Bushiri puts God for sale

Prophet Shepherd Bushiri

…Malawians question: Why selling God’s blessings?

The self acclaimed Malawian Prophet Shepherd Bushiri continues to leave Malawians with more questions than answers following his decision to sale what he calls ‘special prayers’ for MK10 000.

Prophet Shepherd Bushiri
Bushiri, puts God’s blessings on the market.

Bushiri who jetted into the country on Thursday for his Mzuzu crusade, ordered people to pay the said amount for a sticker for them to have a one-on-one with the prophet.

Readers of  Malawi24 complained that the prophet’s demands were nonspiritual.

HERE ARE SOME OF THE COMMENTS FROM READERS .

Francis Kanduwa Mwina ndi sin’ganga nde 10 grand yo ndi chipondamthengo….nanga tinene kuti bwanj!!!, A comment which compared Bushiri to witch doctors who demand money prior to giving any treatment.

Wage Dan NamaQa kutolera za misonkho ku Malawi za Joni kodi Zachepa eee koma dyera ndi la chabe olo kuti palibe cha ulere mmmm zawonjeza malo mothandiza akuti bela eee am so khuzd mwamva zandi khuza hevy uthenga wa Mulungu mulengi wa ziko la pansi tasandusa malonda ndi kumabera anthu koma pa Judgement daY Ziliko ndithu.

Robert Kaphuta Nyirenda Mu Bible mulibe mneneri amene anagulitsapo mapephero. Ngakhale Yesu amene sanagulisepo mapephero. Zimenezi zikuwonesa kuti bushiri ndi mneneri wonyenga komanso ndi wakuba anthu akuwona kaya anti coruption irikuti. This is pure cashgate.

Câptâîñ Sôldiêr Do not judge and u shall not be judged, all we have sin against God. tisaoneke ngati abwino poweluza zomwe zathu akuchita koma timpase mau abwino kuti amutengere njora yolondola. Zoti akulakwitsa kapena sakulakwisa akuziwa ndi Mulungu, tiyeni tisiire iye poti amaona zonse ndipo kuweruza ndi kwake

His ministry is one of the richest following revelations that it sales different branded merchandise with his name and face.

As if that was not enough, local traders were warned to refrain from selling their commodities as his ministry was busy making money out of the gathering.

It was also discovered that all the spiritual products such as anointing water and oil were not for free. Contrary to what the bible says, Bushiri’s ministry was selling a 25 millilitre anointing water at MK 2, 500 each, with the anointing oil going away at MK 5, 00M.

Anointing stickers were being sold at MK 1, 000.

The controversial prophet, whose miracles sparkled debates, has been warning people that they will die for castigating and questioning his ministry.

Contrary to how Jesus Christ entered into Jerusalem, the pompous prophet arrived in Mzuzu City on a jet he claimed was his and had a palade full of police bands into the stadium.

Advertisement

1,362 Comments

 1. SHEPHERED BUSHIRI IS A SIMON THE SORCERER AND HE IS USING HIGHEST LEVEL OF METAPHYSICS AND SOLIDIFYING THE AIR BY THE POWER OF SUB-LEVITATION AND BI-LOCATION TRICKS,MOVING OBJECTS FROM THE DISTANCE AND ALSO USING DIVINATION TO DRAW MUCH CROWED AND MUCH GAIN LIKE THAT GIRL IN ACTS 16.SO HE IS SIMON THE SOCERER THE GREAT ONE WHICH IS BEING TRANSLATED”MAJOR ONE”.THIS IS WHAT GOD HAS REVEALED TO ME WHEN I WAS PRAYING AND SEEKING TO KNOW THE TRUTH WITH ALL MY HEART.”But there was a certain man, called Simon, which beforetime in the same city used sorcery, and bewitched the people of Samaria, giving out that himself was some great one: to whom they all gave heed, from the least to the greatest, saying, This man is the great power of God.” (Acts 8:9-10).

 2. sanalakwitse amakamputa dara ameneyo nawo azimayi akumalawi kodi baiburo limati bwanji za aneneli sanati last ndi john babatst yohane 10 :3″””-7 wolipidwa sakhara m’busa 10.000 kupempheleredwa 20.000kudya njoka

 3. akulakwa kma akusocheletsa anthu osazindikira!!! may God 4ge him…y sellng God??? chingauluke bwanji chidzatera mulekeni

 4. Abushiri mumandisekesa moti mulalikire zakubwera kwa a mbuye amati inuyo dzina lanu ndi so so mumakhala kufupi ndi chakutichakuti a bushiri siyani za utumiki ambuye akukanthani zimenezo siyani si mbali yanu koma mungoyamba za usinga’nga. Basi iweyo si major ayi major ali ku barracks

 5. exactly…from a distance you can not be sure if something it’s a cabbage or a lettuce. He is clever than we are, with power he gained while he was a son of God. He came to Jesus in the wilderness one day and promised him a big city!! Another he will come with job opportunities… with the natural eyes it’s difficult to note

 6. Do you think the Devil will always come with trouble and wars? No…not always! sometimes he will come calling on the name of the Lord, doing many wonders and healing the sick….I tell you before so that when he come you will know…. Jesus said

 7. Vuto ndifeyo anthu kusowa chikhulupiliro mwa Mulungu wanthu wamoyo…. What i know is if u PRAY wth FAITH chozizwa chimachitika…… Sindingapembedze milungu ya bushiri ine nevr… Mulungu wanga ndi wa moyo.

