Wilson Banda is the governor of the Reserve Bank of Malawi which is the central bank in Malawi

Kwacha yagwanso

Ndalama ya Kwacha ikupitirira kutsika mphamvu pansi pa ulamulilo wa a Lazarus Chakwera. Banki yaikulu ya Reserve Bank of Malawi (RBM) yalengezs kuti ndalamayi tsopano izigulidwa pa K1,180 pa Dola imodzi ya ku Amerika, kuchoka… ...
Wilson Banda is the governor of the Reserve Bank of Malawi which is the central bank in Malawi

Kwacha yagwa mphamvu

Anthu m’dziko muno akuyenera kuvala dzilimbe kamba koti pali chiopsezo choti katundu wambiri atha kukwera mitengo kutsatira kuchepa mphamvu kwa ndalama ya kwacha ya dziko lino kuyelekeza ndi ndalama ya dollar ya ku America. Lachinayi… ...