Dan Lu’s wife hits back at critics

Advertisement
Dan Lu

Drama has reached the climax yet again as Emmie Kamkweche has launched missiles at critics for poking their noses into her affairs.

Dan Lu
Dan Lu and wife not moved with epic pregnancy picture.

Emmie and her husband, celebrated musician Dan Lufani, have become a topic of discussion for exposing pregnancy in public.

On Friday Dan Lu posted on Facebook a photo of him and his wife in which he lays his hands on her half-bare belly.

Recordings which have gone viral on social media shows that the issue has taken a different angle with Mrs Lufani being the main character.

In her response to the critics she targets a woman only identified as Chisomo for playing a cheerleading role in attacking her.

She plainly tells this Chisomo to mind her own business because what she did does not concern her in any way. Emmie adds that Chisomo can’t stand the heat if they take on each other.

In another recording, Chisomo the victim of Emmie’s rants plays heroin with more attacks on the Lufani’s for what she calls an act of indecency.

She argues that in Malawi there are rich celebrities who have never done such a thing.

As the story continues to unfold, Dan Lu has been quoted by the papers having said he is not ashamed with the matter.

He is patiently waiting for his baby anyway.

Most Malawians believe the Lufanis have violated cultural norms by exposing to the public something that should be kept under cover.

Advertisement

524 Comments

 1. Iwe Dan lu ndiwe wamisala kwambili mimba udawonandani akuyiyanika pantunda chonchi ngakhale amayi ako adapangako zimenezi ndiwe galu wamuthu osamaziyambadala kuti uwone anthu alakhula chiyani mbuzi iwe zanyasi

  1. Eti unuuu, a Malawi tili ndi vuto. Mind your own business. Kukonda za mu mdima basi.

 2. That’s the unfortunate part of exposing yourself. Your expose yourself you invite critics. So I think Dan-lu and wife invited this wrath that has befallen them. Why go in the kitchen if you can’t take the hit

 3. most of the people insulting this couple are hypocrites!who are u to judge them as if your God.machende ako ndi amako ngati ukumutukwana dan lu ndi mkazi wake!galu

 4. Galu ameneyi atinyasa eti mamuna wwkeyoso mzeru alibe akukhala ngat koyamba kunyenga bwanji kumalora zimenezo mimba mchaniso tapele

 5. Amangova kuti anthu amawonetsa mimba koma kuti ufufuze ma celebrity mukunenawo zimenezo amawonetsa ku Advert ,mabukhu azokhuza pregnancy and amalipiridwa

 6. Ameneyu akazamuona mwanayo muzandifutse ndipo wofunika kupanga zokuti akhale zaka 5 asana bereke ameneyu azingoyiona mimbayo anthu wopanda zelu sindinaone anamusiya mkazi wabwino kukatenga hule wopanda ntchito ngati ameneyu ndichifukwa samabereka chinali chosabereka kani ndikuyamba kumeneku

 7. onsewa ndizitsilu mwamva koma? ndisadzamvenso nyasi ayi apa.

 8. umuthu wavutapo apa asisi, mamuna sayaluka ulemu umadzipatsa wekha evn ntakhala nkazi wacelb icant do dis.kwathu kuli anthu dey always advise me…its the same akatsata ucelb ayenda mbulanda …respect us women if u cant respect ur self..get lost

 9. Awonetsenso zomwe ankapanga kuti mimbayi ibwere. Tione each stage from the beginning till the end, that is mpaka kobereka, mmene adzikaberekeranso.

 10. I think Dan Lu sakukhulupilira kut waperekadi mimba after kukatenga mankhwala kwa sing’anga monga muja tose tikudziwira kut mnzathuyu anali ndivuto loti samamera fupa mkabudula mkona banja lake loyamba lidavuta

 11. A Malawi bwanji nanga? inuyo simungaganize nokha kuti man DAN LU mimbayi siyake, anakwatira wa mimba kale uyu thats why akufuna anthu tiziganiza ngati ndiyake kkkkkk koma GOJO uyu ativuta bwanji!

 12. ma comment tikulembawa ndiamene akupangitsa kuti thiz two pple shld continue posting thoz 4toz had it bn dat we r not commenting even a single comment thoz bad manaz shld stoped that stuppidty plz be WARNED DONT COMMENT anything.

