Malawi Music
Malawi’s fast-rising Afro-Indie star, Issabel King, has released a new banger titled ‘Ku Tsoka’ featuring Refilwe which is talking about reconnecting with people and places that feel like home. In ‘Ku Tsoka’ hit, the sharp-voiced… ...
Prophet Shepherd Bushiri yemwe ndi mtsogoleri wa mpingo wa ECG – The Jesus Nation, lero wagawa chimanga kwa anthu opitilira 1300 mdera la Sub-T/A Nkhanga m'boma la Nkhotakota. Polankhula pa mwambo ogawa chimangacho kudzera kwa… ...
Mtsogoleri wa mpingo wa Enlightened Christian Gathering (ECG) Shepherd Bushiri wati ayamba kuthandiza mwana yemwe posachedwapa anaonesedwa m’masamba a nchezo akudyetsedwa dowe wa muwisi. Posachedwapa, anthu ambiri m’masamba a nchezo anagwidwa ndi chisoni kamba ka… ...