 8. You Malawi people don’t realise what you are having, you are busy judging. He who sits on the throne is a judge. The man of God has a heart for his country but you are busy accusing, may God forgive you. “Touch not my anointed one”

 9. simuziwa chomwe mukuyankhula muziyamba kaye mwafunsa musanalembe mwadya chamba uko munalemba zopusazi ambiri ainu mungolemba koma simuziwa kuti zimakhala bwanji munthu chilichonse kuti chitheke chimafuna ndalama akanakhala kuti akugawa zaulere muzitinso wasatanic kweni amnalawi mumafuna chani simumayamika mzanu akamachita bwino ndiye NDIKUZENI OR MUSHODZE OLO MUNENE BWANJI IFE NDI NGA NGA NGA NGA PAMBUYO PA BUSHIRI PROPHET WATHU WATHU anthu oipa inu koma zikanakhala za mathanyula ndiye kuyamikila muzafa opanda kanthu cfkwa cha nsanje ndichifukwa atsogoleri aboma angokubelani ndalama za mitsonkho cfkwa chokhala busy kunene miseche GOD WILL PUNISH YOU IDOTS

 10. Oh my God mpakana zafika pamenepa? But u must know these ali wotembereredwa yense wogulisa mphatso ya uzimu yomwe iye anailandira mwaulele kwa christ Yesu, pakuti sanatidzodza ife ndi mzimu woyera kuti tikawalipirise koma tikaphunzise ndi kuchirisa onse omangidwa ndi mthenda ya satana mdyerekezi mwaulele.

 11. Masiku omaliza soka kwa amene saziwa mau ndi amene akutengekanazo abale musakhale m’tulo ayi dzukani muwone kuwala kwa manso mphenya inu inu kaya zanu izooo

 12. Akulondola mesa akugulitsa mau amulungu ngati iwowo ali m’busa mkumalamula kwa amene akufuna kwa pemphera ndigeni akuchitayo amene ali ngakhale kuti akudwala sangalandire mapemphero mchimodzi modzi malonda ngati ulibe ndalama sungagule kanthu ndi aneneli onyenga amenewo

 13. Akupanga Bwino Kwambiri .. Kodi Mukulimbana Ndi Bushiri Bwanji? This Z Time To Make Good Relationship With God, Or U Wil Find Out That God Z Judging U And Throw U To Hell.. Be Busy With God Not Man.

  1. Without a a good relationship with with jesus you can not have the spiritual eyes and spiritual ears, as a result you can judge the way those people who are not Christians can thinks about him, we need to have the Holly spirit to connect us to God who knows the secrets anything.

 14. Kwa asing’anga anthu amapereka Chipondamthengo kuti athandizidwe, ndiye uku poti mkwa Prophet, anthunso akuyenera kupereka Chipondamtchalichi.

 15. Mbuye mene munali pasi pano munkavala mkanjo ndi khwaira simunayende ndi olemera abwezi anali amphawi anaimba kale soja

 16. I’ve been here opposing this man Bushiri that he’s a fake prophet koma tiatsikana tina koma ayi mumva bebe lero wabwera,wakwera ndege yake,wajambula chithuzi,wayenda m’malele heee koma mukhaula aaahaaaah!!!abale ndichani?lero siizi akuti mulipire chipulumutso,za annointed water zachepa koma ayi pemphero 10pin.koma uyuyu ofunika aone zomwe anaona Matiki ku BT’s wajayira tsopano wabwenjeza,wabhowa,koma iiiiii!!!abale anzanga yesu pamtanda paja munalipira zingati?popeza Yesu akachiritsa munthu amati pita usakanene,koma awa izi,zinazi,izo,koma uko akuti Pay for Prayer (PP)hahahaha!!!kkkkkk!!!khakhakhakha!!watchout Malawi

 17. oyitanidwa ndi ambiri koma osakhidwa ndiochepa,if not by God u ll stop prophet bushiri, if he is choosen forget it,no one can stop the plan of God,tiyeni tivomelezane apa ,mulungu ndiwachiungamo where is ur faith,things of God r understands by them that let God to sho them,ur not hamble,ur selfish fighting lose battle,how can God answer u since u already choose what u think is right,ur looking for majority hahahaha u ve neva started,i admire this prophet bushiri he is a true man of God,he is strong no matter how much ur condeming him,may God use him much

 18. ine ndinali komweko palibe aliyense amene amalipira, mulungu akukhululukire chifukwa ukulimbana ndi munthu wamulungu chilichonse chinali chaulere

 19. Where is this prophet getting the healing power?is he buying?Jesus sufferd en died for us including this man 4free!why is he selling Gods wisdom?Jesus perfomed great miracles 4 free.Nanga ichincha?

 20. Ngati mukunena zowona mawu amulungu saenera kugulitsidwa chifukwa kwa okhulupira ake mawua anaperekedwa kwa ulurere kma ngati ndizabodza Mukuchimwitsa athu pakulakhura through their comment

 21. my MAJOR 1 please leave him alone n who are you to judge him go to hell maan,PAPA I LOVE YOU n they can say whatever about you i know that you are true savernt of GOD

 22. Chisomo cha Mulungu sagula amapereka yekha bolani ukhulupilire. Analipira kale ndi mwazi wake Yesu ndipo palibe ngakhale verse olo limodzi mu bible lomwe ananena kuti tidzagula ndi ndalama madalitso a Mulungu. Zakumidima ndizomwe mumagulitsana.

 23. Sakuganizira uphawi omwe ali nawo anthu kma ngati mpingowo uli wa mulungu samalipilits kma ngati akupembedza ziwanda dzina ayi akuyenera kutelo adziwe kwa mulungu nd chlango chake.

 24. Vuto laketu anzathunu munatenga dzina lachiweto chopusa, “Nkhosa” iyeyo nakhala “M’busa” ndiye mumati nkhosa ingalimbane ndi m’busa wake? ? ?

  Akuberani kumene ndipo simunati sinanga anzathunu mumakhulupilira miracle kwambiri mwayiwara kuti ngakhale Satan amapanganso ma miracle.