 13. Rights should be depicted concurrently with responsibility. I guess this is pure garbage and immoral to the cultural house

 14. Kkkk kodi emmie nkulukuluyu mimbayo ngat ndi yoyamba? kapena amadikila Dan akamazamangitsa mu saloon mwake nde azamufusile ndikupanga izi kufuna potchukilapo. Potumiza pa public mesa amafuna anthu aone akaona ayankhule nde akulusilanji amayiwo? Amafuna anthu aope kuyankhula zili nyasi? Sitikuletsa kuti ndi celebrity koma aziona komwe ali ndikomwe akuchoka chikhalidwe chake, chifukwa choti mamunayo amaimba nyimbo zangat zaku Nigeria chisakhale chifukwa chobela chikhalidwe chakumeneko ichoso nawo ndi chikhalidwe amalekelanji kuvala moonetsa chikhalidwe chaku Malawi? osamangoti awa sioyamba ma celebrity amapanga, ku Malawi anapangapo ndi ndani kupatula maiko ena? Tisamufanizile Malawi ndi maiko awanthu ena, osamati mind your own business ngat kuti pali anawajambula mokuba ndikutumiza chonsecho anatumiza okha kuti anthu aone ayankhule, anyway poti mimba taona plz osaiwala kupanga vd record pobadwa mwanayo muzationetse, nanga patsala pati?

 15. As far as am concerned these guys are not involved in Maize gate, Cash gate nor corruption. Malawians we need to focus on issues that will benefit our nation not pointing fingers on who is living righteously or not. We have bigger issues as a nation let’s not aim at criticising each other and hiding under the leaf of culture. You must know that there is no book that says what Dan lu did is against out culture coz we have so many cultures in Malawi there is no such a thing as Malawian culture. The only culture I think is in Malawi is stealing. Plundering resources,corruption,cashgate,maizegate etc those are some of the cultures in Malawi as far as am concerned

 16. Winawu ndi umbuli coz myb zayambila pa iwowo komaso amujambuletu akubeleka mkaziyo kuti nafeso tione, izi ndi zausilu hvy and afiti nawonso amatenga advantage pa zinthu ngati izi. Zauchisilu man a Dan Lu ndi mbuli yothelatu.

 17. Hahaha akanakhala kuti alibe mimba kunvala choncho ndikujambulisa video anthuni bwezi mukusekerera kuti video ya dan lu chikazidzi chinakongola asiyireni eni ake izi anthuwo si inu ndi ma celeb nde si mungafane zochita

 18. Kodi alakwadi chani photo yo ngati amayenda mmisewu mkumaonesa tawasiyeni athu ndi ufulu wawo ngati palakwika bwanji sanakawamange

 19. uhuuuuuu Malawi walelo ndekuti tinene kuti iyiso ndi technology yokhayokha kapena uchisilu wainu awili?komaso amayi ngati ameneyo akulilamo tinene kuti aka ndikoyamva kukhala oyembekezela kuti azitilawula?ndikwabwino mupite kunja muzikapanga nyasizi musati onengele ana akamaona uchisulu oyambila kumakolo anu opanda mwambowo ,ndekuti mwambo munalandila kuukwati ndiumenewu?I hope izi ndizapasi panyanja mmmmmm shame on

 20. Zinthu zikusintha, anthu sankayenda mbulanda koma lero azibambo akusilira mwendo wamwana wao chifukwa akt chitaun kikikikikiki Ndiye awa akatenga ziwanda zaku Nigeria

 21. I thought after all the accusations they could come openly and say they are sorry for what they’re doing? Unfortunately they are also growing wings which truly confirms how arrogant and selfish they are, and now I doubt if these love birds have parents whom they respect and get advice from. They will truly regret for their selfish behavior

 22. ndie muzidziwa tsapano kuti munthu akalowa mu music industry. amaphunzira zonse including uchitsiru. why he sold his soul. he never mind what eva happen. shame to those who are in de same spirit. my almighty GOD will punish u coz of dis. damn..!

