Blantyre urban governor for UTM, Charles Nkoloma, has stepped down from his position and has endorsed anti-government demonstrations. According to a letter Malawi24 has in possession dated 3rd February, 2022, Nkoloma has informed the party's… ...
Gospel hip hop musician, Duncan Zgambo, professionally known as Gwamba and a Rapper Waxy Kay real name Wonderful Kapenga, have engaged in a social media war of words. Fans were shocked when what had started… ...
Moto wawotcha ofesi yowulutsilako mawu ndi zinthunzi ya kanema wa Luntha ku Lilongwe. Malingana ndi uthenga omwe akulu akulu ku wailesiyi atulutsa ati padakali pano sakudziwa chomwe chinayambitsa motowu. Iwo apitiliza kunena kuti motowu wawononga… ...
Chipani cha Malawi Congress-MCP chachotsa a Frank Chiwanda ngati membala wachipanichi akuti potsatira zomwe adalankhula ndi wailesi ya kanema ya Rainbow posachedwapa. Malingana ndi kalata yomwe  wasaina ndi mlembi wachipanichi, a Eisenhower Mkaka omwenso ndi… ...
Minibus Malawi
Anthu oyenda maulendo osiyanasiyana pa Minibasi kuyambira lero ayamba kulipira mtengo okwelerapo kamba ka kukwera kwa mtengo wamafuta a galimoto m'dziko muno kuchokera lolemba. Kalata yomwe alemba eni Minibasiwa pasi pa bungwe lotchedwa Minbus Owners… ...