Four arrested for illegal possession of foreign currency

Advertisement
Arrested

Police in Malawi’s border district of Mwanza have arrested four people for being found in illegal possession of foreign currency at Mwanza border.

Deputy Public Relations Officer for the Southern Region Headquarters Surgent Widson Nhlane identified the four as 31 year old Agness Tchali, 32 year old Precious Musapha, 35 year old Judith Matope and 39 year old Peter Augustino.

ArrestedAccording to Nhlane, Tchali was found with 3650 South African rands, Musamba and Augustino had 3000 rands each while Matope 2680 rands.

“All were going to Sourth Africa and upon being searched they were found with the said currency without documents,” said Nhlane.

Nhlane has so far urged people to have supporting documents whenever they are going out of the country with any amount of foreign currency.

Tchali comes from Mwanju village in the area of Traditional Authority Chimwala in Mangochi district.

Matope hails from Chalata village in Traditional Authority Mpunga in Chiradzulu district, while Augustino is from Chapota village Traditional Authority Changata in Thyolo district and Musampha comes from Makalani village Traditinal Authority Mpama in Chiradzulu district.

The four will soon appear in court to answer charges of illegal possession of foreign currency.

Advertisement

83 Comments

  1. Mesa kugwa kwa kwacha uku mchifukwa chosowa ndalama za kunja(foreign currency), ndiyeno anthu akuthandiza boma kubweretsa ndalamazi mukuwamanganso? Asiyeni akuthandiza malawi amenewo. “a #Yusufu ndalama ndi ndalama”, amalawi foreign currency ndi foreign currency basi.

  2. kodi police imadzitenga ngat ndani zoti muzilimbana ndi kutukula mmakwanu koma kulimbana ndi kumanga anthu zopanda pake ngat izi

  3. abwana its not kuti anthu malamulo sakuwadziwa koma malamulowo amagwira ntchito kwa anthu owelengeka ndipo izi mukuzidziwa ngati muli ndi mulungu mumtima mwanu, mwa anthu 100 amatuluka kapena kulowa ndi angati amankhala ndi mapepala andalama zawo? ndayenda inu mudziona mabus paborder po, tikudziwa ndiinu ophunzira koma pali anthu ophuzira APA ndipo odziwa kuposa inu bwana.

  4. zinangovuta kuti sanawanyemele izi sitikanadziwa, anthu onse aja akumadutsa paborder akumazitenga kuti ndalama zakunjazo mmene zikusoweramo.?

  5. Apolice ndi anthu oipa akuba kwambiri kukhala ndi ndalama ndi tchimo zausilu bas aba,mesa ndi zawo ndiye vuto lilipat koma akanakhala akuba ndiye chimwemwe tsaya poti mumagawana anthu opempha inu fotsek

  6. Apolice ndi anthu oipi akuba kwambiri kukhala ndi ndalama ndi tchimo zausilu bas aba,mesa ndi zawo ndiye vuto lilipat koma akanakhala akuba ndiye chimwemwe tsaya poti mumagawana anthu opempha inu fotsek

  7. Mbuzi za anthu odana ndi chilungamo inu, don’t you know that being found in illegal possession of foreign currency is an offence when your police is trying to what the laws say you criticize, go to South Africa if not Mozambique and see how our brothers and sisters are suffering by police,,,,kusayenda kukuchitsani kukamba za nonsense

  8. I really think this law need to be changed somewhere somehow. I understand they can be money launderes and at the same time they can those that worked so hardly to earn a little they could and go home with it. So pliz #checkthislaw again.

  9. Munakadziwa mene a Malawi akuzuzikila moyendamu sibwezi inu manachoka mabanja olemela komanso mulindimtendele wamutima mungawazuzenso chonchi ngati alindindalama ndizao zimenenzo dzana ndi dzulo mwalephela kumanga anthu omwe anasakadza chuma chaboma mamilioni ochuluka monga ndasiya basi koma zandikhudza kwambili

  10. Make a follow up of the case and see if the police will loose once they take the accused pipo to court thats when you will realise that malamulo simukuwadziwa

  11. Apa pachuluka mbuli zosadziwa malamulo a foreign currency.Tafunsani anthu akuwuzeni, mainly ask your nearest bank they will tell you offences associated with foreign currency.

  12. apolice achsmba amenewo munthu asakhale ndi foreign money koma yakwanuyo yooanda mphamvu zitsiru inu,mbava zobela anthu masana inu..zayamba liti izi? munthu akavutike kufuna ndalama inu kuzangotola chikwama.