 23. Kawilikawili mukadzaona anthu omazionetsela chikondi chawo pagulu like kissing n whatsoever in public areas just know that they are just pretending koma kukhomo kwaoko they don’t get along….chavuta apa nkuzikayikila

 24. Kodi simukuona kuti anthuwa Ndi oyera? Posakhalitsapa akhala azungu. Panopa Ali mkati mopanga training zachizunguzo kuti akadzakhala azungu Eni Eni, asadzavutike.
  Koma wakuda ngati ine, kupanga zimenezi sindingakwanitse. Chifukwa bambo wanga kuona chimimba cha akazanga ngati chonchi, angawelamire pansi ngakhale mimbayo ili pachithunzi.
  Koma ngati kuli kuyenda kwambiri Maiko achizungu. Tsiku lina tidzaonetsedwa mmene kukuonekera Ku Jehena ndithu.

 25. Chifukwa chan magule a chikhalidwe chathu ovina samavala kubisa thupi lonse? Chimenechi ndiye chikhalidwe chathu mwamva kaya.. Colonisation idakupangitsani kusiya kutsata chikhalidwe… Chifukwa chake mukuziona zofoira..

 26. Zimayamba ngati boza, Poona ngati ndi ufulu wadziko mwaiwala kuti ziwanda zimagwira ntchito kwa anthu. Mwaiwalaso kuti muli ndiudindo ozilemekeza ngakhale muli ndiufulu wathupi. Zimakhala zovuta ngati mwana Ali hule kuti alangize mwana wake kuti uhule ndi onyansa pamene iye ndihuleso. Choncho zili ndiiye kuvomereza kuti wachitazi ndizonyasa pamaso pa mulungu komaso kumtundu was amalawi pa chikhalidwe. Sizinasiyane yemwe akuonesa anthu maliseche ake poti mimba ndichobisika pa chikhalidwe cha chizimayi.

 27. she doesnt knw hw malawian get angry ukawalakwira uli nd mimba she jus need to punish mwana osabadwayo coz atha kumpasa over stay for 2yrz osachira or kubala mwala

 28. ine sinduona chomalalatira pano coz sizoyamba. aximayi ena apa akulalata koma iwonso ali ndi khslidwe lonyasa lomaonetsa ziwalo in the name of kuflasha,kuvala zominula,dindadinda shape yonse kuonekera. azimai oteroo asayese kuti zinangobwera oyamba kuchita ananenedwa koma pano kuvula kwasanduka fashion. kuteroku tsogolomu izi sizikhalanso zolaula. anthu ochimwa okhaoka kunenana.yamba kuchotsa chitsotso chili mwako. get a life people

 29. Emma sayz de truth,how does tht affects us anyway???…mimbayo ndi yao,plz plz special request fellas,alipo ali ndi nyimbo ya billy kaunda ija imati,”kunena za ena”,

 30. mkaziyu ndi bitchi wachabechabe,and zaonetseratu kuti mimbayi si ya Dan Lu,anakatchaitsa penapake. Zikuonekanso kuti mwamunayu ngosabeleka kapena kuti gojo coz ikanakhala yake sibwezi atapenga chomwechi. Tapatsapo mimba ife koma sitinalaulepo dziko like this stupid and rabish family,mxiew

 31. we see alot of mimbaz in town, who tells em dat its against our culture?? ma mini amakhala akuyenda ntaunimu simumawaona?? simumaona cholakwika. now someone appreciates his wife and gives her the comfort dat he is indeed wit her thru out, and u busy here kumunena munthu. why cnt u jus acceptdat our culture is evolving?? do u really think tizakhala ndi mentality ya culture imeneyi mpaka 10 yrs frm nw?? accept wat z, those who r criticising these guys are mor stupid than i thot, musiyeni munthu ndi nkazi wake, they werent having sex in public, were they?? so go mind ur ownn damn business anthu osowa chochita inu,assaaaaa

 32. Mmm koma ndiye timva madzi2,kondi mmesa Emma amayimba gospel?kamimba kokunamiziranikoso mutinyase..we gat best artist in the country who also married 2 vry beautfl wife bt samapanga nyasi izi..muti size ya America eni akenu?

 33. But this is childish and foolishnes…. are they the first to impregnate each other?? Should they be exposing their nakednes and bellies here…… I have never talked harsh but its time we dont get carried away with technology

 34. Nchifukwa chake ndimakonda oyimba akale aja basi,Tembo,Kaunda,Mereka,Paul and soldier Banda,nkasa,Rod Mvalam’manja ndi wena akale izizi izi ayi,sindilimbana nazo ,bola kale ndithu apo bii zimbabwe alowe m’bwalo basi fumbi ……..kkkkk

 35. Chomwe mungadziwe usilu samagawana. Zinthu ngati izi aku tengera maiko akunja. Mzimayi oyembekezera mimba zikumakha la panja, kuvala mosazilemekeza. Kwaiwo sakuona vuto. Tsoka mtunda ndi nyanja poti simukudzi wa ali mbali iti?. You know what I mean musazitengere izi.