  Inu Mulungu safuna munthu wina mpaka akulumikizeni pakati pake kuti inu mumvane naye, ndiye Atumiki omwe aja anabwera aja basi. Inu unthuyo janabah ya chaka chatha inakalipo ndiye kumati akupemphereleni? ? ? Ha a a a a mumandiseketsa ndi kundimvetsa chisoni ndi umbuli wanu paza Mulungu wo bwanji!!!! Mukapitiliza kukhulupira izi mudzakathera kung’anjo ya moto mudzaona!!! Apapa simungandikhulupilire kma tadikirani mukadzangosiya kupuma ndi kupenyako

 25. If he is Charging Malawians K10,000 for special prayers how much does he charge when he is in S,Africa? Our local Churches we give tithe not pay tithe; Prophet Bushiri why sell Gods wisdom thru special prayers? Some time l always wondered how Pastor Salanje got so rich a few years after dumping his Church in Chilomon; So the secret is selling Gods prayers, my footy: Its good you came to expose your secrets to Malawians’–Now l know why the late James Handley Chase wrote a Novel called Whats Better Than Money; Shame Bushiri – K10,000 its too much for an average Malawian who is in need of special prayers:

 26. WASTING YOUR TIME….THE DREAMS HAS COME TO PASS FOR OUR FRIEND BUSHIRI AND NO MATTER HOW PEOPLE WILL TALK HE IS NOT GOING TO MOVE BACK AN INCH.

 27. am happy that Bushiri he is a businessman osamudandaila ndi enterpreneur wankulu dont spoil somebodys business agwirizana kale 10 grand ndi 10 grand basi no discount amene sakufuna apite kwa Prophet Liyabunya

 28. Matsiku osiliza chilichonse chikuoneka pomwe Bible linayakhula kale…..Aaaa so wat picture shud we have pa bushiri ndiwe otumidwa ndi mulungu kapena unangofika kuzapanga money?… Coz za mulungu ndiulere2 mmmmm God have on us

 29. Ndikuganiza kuti zikufuna kungokwanilitsa zomwe malembo ananena zamasiku otsiliza, nanga ataukitsa wakufa angati zingati?

 30. kmano kutengera ndimene chaka chino zithu zkuvutra ndkuona kt a Bushiriwa sakulakwitsa chfkwa iwowa nthawi ya mbiri amakhala akutumikira mbuye ndeno mukut ndalama ayitenga kt pamenepo!!!?

 31. Bushiri alipaukapolo jaji ment day ndioyipa osamumvela olo pang.ono amene akupusitsika mukuyenela kudziwa kt bushiri ndi chiwanda chenchen chofuna kusocheletsa khosa za mulungu ine ndachikana chiwanda chimenechi holy ghost fire

 32. ngati wolemba nkhani ukutinamiza ziwa kuti bodza ndi ntchimo pamaso pa YEHOVA ndipo ukuyenera kulapa mu dzina la YESU ngati ndi zoona mlekeni nansongole ndi tiligu akulire limodzi azasankha mwini, bible kumanja osaiwala kulimbana kwabwino ndikupemphera

 33. tiyeni tiyike zopemphela kaye pambali. nigeria earns a good amount of money thru TB Joshua thru ppo travellingt to scoan and the nigerian bottled annoiting water. inu u have bushiri amene akugwedeza kunjaku koma kumupanga defame. akankhala Kuti he was based here bwenzi kukubwela anthu kuno. he prefer kumene akupeza ntendele uko.

 34. ndibwino ngati mulungu wapeleka mphanvu yochiza matenda pitani mzipatalamu anthu akuzunzika kulila usana ndi usiku ululu osatha akulakalaka mutawachiza

 35. Myeyo mndani kodi kuposa yesu ngati angadzutse wakufa ngakhale atati K10.000000 ntchito imeneyo ndiyaeni akulowerera kodi Yesu analandira zingati poti iye ndamene anagwira ntchito yopambanai Oky

 36. Opusa ndi anthuwo iwowo mwawokha ndichikhulupiliro chawo kupempha mulungu sangawayakhe? Kumbukirani mau aneneli yesu( ndizakhala ndikukupirirani paka liti inu anthu opotoka mtima nanga chikhulupiriro chanu chili pati.)ngati iyeyo bashiriyo amakhulupirira mulungu ndichifukwa chani akuyenda ndi ma bord gud kumukayikira mulungu kuti sangakwanitse kumuteteza komanso muziwe kuti yesu anakana ulemelero wa ziko lapasi chifukwa chake analola kuzuzidwa nanga iwowo akulipiritsa pembero akuyembekeza chani kwa mulungu

 37. Sanalakwise ayi, panopa zinthu zambiri zakwera mtengo nde iye wayeneranso kukweza kwa ofuna kuti awapemphelere, mudziwa bwanj komwe amakatenga mphamvu zakezonso akweza.

 38. Amene akupemphera mpingo kapena chipembedzo koma iye saperekako ndalama ayambe kudzudzula bushiri. CCAP kuli yachitupa, aroma kuli chamtulo, bible tikugula. Kodi kumeneku sikulipilitsa mau a Chauta? Bushiritu wangozibweretsa poyera ngakhale zikuchitika mwachinsisi m’mipingomu.

 39. Amalawi mungooneseratu kuti ndiinu amphawi tamvesesani akuti AMUMPINGO WAKE osati WANU ayi asiyeni amumpingo wake azipereka macoment osaukawo athawa okha inu amafellowship inu opemphera mmakalasi chikukukhuzani ndi chiani achamba inu chikukukhuzani ndichian amatisheti ataliatali inu amashati amadigadi inu amatrouza aturnup inu amajekete a 1 ng’amba inu asapato za?mark inu ndi mahule onse amene akuona kuti azibambo akayamba kupereka ma 10 pin game yayo yagona musaperekenso macoment tisiire zikhwaya za mchurch mwakemo azipereka ndiponso ndiyochepa kwambiri iweyo ndi ine tizingolira ndi uphawi wathuwu basi mapolofiti ena inu kupeza mwayi opita kunja bandukani ndichifukwa Bushiri anaiwerenga kuti amalawi amxanga ndiasiru umphawi too much lero tinapereka madaliso kwa anzathu akusouthafrica MAJOR 1 MORE FIRE usazabwerenso uzingopita ku Amereca ndikubwerela konko ku SouthAfrica

 40. Anthu zomanamizira munthu wa Mulungu sibwino,komanso bible linati usaweruze kuti uzaweruzidwa kodi zanu mmachita zinja amakunenani ndindani musiyeni Mulungu aweruze yekha,ndipo iye mukumuthandiza kukwera ,komanso kuti dziko limuziwe koposa poyamba amene sanachimwepo azikamba,koma ena tonse ochimwa tikhale chete.

