
Timu yampira wa miyendo ya azibambo imakondeledwa — watero Tabitha
Mtsogoleri wa timu ya mpira wa miyendo ya dziko lino yomwe osewera ake ali azimayi, Tabitha Chawinga, wadandaula ndikusowa chithandizo choyendesera timuyi. Chawinga wauza nyuzipepala ya Nation kuti dziko lino lilibe chidwi chotukula mpira wa… ...