 36. kwaamene amatsatira anthu aluso padziko pa sanadabwe ndi izi.kuti munthu upange dzina ngati ku maiko akunjawa amapanga kauchitsilu kena kake.apa nkhani yakula poti Dan Lu timadya naye nsima koma akanakakhala kuti ndi Beyonce bwezi nkhani ili yoti iiii beyonce ali ndi mimba ndaona pic yake.ndimene wafunira mwini wake onani mavuto anu abale

 37. kwaamene amatsatira anthu aluso padziko pa sanadabwe ndi izi.kuti munthu upange dzina ngati ku maiko akunjawa amapanga kauchitsilu kena kake.apa nkhani yakula poti Dan Lu timadya naye nsima koma akanakakhala kuti ndi Beyonce bwezi nkhani ili yoti iiii beyonce ali ndi mimba ndaona pic yake.ndimene wafunira mwini wake onani mavuto anu abale

 38. as fellow student at Thandizo pvt seco xool , am very sorry Emmi, this is not ON and its ashame. mene unali ku xool ungapange zimenezi. we lady we are specially made by God and we dont need to expose our body to anyone. Guys !!!! the hear me out . where do you find god and diamond? deep deep down the ground and its not easy to find god as u its expensive stone. we ladies we are god . we need to make ourself expensive for the godminers!!??????

 39. Kodi chi tawn chimene munenachi chilipati muthu mimba ngungungu chomchi pagulu ndikumati chitauni. Muudzeni dzanu chilungamo chingakhale amve kuwawa koma chilungamo achiziwe .

 40. malawi still sleeping shame on u guyz. this is 2017 not fucken 1890 wakeup gyz this is development can’t u c, kuzolowera chikondi cha mumdima basi

 41. Guiz just keepit noise” palibe cholakwika apa. Ndi fulu kutero kodi ngati dan walakwa bwanji a police sadapite Ku mtenga m’ kusekera Ku chitokos mmm’ amalawi amalawi inu ndi amalawi basi …kodi mukuti chinkhalidwa mu chaka cha 1892 mukundiwuza kuti dzinkhalidwe zinali chimodzi modzi? Tiyeni tisegule matso athu osamango satira zomwe zakalezo. Things is chingeng ich and Every day’ palibe cholakwika apa sanaphe munthu dan. Tikayenda town muno azimai akuyenda mbulanda what more dan and here family yemwe zamunyatsa atenge ufa ayanike pachigwe!

 42. keep doing dat my friend mulemera en mwanayo akabadwa mukapereke ku satanic kwanuko,,mndan sakudzwa abt yo join to illuminate kkkk tyee nazo imbwa iwe

 43. Dan Lu where ever you are please advise your wife that we people commenting here are your customers. Ndiye akachulutsa kubweza moto next album ungazaone zomwe anaona Limbani Banda. Ife ndiye ma Bwana anu.

 44. dis is shit couple of love ihave never seen madness love like dis they should respect themselves not like dis publicaly mayb there is something they knows each other

 45. TIYENI TIDZINGOYANG’ANA ABALE,MUKAZITENGERA NDIYE MUSINTHA ZAMBIRI.TIKUWAWONA AZIKAZI AMAPASTER AKUYENDA MWENDO POYERA AKUTI KUTCHENA,NANGA MMASUKULUMU NDIYETU MUTHETSE LIFE SKILLS.BOLA INU MWAWONA MIMBA KOMA ANTHU AMACHITIRA CHIGOLOLO ANTHU ENA AKUWONA, OK CHABWINO ZAMASIKU OMALIZA IZI.

 46. The time u wasted here talking about Dan lu you would have discussed something reasonable helpful to MW not them….why is it that you voice out your views on senseless things unlike things that have benefits……Will the pregnancy benefit you anything and you say MW is poor you yourself pple your are poor in reasoning wake up MW

 47. mimba zobwera chifukwa cha nansula amajejema nazo choncho koma kwa amene amabeleka kopanda khini sangapange zimenezi kkkkk tunthumbo twachimika ninthena wanthu wakunjenjema nato and i think ukanjira fisi umu hokoyo take cover.