 41. Ndimasowa umboni woti bushiri ndi wabodza apa ndiye ndawupeza mpaka kulipilitsa mdalitso yesu sanachitepo zimenezi iye wazitenga kuti

 42. Bushilli ndi friend wanga ndiye ndingokuwuzani mmene amapangira;Adaawa akapita ku Moshico(Mozambique) amakatenga chithumwa cha miracle money,ndiye akabwera kunoko ndi mmene amayamba kupanga ma miracle money komano chithumwa chija chikatha mphamvu iyeyuno amayenera kuti apeze ndalama zoti akapangitsenso renew chithumwa chija, mwamva?Ndiye mumaganiza kuti ndalama panopa mmene yavutiramu iye apanga bwanji?(Musamuuzetu tingasiye kucheza)

 43. Bushiliyu asing’anga amchulukira, ndiye atani?Pa usatana wake anayenera kuti apemphe ndalama kwa onse omwe Mulungu sanawatsegulebe maso.Onse omwe amapereka ndalama kuti apemphereredwe si ma born again koma ndi kagulu ka anthu kamene kanatopa ndi kupita kwa asing’anga,nanga atani?Bushili is an African doctor.Lets open our eyes and see that Jesus isnot a man to lie,He warned before about false prophets like the Bushillis,nevertheless Bushilli is not alone.

 44. Akuluakulu amipingo akhale naye pasi amufunse machitidwe akewa ngati ndizoleledwa pa zauzimu kapena. Afotokoze kuti Bushiriyo zimenezi anawerenga kuti. Chifukwa. Chiphuzinso cha chilendocho mulibe mbayibulo.

 45. we malawians,we were born jealous but remember,”the more we oppose him,the more GOD uses him and perform more miracles than before”.Let God Judge And Not A Person.Which Church Doesn’t Want Money??

 46. inu oziwa mau lalikani za mawutu osati kunyoza mneneri mwachitapo chani pa ntchito wotumikirayi,inuyo mukuoneka oziwa mau lalikani osachita phokoso lopanda ntchito,mukuoneka azeru apa mukanakhaladi anzeru mukanapanga zanu,iye woitanidwa ndimulungu sazaleka chifukwa chamibwebwe yanu,hahhaha tioneseni zoonadizo,let me tell u God is God of impossibility,zosatheka ndi anthu zimatheka ndi mulungu kwa iwo achikhulupirilo mwayesu,tioneseni chikhulupiliro chanu!!!!!! mumangoziwa za satanic basi ,hehehe sumunayambepo

 47. zizindikiro za masiku otsiriza,many will come in his name (Jesus) claiming they are prophets yet they are agents of the devil,but behold brethen do not judge,Only God can judge for human can not judge human,and judgment its for the almighty alone

 48. Ndimafuna ndikumbusane nanu amene mukumanena kuti anthu akamapele ka maganizo awo pazomwe Bushiri akuchita inu nkumati anthuwo akuchita nsanje chonde ndikupempheni modzichepesa kuti ngati muli anthu oti mumapita ku church ndipo choonadi mukuchidziwa chonde awuzeni zamomwe madalitso amapelekedwela pamunthu kuchoka kwa Mulungu. Kodi Mulungu akanati anthu adzigula madaliso ake inu mukadagula inu? Ngati muli nthumwi zabushiri wanuyo anthu simungawauze zoona coz inuyo mukudya naye ndalama zotembeleledwazo, anthu inu musaiwale Yesu akanafuna kuti azilipitsa pazomwe ankapanga ndukuuza ni panalibe amene akanakwanisa kugula coz anthuwo zowaeneleza analibe, nde inuyo wanuyu uyu munthuu wapambana chani kuti nkumagulisa madaliso? Iyeyo ndi Mulungu? Nkutheka kuti madalitso amene akunenedwa apawa ndiathumba osati ochokela kumwamba mwina pali njila zomwe zikusatidwa kuti muzinamiza anthuwo, musaiwale mfumu ina phwando litakoma anaamba kunyazitsa Mulungu, mundiuza ndinu zomwe zinamuonekela amene uja, awuzeni njila yoti anthu akapulumukile osati zokonda ndalama zanuzo Mulungu akukuonani ndipo kulanga kulipo ndithu.

  1. he didn even charge for the prayers. On saturday nit he conducted a dinner and the charges wer ten thousand. The prayers wer for free.. Anthuwa angotengapo nazo thembelero

 49. osayiwala kuti Mulungu wampingowo ndiiyeyo ndiye akutchaja cauz mphamvu amazitenga akuziwa iye#Anthu achulukirenji omusatira oyipayo mmmmmh Ndimangonjenjemera ndikaganiza mphamvu yamulungu.

 50. You haters of bushiri u r just jealousy of the. Prophet bushiri komatu one thing u should know is that its a curse to talk bad about the man of God.pitani uko ana a njoka inu nonse mukunyoza papa Wa ine major 1

 51. kodi mau amulungu amalipilisa abale?mmm koma tsiku lomaliza kuzakhala tchito abale tichenjele ndi atumiki onyenga angatisochelese poti chikhulupilillo ndi cha iwe ndi ine tichenjele

 52. I am not the follower of the guy, but the truth is that the guy is just honest because there is no single church that does not ask money from its church members. Honestly where do you think the man of God would get money to hire venues like the Mzuzu Stadium, run his private to enable him reach out to many needy souls or even feed his family as his sole job is spreading the word of God. The 10 000 for a prayer will help him reach out to many elsewhere.

