
Senior Chief Malemia yathokoza chifukwa chowakwezera mafumu malipiro
Senior Chief Malemia ya boma la Zomba yathokoza boma chifukwa chokwezera mafumu malipiro ndipo ati izi zipangitsa kuti mafumu azilimbikira ntchito. Senior Chief Malemia yawuza Malawi24 kuti mafumu andodo a Boma la Zomba akondwera kwambiri… ...