 48. That’s ataboo according to our castom & culture….l due respect a pregnant woman…un a expected woman (mai wapakati or mai woyembekezela)wapakati =coming from labour room dead or alive….woyembekezela=expecting ababy but either dead or alive….with all this ….that’s why we Malawians give respect to our pregnancy lady’s…we have to respect them, we have to take care of them ,….& cerebrate with them after labour time….comfort them once the outcome is bad…but not expose them to the public…..that’s foolishness..

 49. Ndikangomuona Dan ku mangochi kwathu kuno ndimugenda wativula salu athu akumangochife ….
  Tikhanyadira kuti tili ndi muthu widziwika ku mangochi koma mmm watipanga chipongwe che LUFANI

 50. koma fazi simukuwona kuti anthu amenewa akungofuna potchukilabe? pamenepatu anyozetsa mwana odzabadwayo chidzakhala chitozo pamaso pa anthu ena komaso ena atha kupezelapo mwai kwapanga chipongwe osadzabereka mwana pena pake pofuna kupanga zinthu zimafunika kumaganiza kumakhala ndi umunthu ndibwino osati nyasi mwaika apazi.

 51. By posting the pic of the pregnancy on social media she made it our bussines we ar suppoz to comment on how we feel about it.so asalusepo apa isaa!people have different views on issues like this one’s so let pipo talk.

 52. Apa kungoti zinangokumana zozelezeka . Hule ndi hule amamanga banja ndipo limakhalitsa. Sindisowanso kumvera nyimbo zake dan lu. Malawulo enieni awa.

 53. Let the couple do what ever they want… 1+1=1banja. Enafe we can’t kiss our spouse, coz chikondi chidazirara.

 54. Mubanja lililonse simulepheramo kukhala chitsiru chimodzi,kwa mai ndi bambo Lufani chitsiru chawo ndi Dan,chimodzi modzinso ku banja la a Kankweche nkhumba yawo ndi Emmie

 55. Yesu akubweladi posachedwa mukazaona chonyasitsa chitaima pamalo poyera dziwanikuti tayandikila kwathu Malawi kweza maso ako chionongeko chayandikira odala amene awelenga mawu nazindikira nyengo ndi nthawi yomwe tili.zikamachitika izi zopanda ulemuzi zoononga maso pozipenya ndikuvetsa kuwawa make khutu poziva zikutiuza kuti nthawi yatha yesu Ali pafupi kwambili kudzaweluza dziko.langa ndi fuso kuti muli mbali iti?popeza njila ndiziwli basi yopita kumoyo osatha ndi yakujahena uzisankhile wekha.God bless Malawi Amen.

 56. People what u mast know zikusangalasa mukamabwebweta zaiye this why azingobwera ndi zake apa mukupatsa mangolomera tamusiyani azipanga ndizake zimemezo

 57. Mwasiye anzanu azipuma chikondi chao chapitilila pa lv mukusewela ndi ma super star wo kudya kwao kumeneko kodi inu miseche bwanji pangani zanu osakhalakujeda anzanu zimenezo mwayamba kuziona lelo?mungozolowela basi

 58. NDIPEPESE MAKOLO ANTHUWA KUTI PEPANI MAKOLO MUNABELEKA MUNATAYA NTHAWI POBELEKA DZITSILUDZI DZOMWE DZACHITITSA MANYAZI AMALAWI AMBILI

 59. Zilikuno eee sungazivetsa. Zidatipeza titakalamba amake a Dan lufani ndi amake a esmie akuombera mmanja mwina akakhala chitsiru Makolo nawoso amakhala chitsiru

 60. Zimatero ukakhala ndi kamtima ka uhure.Suyilora kuti wina akuyalutse potengera kuti nawenso ndi woyaluka.Pamakomentsi omwe ine ndidawerenga zikuwoneka kuti anthu ambiri sizidawasangalatse nyasi zija.
  Pamalawi pali anthu ambiri okondana komanso otchuka kuposa kabanja akaka.Koma sanapangeko nyasi zoterezi.