  1. Ndipotu he didn even charge for the prayers. On saturday nit he conducted a dinner and the charges wer ten thousand. The prayers wer for free.. Anthuwa angotengapo nazo thembelero

 53. Ngat mzakwamulungu ziri bwino more than best,koma ngat ndizina ,the opposite is true,NB. Its not for us bt GOD Himself to reveal ameniiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiiii

 54. If it is for God it is free becoz we recieve for free but if it is for aperson it is for sell and more over things from prophet TB Joshua is for free why to pay to other one dont get any coin from people of god becoz Is not cheated

 55. When a dog bites a man its not an issue but when a man bites a dog it brings questions.The problem is this issue seems as if people are against Bushiri and his followers but the best thing is ask religious scholars both christians and Muslims to answer that coz if ordinaly people comment his followers think they are against him.

 56. Koma iyeyo bwanji…TB Joshua ndim’modzi mwa aneneli koma ndamene amapeleka chithandizo kwaanthu osianasiana ena kumalipilila xool….tsono satana amene amapembedza uyu mukumuti major ngotani kwenikweni?

 57. Kungot amasuta chamba amene, YESU, amachiritsa anthu akhungu, osaona mwaulere,mneneri onyenga ameneo masiku otsiriza chenjerani imatero bible

 58. Kulikonse mwalowelako mpaka kuma challenger gulu. Mawa ine ndikakhala prophet ndiye muzandiyamikileso. Hahahaha! Be strong to your belief but mukakhala ngati deya osatila madzi mupusa. Umphawi watifikapo, munthu kungokhala ndi chuma basi timukhulupilire? Omwe anapita ku mzuzu akuti kunali kuukisa akufa, i can’t blv that.

 59. Zabwino anthu samayamikila amayesetsa mu njila ill yonse kt munthu ukhale oyipa iweo loko atakhala akulipilitsa chakukhudza ndi chan? Akukakamiza munthu kut apite akalipile? U pipo u hv 2 leave Bushiri alone mind ur on business coz mukuchedwa he iz nt ur level samadziwaxo kt muliko inuo

 60. if the story is true bushiri is totally wrong cz GOD gave us life for free why him can’t do the GOD’s work for free? he better stop GOD himself will give us another prophet!

 61. Rastaman talk it
  put not your money inna pastorman pocket
  fi enter Zion gates seh yuh no need no budget
  just clean up yuh heart en yuh soul coz yuh no need no ticket!

 62. Sızowona zımenezı mpaka k10,000?munthu asıye kukagula nthumba lachımanga ndı matemba adye ndı ana zowona akagulıle mapephelo?bola munthuwe upephele wenkha kwamulungu dırect ndıpo amanva.palıponse palımulungu ndıpo nkhutu yake sılogontha

 63. No if God send you to spread His good news to the people you dont have to take an advantage of it to make business,it just shows that his prophecy is not real

 64. UTUMIKI UMENEU NDIONTHERA PANSI POMPANO ZAMULJNGU NDIZAULELE OSATI ZIMENEZO AYI.PAKUFUNIKA KUSAMALA ABALE NDI ALONGO.AMEN

 65. ambuye amava pemphero lako munthu bola chikhulupiliro so wat z bushiri,k10000 4wt madalitso bas mulungu sankalipilitsa or amat imadya pomwe aimangilila.

 66. Nanga osowa ‘monga wakhathe uja tikawerenga bible anakha zaka 38 osowa omuthandiza kuti agwere muthamanda muja,tsono pali anthu ambiri ofuna mwai ngati umeneu koma alibe pogwira atani?

 67. Prophet Shepard bushiri is a true man of God he’s the lord Gods voice if you don’t believe him you can just leave him alone.touch not the annoited ones

 68. Vutondiloti wabwela public ndiyemukumunena. Alipo ambiri. Inumukuwona ma prophet akugula ma private jet amazitengakuti ndlama? Don’t blame him. Phuzilani kupepelapanokha yehova azakuyakhani more fine prophet akang’athe 10 yachepa.

 69. Ernest O Nyirenda#thnx 4 yr comment.koma ngati nkhani yolipiritsa madalitsoyo ndiyoona.ai si munthu waMulungu.ngati anthu angopeka,tsoka kwa iwo

 70. Muwelenge Buku La Mafumu Lose Mumve Zomwe Zinachitikira Ana Ena Amaseka Zadazi La munthu Wamulungu Kunatuluka Chinyama Chomwe Chinadya Ana Ose Samalani Mulungu Angakutumizileni Zoopsa, Nanuso Amalawi24 Mudzatembeleredwa Zaeni

 71. anthuwa tinawazoloweza tokha pomawathamangira ndikuwapatsa ndalama komanso ena tikumawakhulupirira ndiye kwa amene zikutisangalatsa tiyeni tiziripira but know whom you are serving. In the bible palibe amene analipiritsidwa so mulungu wake ndi uti? popeza ndikumdziwa ine anali, ali ndipo adzakhala (samasintha)

 72. Ngakhale Masiku Amose Ena Anamunyoza Mose(Kumbukilani M’baibulo Miliam Atanyoza Mose)chinachitika Ndichani?Samalani Zingakuchitikileni Osanyoza Atumiki Amulungu Kuweluza Ndikwa mulungu Mungadzapange Nkhate

 73. all pple who r against man of GOD,bushiri,its waste of time…u can not understand him becoz he z preaching things of spirit so be n spirit…viva major 1,continue putting satan n PHENI,N JESUS NAME……..about money u miscought him,and remember aprophet iz not welcomed n his home towm,jesus said,look at the case of tb joshua, pple n nigeria create alot of bad stories for him but they hv failed to stop him why?they found themselves busy fighting against GOD,So do u think they can win?????so we malawians will win bushiri????JESUS HAVE MERCY!!!!.

 74. It is bushiri ministry owned by himself bushiri so if u are not in terms with his policies @ his ministry u can join others or form u’rs but stop spreading false news agains u’re own fellow son of malawi ,,,,,remove that envy from u’re heart MALAWI

 75. Eeeeeee! Munyanya anthu inu, apa wapanga bwino kuti manthongo achoke m’maso mwanu ndikuyamba kuwona. Ife tikamati ameneyu si mneneri wa Chauta paja mumatsutsa mumvekere the Major one, Man of God. Apatu mwadziwa kuti mkuluyu ndi man of devil eti? Baibulo limakuwuzani tsiku ndi tsiku kuti ambiri adzadza mu m’dzina langa, tsono inu mumati Baibulo limanena ndani?
  Kutengeka a Malawi ndi zinthu za ziiii zonunkha, machiritso kapenda mapemphero amalipiritsa? Hahahahahaha!