  13. What do you mean by foreign currency, how much is that , why dont you disclose to us the amount? Why arresting them , was that your currency, did they steal from you ? Dont they have the right to owe the foreign currency? Is that a crime? Shit, by metioning the word boarder means more than one country sharing a boundary and that clearilly means that different foreign currencies of different countries found at this place ,was it a Zim . Dollar, USA DOLLAR, ZK, RSA RAND, tell us , why arresting them, you better explain to us so that we can learn from there and avoid to have foreign currencies.

  14. Ndalama zake mukummanganso.mumafuna ndalamazo zipezeke ndindani?kapena mwanva kuti waba?amalawi tidatani kukhomelerana tokhatokha?achibale aziti mwana wamangidwa chifukwa anapezeka ndindalama,shame on you mumafuna akugawileni eti? n

  15. Malawi Police Officerz its unfair 4 wat u hav done kod kusauka nd chifukwa bwanj mumangofuna kumakama yoonda kod mwaxowa ndalama zoyendetsela dziko?

  16. Apolisi mukulephera ntchito… Moti akuba masanawa simukuwaona mukalimbana ndi azimai ? Mukungofuna kwabela ndalama zawo, asiyeni nao azimvela kuwawa sikuti angotola ayi

  17. Mesa mumatinso foreign ikusowa ?Koma zikanakhala zanu.Wakudandaulirani kuti amubela ndani ? Muwamasule ndisanafike kumeneko pano ndikuoloka Mkulumadzi.

  18. Mwasiya anthu akuba ndalama yaboma yomwe ikanathandiza amphawi kulimbana ndi anthu omwe akukazisaka, (migwanya) pepani kwa ma friends anzanga ena muli mu police ,ndikhululukileni ponyoza koma ma officer ena amalimbana za ziii

  19. Aaaaaah ure arresting them couse of 3000 which has been sent frm south africa to malawi aaaaa ma coutry eish u can’t arrest Dausi whn he change billions of kwachazi in foregh corrence why dnt u ask him where he gets those billions? Osauka tidzakhala osauka kumalawi apolice apa mwaza ndinu zitsiru kwambili ogona ndi agalu

  20. Kanundu eti! illegal possession of foreign currency? Do you want to tell malawians that anyone who goes out of this country declares the foreign currency that they have? This doesn’t carry any weight .Pali zimene a police mumafuna ndiye akukanirani, I believe so then you decided to misuse your powers.

  21. Why is it news now? Even them are also doing the same business through those guys,something just went terribly wrong.If I am working across the border what currency am I supposed to have? Do I need to to the bank to get papers? Where are our foreign exchange bureaus getting those monies?

  22. Kodi Malawi wa ufulu uja anapita kuti?, kodi nanga ufulu imeneuja tizaupezanso? , ndizotheka chifukwa chakuti mulungu alipo. Oooh ambuye tikupenphani kuti mutichotse mmavuto omwe tikukumana nawo mdziko muno

  23. Ine ndiye Foregn Currency ndiri nayo ya Maiko osiyanasiyana ndiye mudzandichulukire Nzeru mudzayaluka ndithu mukuona ngati anthu amenewo Rand imeneyo anaipeza ku Malawi afufuzeni mupeza kuti analinso komkuno koma poti ulendo olowa kuno akuudziwa ndichifukwa sanamalize zawo zonse malume dyera kkkkkkkkkk

  24. Umbulitu uwu so called police, pa border! Really? What about aja amabera anthu ma R50 pa bus in the name of fake this, fake that just to torment the innocent just because they are travelling. Mumawamanga amene aja? Kadziko kang’onong’onoka ena mmadzimva ngati you own it

  25. Koma inu azimai mwawagwilawo ananva kuwawa kwambiri asiyeni ndindalama zimene anapedza akagulitsa utsipa ndi mipunga kuno kuno aaaa

  26. Apolice ili nde bodza ili . Mwangosowa owamangawo chifukwa pa border foreign currency nde ambiri amakhala nayo osati mkumanga anthu 4 okha ayi. Munali nawo zifukwa

  27. Nde zopusa ndi ndalamanso imeneyo? kodi apolice mumafuna muzitchukira pa anthu osauka bwanji? si mumati munthu akamapita ku SA akhale ndi R3000 mu passport yake, mumati aike kuti ndalamayo? aike mmimba? mxxxiiieew, apolice muli ndi mtima wa nsanje kwabasi, ku Malawi kuno kulibe ma bureau or ma bank oti munthu akhoza kukhala ndi foreign currency? mwandinyasa kwambiri apolice, mumakonda kunzunza anthu

Comments are closed.