Bambo wina wadzikhweza ku Dowa
Bambo wina ku Dowa yemwe dzina lake ndi Kelvin Songazaudzu wa zaka 47 zakubadwa wadzimangilira kudenga la nyumba yake kaamba kamavuto a m'banja. Mneneri wa apolisi m'bomali a MacPatson Msadala watsimikiza za nkhaniyi ndipo wati… ...