pipo r enjoying dis government??????? Am a historian i dnt do politics bot i know politics

 83. siuja tinkati ndiophunzira,ndiizi mawa tikumuvalira black & red, utsogoleri siofuna kungovumbuluka ndikumazitama kuti ine ndimatha!!!!

 84. ndalama zoyenderazo tangothandizani boma kumbali imeneyo ya health sector odwala akukondani nangamuyende mukuwona chitasinthe mchani malawi alibe ndalama koma Billy mayaya musakhale ngati wachichepere

 85. Just pray hard that u come back from demo alive otherwise your Children can bcome orphans b4 time ine ndili panyumba chifukwa palibe chingasinthe pa Malawi

 86. Ko agalu inu mukudana ndi zionetselonu tiziti pitala wakupatsani masikono mkamwa mwanumo? Koma ife amalawi ofunila dziko lathu zabwino mawa ikamati 6:00am tokapezeka pa mseu basi no matter pita akatumize agalu ake aja ametchedwa apolice kuti akathane nafe koma ife sitiopa,, sitingalole mtchona komaso yemwe watsala ndi zaka zochepa padziko pano kuti ationongele Malawi wathu, ana athu akudalilaso Malawi yemweyu,,,,,

  1. PITA WEKHA IFE SITIKUONA VUTO TIMAZILIMBIKIRA TOKHA,BOLA USAKAYESELE KUSWA MA SHOP UKAZIONA ZIPOLOPOLO, KUTI PHAAAAAA!!!!!

  2. Eeeeeeeee! Yankhula Ngati Wolengedwa Nd Mulungu, Iwe Nde Uli Nd Zaka Zochuluka Pa Dziko Pano?Pitan Mahero Pot Tonse Sitingakhale Mahero Mm-mm

 87. ma demo mukapanga ndiye mukhale mutatukula dziko lathu mawalo
  tsiku lililonse tidzingowerenga nkhani zauchitsiru basi.mudzayese kukhala anthu osakonda ndale mudzaone mtendere mudzakhale nawo.
  mmalo mokagwira ntchito muli busy ku msewu.mukadzachoka kumeneko tione dziko lathu litalemeratu.Anthu Opita Kumsewu Kuzionetsero,okhoza Ndi Wopangitsa Zonsezi Ndinu Zitsiru

  Nanunso A Malawi24 nkhani zinakutherani eti?
  tamayeserani kuphunzitsa anthu pa page yanuyi za momwe angatukukire osati ndale zokhazokha.
  Ifetu Sitisowa Ndale Coz Timadziwa Aliyense Wandale Ndi Galu/chitsiru Ndi Onse Owatsatira Amakhala Opanda Nzeru.Ife Tiphunzitseni Kuti Tingatukule Bwanji Moyo Wathu Osakhala Za Mademo Agalu Inu.
  #taonenikupusandizopandapake

  Mxiew!!

 88. Go ahead for as long as there is no element of hatred,jeolousy,frustration and unpatriotism in the motive of it all.Tiyende pamodzi ndimtima umodzi tikatere Malawi yanyamuka kuti odi uko tambala walira kaya wina afune kaya asafune Malawi ili paulendo. Guys find me pa wasap +27815898327

 89. Ziwonetsero zimenezo mukapanga anthu awiri ndi akadzako ndithu, m’mene munayambira ziwonetsero muja zikupindula chani? Mukungofuna kuphetsa anthu osalakwa basi. Anthu omwe anafa pa 20 July aja abale awo mukuwathandidza bwanji? Mukungofuna kugwiritsa ntchito anthu pa zinthu zakuti mukupindula ndi inu.

Comments are closed.