 76. kkkkkkkkkk ananena kale mawu Masiku omaliza kuzabwera anenili onyenga azizatchula zina langa. ndy mufunilanji umboni winaxo kupoxa umenewu zoxatheka muthu kumatunga madzi kuchisime kumakakhutula kunyanja athu okuwona aziti chan

 77. Nde Bushiriyotu tsopano nde ndi businesi,,,ai this is too much wayesa kuno ku SouthAfrica anthu akumapereka ma R5000 kuti akupemphererere iye osasiyanitsa bwanji mmene kulili kwathuko pano ukaitenga kuti ndalama yonseyo,,,,,anthu pano tikudandaula ndi ma fees a ana boma nalo mmene lakwezera,,yooooooooooo ,Ambuye muchitireni chifundo Bushiri sakudziwa chimene akuchita.

 78. SIZACHILENDO AMENE MULI AKATOLIKA TAPITANI MUKAPEPHE MISA KWA WANSEMBE NGATI SIMUKALIPEKAKO NDALAMA KAYA NDIMALIRO KAYA CHIKUMBUTSO MUKALIPIRA

 79. This thng is becomin 2much now…Peter wakukanikan and u r becomin poorer everday and u are silent… leave Bushiri alone and focus on ur povty….Mind u sakhala kumalawi kuno….Maliwias to much jerouse

  1. Simunaphunzile phiri that’s why u are inferior kwaBushiri, jealous yachiyani munthu alikubela anthu ndalama ndidzina lamulungu its time for you to wake up and stop dreaming ,Pitara alikutenga ndalama zaanthu so? Chamba ethi

  2. Shame on u Shaya and Colla,,,,,,Av ever heard Bushiri stealin taxpayers moner????If u r not interested in him just him alone and focus on politics and cashgaten

 80. malawians we must love one another osati kudana nkunenelana zoipa ai bushiri anakakhala wa dziko lina bwenzi tikumuyamikira.chikondi chathu chinapita kuti amalawi anzanga inu but any wei God achitebe chifundo kuti tidzikondana wina ndi nzake.

 81. ineyo sindidzakhulupiriranso mneneri ngakhale mmodz even ataonetsa mamiracles kaya kudzutsa akufa or atasunthitsa phiri kulichotsa malo ena mkuika pena coz ngakhale saturn ali nawo ake mamiracles so palibe wina mneneri owona angadzuke pambuyo pamneneri owona waola lino BRANHAM ena onsewa ndaneneri akumadz sindingaopenso kunena zimenez coz amandimenyera nkhondo zanga zonse ndimulungu yemwe anali mwa branhamyo

 82. bushiri sakulondola chifukwa olo mu baibulo palibe pamene panalembedwa kuti ambuye yesu amagulitsa amalipilitsa anthu amene amawapepherera/kueachulitsa iyeyo ngati ali mtumiki wa mulungu akuyenera kutsatila zimene ambuye yesu amachita,komanso akuyenera kudziwa kuti pali anthu ena amene ali ofunika mapemphero koma sangakwanitse kulipila ndalama ngati imeneyo nde akufuna kunena kuti anthu ngati amenewo saziwathandiza

 83. Even shaytan/satan can do magic, so becareful you who just trust anything, we are in the last days remember and no person will enter in paradise without being tested in this world, watch out

 84. kod A tumbuka analakwa chani?? Nzeru ndizathu mukuona ngat mungalande?? ma Brainz akubadwabe mukhaula. Morefire a TUMBUKA!!!!

 85. Akulondola zedi, koma wopita kwa iyewo ndi amene akupenga ndithu…Mujlungu sangachhite kuti tikhale popanda mayeso padziko lino, wamisarawo adzaoneka….Bushiri alibe chifukwa, koma omwe akupita kukapheredwawo ndiomwe ndikuona kuti misara irimo kwambili mumitu yawo….

 86. Koma zinthu zake nzovuta kunena kwake chifukwa ndi mmalawiso ndi kwawo kuno ndiyeno bible limanena zoti mneneri satchuka or kukondedwa kwawo komabe limanena kwa njilaso yoti masiku osiliza zinthu zizatelo lokhaso limanena kuti usaweluze.ndiyeno pa zonse ndatengaposo mawu akuti anthunu muzisamala kunali simon wamasenga uja anasokhanisa ndi kusochelesa ambiri koma atamwalila zonse zii zinatha winaso uja chimozimozi koma ngati uyu ndi olondola tchito yake yizawonekaso mapeto ake.#@fra

 87. Eeetu, ukadwala pamafunika consultation fee. Inu simukuona Pitala akulipiritsa muzipatalamu. Bushiriyu si Yesu, ndi munthu wamba wa business yake. Ma employees ake awalipira ndi chani. Apa chofunika ndi anthufe kuchenjera basi otherwise akuberani mukuona.

 88. Wabizinesi uyu kodi amalawi tulo bwanji osamuuza apite kusentro hospitor uko anthu akumvutika ndiye akunamizeni kuti ndikumphembelerani pali aliyense chikulupiliro mumtima basi izo ndi mbala .

 89. pa bizinesi yake walondola, pot nayenso ali ndi mulungu wakewake, am tellin u amene akupembeza mulungu wa #bushiri will pay [email protected] amount, koma kwa onxe amutxata mulungu wamoyo will b shown d right way. adzaulura onxewa pamapeto, ngat akubona CHRIS BROWN kuli bwanj iwowa. GOD will fynd a way.