 61. Awa asatinyase nako kamimba kawoka kodi ayamba kutenga/kupereka mimba ndi iwowa? Ngati uli u celebrity mwautengera pamgong’o

 62. This is what we call real life..even my wife when I get married we will be doing such kinds of enjoyments to show to the world that marriage is all about happiness..Make your wife feel at home always ..Dan Lu I like this.

 63. Zimateno umunthu n umzimu ukakuchokela,ngakhale anthu atamakulangiza kuti izi ayi ndizolakwikwa sumava reason why wisdom n spirit in ur mind u dnt HV.kusiya MkaZi wabwino ndikumatenga amkazi opengawa azitilawula APA.kodi MkaZi wako uja unamuveka phete uja analakwanji ndipo mimba imeneyi ikadakhala idali ya iyeyo CRC akadakana kunjambulisa picture yowonesa mwana waphepoyo ngati Mene ananenela wamkulu San B.

 64. Mwina mutawafufunza bwino bwino kuti ukwati wawo anatengana bwanji? Akanakhala ndiwumunthu chidzudzulo choyamba chija chinakwana sakanachitanso. Koma awa anthu chilipo akufuna iwo akungonamizira mimbayo.

 65. Ine mimba yoyamba ya mkazi wanga ndinali more excited kuposanso Dan yu koma sindinafike apa. And ena mukuti ndi ma celeb kulitu anthu otchuka olemela koma sanafikepo apa. Ali ndi chani awa. Mnyumba mukangokomana zitsiru zokha mapeto ake ndi izi. Mkaziyo umunthu ukanakhalamo sakanavomeleza zopusa za mwamuna wakeyu poti woyaluka kwambiri ndi iyeyo. Nanga mkazi kumangomulonda mwamunawake ku ma show si uhule umenewo? Achina Billy Kaunda, Lucius Banda sanapelekepo mimba? Kapena ndi opusa iwowo? Pokhala mimba yoyamba analangidwa anthuwa koma? Mkazi ukazilemekeza anthunso amakulemekeza. C V ya mkazi uyu yachoka marks. Ndipo muthokoze poti afiti ambiri sali pa Facebook, akanachiona tikanakuonelani mapeto ake anthu osavinidwa inu.

 66. Komanso momuja a Dan Lu anali kuti mimba yokapeleka pano siyawo fisi analowa nchifukwa akumayilemekeza mimbayo komanso mayiyu has got mentality prblm kodi anampeza kuti sakudziwakuti kuyalusa Malawi culture kumeneko

 67. Koma atati mkaziwako wapitilila ungayaluke kumzinda wamalawi chifukwa palibe alukuona ndi ubwino pazimene wapanga ayi.nde poti mimbayo achita mokupangila azako oyimba ayi njoya wapeza chomwe umafuna.

 68. Koma zinazi osamaziyamba dala kuti anthufe muzitipezera machance Ndiyambe ndi iwe mwana wa KAMKWECHE”: are you a gospel singer Tikudziwa! Nanga zomwe zapangidwa apa zikutanthauzanji?? Nawenso Dan Bambo ako ndi A Busa anakulorezani kutero kuti mupange zowolazo?? Iwe Emmie sakukudziwa ndani my BT kuti ndiwe customer care pa casino ?? Apa palibe zomwe mukuchita amayi ako uwafunse kuti” kodi Mimba yanga munaisunga bwanji, I think if amai akowo amagwira mutu bwinobwino akuwuza zonse, nawenso Dan utipeze kuboma kuno tiwafunse A Lufani ngati izozo anapangapo mbuzi iwe eti how can a sense man mkuzapanga zinthu zosakhala bwino, ngati ukupangira zopangira Moira wakowo Mulungu akhale witness paizo koma if you r doing that kusangalatsa satana aaaaa azabereka Fuwa ameneyo anthu ochititsa manyazi. Naye EMMIE KANKWECHE ngat umalola kuti muziyalutse pa media pano apo ndie mwaitha koma just know kuti from today Nonse kuyambira ma relatives anu ndinu a #Satana I mean it

 69. Ndi ufulu wa munthu kupanga chomwe akufuna pa umoyo wake oro kugonana pamseu mamuna ndi mkazi wake palibe vuto ndi ufulu wawo anthuwo

 70. A Dan Lufani why are you too pompous??don’t you know that your so called wife is a prostitute??mumadzitukumula muli ndi chani inu,,tazizipatsani ulemu.ndi mkazi wonyadila ameneyo.kufela kuyela kophodako.za ziiiii!!!!

