Boma likuyembekezeka kugawa masikito mdziko muno
Boma lati ligawa masikito otetezera ku udzudzu mzigawo zonse m'dziko muno pofuna kuthana ndi nthenda ya malungo yomwe ikadaperekabe chiwopsezo chachikulu pa umoyo ndipo ntchitoyi igwilika ndi thandizo la ndalama pafupifupi 84 biliyoni kwacha lomwe… ...