 90. Mwina its misunderstand of some pple so do’t against de man of GOD,MUNGATENGE THEMBELELO, NGAKHALE OSAKHDWA ATALAKWISA SMUENELA KUNYOZA, KUMBUKILAN MILIAM NDI MOZES,

 91. mutati mupange kafukufuku you u go find that most of his service attendants are women, komanso tikatengera mbiri ya mau a Mulungu kuchokera mu buku la. Genisis mpaka chivumbuluso mutha kuona kiti women are easly deceived than men can do, nde musaone chachilendo zimaenela kutelo, bajansotu baibulo limati women must shutup before men. Nde bushiri mpake kumawanamiza azimayi athuwa.

 92. 1 Timoteo 6 vs 10: pakuti muzu wa zoipa zonse ndiwo chikondi cha pandalama; pamene ena pochikhumba, anasochera,nataya chikhulupiriro, nadzipyoza ndi zowawa zambiri.

 93. Good but mukaone kwa JIMMY SWAGGANT [ SONLIFE TV] amagulitsa zithu zingati and ndichani anthu amatenga mwaulele? ali ndi tima buku amagulitsj 28$ kamodzi, alindima dvd amagulitsa 48$. tipite kwa TB JOSHUA anthu kuno amagula anntwater pa 25000 kwacha and pali L MUMBA amagulitsa zithu zingati? Iweyo ngati umapephera bible adakupatsa ndani? mesaudagula? nanga thawi ya yesu amagulitsa mau akewo? Mulibe nzeru zauzimu koma zakuschl zomwe sizingakupulumutseni!

 94. We are Christians and what ever a miracle we may perform is received as a gift from above for free and for free we shall give.
  I don’t knw which chapter from a bible is this man of God telling to sell miracle.
  The bible clearly tells us that freely you receive & freely you shall give.
  May God work in this prophet so that he may realise his wrong doing.
  Amen

 95. Mmmmh paja amalawi muli ndi vuto ntchito kunyoza basi zazii mukhalira yomweyo ndimtima wanu onyasao zikukuipirani chifukwa bushiri ndi wakumalawiko kpma akanakhala wakunja kukanakhala kumusapota umbuli kusazindikira ndinkuona muli ovutika ndi osauka chifukwa cha mtima wa mkhwidzi eishhhhh!!!!.

 96. wina aliyense amene amanyoza mneneriyu alape ngati sakufuni mulungu amene anaitana mneneriyu amulange let it b cased avery work of these wicked people from today,mneneriyu amakhala akupephera iweyo ukunyoza,tell me ur good enough,reiceve ur pushiment to day, malawi osakonda abwino ulindi soka

 97. Business.kkkkkk.Mulungu amatipatsa ife zinthu zambili kwaulele so how come bushiri is he truely worship God or he is using devils power?mmmmmm masiku omalizadi ano we need to pray hard.

  1. koma a prophet mwaonjeza tiziti ufumu wakumwamba ndi ogulitsa?Kumbali ya chopeleka yesu ananena kale zaka esala zipite kwa ka esala za mulungu kwa mulungu,nde iyeyo akufuna kusandatsa church kukhala money maker instead of soul winner,God should 4give you

  2. tamuuzadi ameneyu coz sakudziwa chomwe ali! Musadaweruze anzanu yang’anani zintchito zanu. Inu a Malawi24 ndiangati amakumandaulani? Mumaona ngati mukunena zachilungamo apo ayi! zimene mwalembazo amene adayambitsa ndi mayi wina ndimakwera naye minbus amene akut m’muna wake adamusiya mkukakhala m’londa kwa bushiri iye adali msilikali. zonse mukunena apa ndizabodza and zogulitsa tima frag, buku, ndikulikonse!!

  3. Whu Falce Yhu To Like Dis Page? #wongan
   Atumbuka Nd Atsilu Kumene…2019 I’ll Bi Runng For Prezdent When I Wl Won I’ll Kill O Tumbukaz Who Stay In Southen En Central In Mdubx. Thats Ma Manufesto Lol.

  4. #viclaxi usataye tym yako thinking about things which can’t happen……atumbuka mdiwomwe tikutukula dziko lino…..ndichifukwa chani u don’t federal government ???????? u know kuti atumbuka they will be successful in everything man…..although government ikubweretsa njira zambiri zoti atumbuka asamapite kuma college aboma but we still maintain the position of most educated tribe in malawi……….open ur eyes #vic

 98. Mmmmmh bola sng’anga…iye nde akudya ganja2…mapemphero amalipilixa??…ngat akuxowa doka akalowexo mkalasi…munthu wamulungu amatero…”zopuxa”

 99. Ineyo ndikuti sanalakwitse vuto ndife anthu kuti timumvese munthu zimavuta kwambiri mmalo mwake tikutukwana ndiye akulakwitsa ndidani pamenepo kumbali yanga ine ndikusowa nditakumana naye koma zimavuta kwambiri amene muri naye pafupi chonde pangani zoti ndikumane naye ine olo r500 ndipereka bola zanga zitheke basi sizomwe mukunena apazi mwanva

 100. Yesu Anenelatu Zakubwera Kwake Chiyambi Cha Masauso, Y dnt u jux let him fufill the scripture 4 it was written, so it shall b done. As 4 me am jux lukin 4ward 2 the doomz day

 101. Am not here to point a finger to any one.but what I want to say is that , Just stand constant on what you believe.dont be shaken.follow the teachings you taught .cra finish. but always pray that GOD take me to the right path like you did to all prophates that are mentioned in the bible.

 102. mh…GOD…whea au? Y cant u jst cm? ? open our spiritual eyes and ears so dat we may be able to hear and see both fake and annointed prophets…other wise many wu go astray ….

 103. Zandikumbutsa Ulaliki Ku Utatu Oyela Ku Kawale,

  Ophunzila Wa Yesu Amaletsa Mpolofeti Wina Kuchotsa Ziwanda
  : koma yesu adati, asiye musawaletse, poti nthawi ikudza sadzachotsanso ziwanda mudzina langa amenewa; lelo ndikunena kuti;~ those who is not Against Us Is 4 Us: Mark 9 vs 38~41
  Wadzulo Woti: Ngati Muchita Mantha Kudzudzula Anthu Akuchita Zoipa; Ndithu Mulungu Adzaweluza Ekha: Anthu Mwachita Kufika Podzipatsa Mphamvu Kuposa Mulungu Mwini; Samalani Masiku Omaliza Ndi Amenewa, Mukatengeka Mutaya Chowonadi; Kenako Nonse Wakumoto.

