“Bodza ili”: Premier Bet yatutumutsa gulu polengeza kuti munthu wawina K639 miliyoni
Anthu m’masamba amchezo ati ndiodabwa kuti kampani yochititsa juga ya Premier Bet yalengeza kuti munthu wina wawina ndalama zokwana K639 miliyoni pomwe malamulo a kampaniyi amati munthu sangawine ndalama zopitilira K500 miliyoni ndipo ena akuti… ...