 104. Apa pokha ndilankhulako bcoz if the bible says salvation is free, why some1 is made it to be apayable salvation. Adakayamba kulipiritsa ndi ambuye Yesu bcoz adapanga ntchito yotamandika pa dziko lapansi pano. Tili ndaneneri ambiri padziko pano bt they prefer kuthandiza anthu osatikudyera anthu. This means that salvation is 4 only rich pple nt poor ones. I cannt judge nw bcoz judge of judges wil judge himself that time. God has mercy,grace & love upon us amen.

 105. izi zokha nde mwanama…wat i heard z ma bus omwe amapita ku mzuzu anthu amalipira ma 10grand..not this. kapena mungofuna kumva ma comments a anthu.zaziiii

 106. aaa mpakana malipiro, tidelanji nkhawa ngati tadwala malo mongogwada pansi ndikupempha kwa Mulungu, iye amamva pemphero lamunthu aliyense, ananena yekha kuti ndiyeseni, palibe cosatheka ndi mulungu bola iweyo ungomupempha ndichikhulupiliro, aliponso anthu ambiri anadwala kapena anapezeka ndi matenda koma pawokha atakankhila kwakuya Mulungu anawakhuza ndipo iwo anacila, sibwino nthawi zonse kumangodalira kupempheleledwa,machilitso sagulitsa ndi mphatso yaulele yocokela kwa Mulungu.

 107. musana lembe nkhani muzi fufuza utha kulemba zosangalatsa dziko ndiziwanda koma choonadi ukuchidxiwa ndiwe watsoka kusakha kunamizira mtumiki wake ngat zinaku bowa kunayenera kupeza zako koma pot satana wakugwiritsa ntchito yonama mulungu akumasule

 108. A devil iz a lie i mean bushiri iz a notolias”what knd of prophet is him? Tiziti aliyense amene akufuna kumulandila yesu adzilipila” mot tiyang’ane kwa khristu amene anatifela bas busy worshp the sinner as us..bwnj osangotenga ndalamayo ndkupatsa ana amasiye kapna osowa? Koma ndalama yathu yomwe kukagula ziwanda….nonsese”!!

 109. zaboza basi yemwe walemba khaniyi ngati alibe ufiti ndi mwayi musiye kuwononga mbiri ya bushiri panga zako zokuthandiza osati zowono ngelana mbiri,live my papa alone plz do ur own bussines satana iwe

 110. robt mwalmba sukuvetsa pati abusa amalandila maliplo osati kulipilitsa malipilo ezi ndizachilenda zikutantauza akakhala ndi nsokhano anthu amane alindimavuto osiyanasiyana asanapemphele azilipila!!!abusa amalandila zachopeleka osati kuliplitsa pemphelo.sanaganize bwino!!azilandila zachopeleka mawu amatelo kuti

 111. Vuto anthu onyasa n’kamwa ndinu achigao chakumwera ndipakati, ife tikukuuzani zinthu zoti tikuziona ndimaso, inu makani kakakakak!! Jelasi basi!! Bwerani muzaone ngati angazakulipilitseni aaaaaaaah zikunyasa pano bwanji, kusowa khani eti,,,,,, osamanena za peter ndimene zilili zinthu kuno. Wayiwala chisotso chako chilimasomo bwanji so fast to ur frndz lol bta change end do ur bsines plz! Mzanu alindidege inu or njinga mulibe.

  1. if yu kno u r saying the truth then u dont need to swear(kutukwana). .it wont stress yo point but rather tarnish it..just speak yo mind and let ppo decide whether to blv u or not..its up to them to decide …

 112. kungoti anthu ambiri ali mu mdima wa maganizo,ndipo sakugwiritsira ntchito chenjezo la Yesu khristu la pa Mateyu24 vesi 23 mpaka25.Komatu Yesu pouza ophunzira ake anati,munanalandira kwa ulere patsani kwaulere,kutanthauza kuti sayenera kulipiritsa.Nanga uyu lamuro loripiritsa walitenga kuti?kungoti afuna agule ndege ina,ameneyutu ndi uja adzakanidwe ndi yesu kuti chokani pamaso panga sindikuziwani,Mateyu25 vesi 41

 113. 10,000 ndiyake ya bushir, zamulungu ndizake za mulungu. dziko lapansi kulibe prophet opanga za mulungu, zomwe amapanga ndi njila yongopezela ndalama basi.

 114. Bt do u blive is true?? musathamangire kunyoza, kutukwana, kuweruzaaaaa!!! pezani umbon woona, kenaka comentani. anthu angotembenuza nkhani kut zimudere winaaa!! watch your mouth pliz.Kod olo mumutakwane Bushiri yo, Mulungu akumverani? mupindulanji a Malawi? Lalikiranitu anthu adziwe choonadicho kusiyana ndi kutukwana nde mchikunja akabwera, atolapo chani za chikhristu?? mukamatero mukuonjezera misleading the ppo. Malawi akadali mmavuto.

 115. lets play to God people izizi tichimwa nazo mulungu amaona zonse za padziko nde even bible says dont judge nde kwakukulu musasiye kupepedza mulungu

 116. achamanza osaopa munthu mayaz! koma kuima njiii pa yehova! awo anazolowela kudya ndalama za magaz nde mwina ku mtundu kwawoko anthu atha! koma nanu athu kusiya kuyang`ana kwa iye mwin ndikumalimbana nd sasamba ngat ameneyo! nankha akanakhala kut mulungu anamupasa iyey miyoyo kut azigawa kwa anthu kod enafe bwenz til nawo!?

 117. akamati satana azapanga zozizwa kapena kusochelesa anthu sazabwela satana weniweni koma kupeleka mphamvu kwa anthu a mizimu yoyipa ngat buchili wanuyo.lalikani uthenga wakut,tembenukani popeza ufumu wakumwamba wayandikila