 71. Inesotu ndimaona ngati Dan lu ngozelezeka Ngakhale kutu nyimbozo Inde anaimba bwino Koma sikuimba kokha komwe kumapangitsa munthu kukhala munthu wa zeru mmakhalidwe a munthu..chimene chidapangitsa kuti akondane ndi umagineti okula mosowa malangizo amakolo or mwana akubwerayo adzakhala patapata okana sokosi

  1. Mayiwa amakakwera pa stage nkumamuphyophyona mamunayu ati chikondi cha private ku guru LA anthu ati wina zomuwawe manga ziwawa tosefe?nde umbuliwo nanga ma band members Ose Atati azikazi ao azikawapukuta akaimba ingakhaleso show yao yapadera

  2. Uchitsilu. Its just like taking your wife out to a public place not knowing that half the people there actually slept with her at one time or the other kkkk

 72. Mahule akwathu kuno awa nkadz wazeru sangalore kupanga zausiluzi kuziyalusa komanso nae mamuna amayenela kupasa ulemu nkaz wake not zausiru zmene apanga apazi kukomedwa ndzaziko znjoyi….

 73. Dan what you have done is total abomination and it is contrally to our culture,wemen deserve respect….my brother you need 5 tins of Doom for deliverance.

 74. Hahaha mimba yomweyi anzanu azitenga ndikuzipeleka ndipo anatopa nazonso inu ndiye mukuphunzila kupasana mimba eti? Shaa! aDan Lu mwakuliramo simunapelekepo mimba eti kuteloko mukuyamba? Ndiye ngati mukuyamba mimbayo siyanu man, Shaa! Inunso a Emmie Kamkweche mwakuliramo palibe anakupatsanipo mimba? Shaa! Ndiye mwakumanatu a Mental nokhanokhatu inu ndiye ndi zomba zomba hospital ndithu.

 75. #PoTI_MU_BOOK_ZINALEMBEDWA_KUTI_ZOLAWULA_ZIZATSANDULIKA_KUKHALA_ZOPAMBANA_NDIPO_ZABWINO_MKUKHALA_ZOIPA_MATSIKU_otsilidza tsoka mtunda ndi nyanja poti oipa watsikira konko #we_living_in_last_days

 76. AM NO LONGER AGAINEST YOU EMMIE.AM JUST CONCERNED ABOUT WHAT KIND OF A MAN IS YR HUSBAND BCZ I BELIEVE HE IS THE ONE WHO HITS THE FANS WITH BAD EMERGE AS HEAD OF YR MARRIAGE

 77. IF DAN LU AND HIS WIFE DID N’T WANT MEMBERS OF THE PUBLIC TO POKE THEIR NOSES INTO THER FAMILY’S AFFAIRS THEN THEY THEM SELVES WOULD N’T BRING THEIR PREGNANCY ISSUE TO THE PUBLIC IN THE FIRST PLACE. STOP PROVOKING PEOPLE BECAUSE THEY ARE THE BOSSES FOR DAN LU. THEY ARE THE ONES WHO MADE DAN WHO HE IS TODAY.WHAT KAMKWECHE IS DOING IS KILLING HER HUSBUND’S MUSIC CAREER. IF MALAWIANS SAY WE WILL NOT PATRONISE DAN LU’S SHOWS IT MEANS NO FOOD ON THE TABLE FOR KAMKWECHE.

 78. IF DAN LU AND HIS WIFE DID N’T WANT MEMBERS OF THE PUBLIC TO POKE THEIR NOSES INTO THER FAMILY’S AFFAIRS THEN THEY THEM SELVES WOULD N’T BRING THEIR PREGNANCY ISSUE TO THE PUBLIC IN THE FIRST PLACE. STOP PROVOKING PEOPLE BECAUSE THEY ARE THE BOSSES FOR DAN LU. THEY ARE THE ONES WHO MADE DAN WHO HE IS TODAY.WHAT KAMKWECHE IS DOING IS KILLING HER HUSBUND’S MUSIC CAREER. IF MALAWIANS SAY WE WILL NOT PATRONISE DAN LU’S SHOWS IT MEANS NO FOOD ON THE TABLE FOR KAMKWECHE.

 79. What this crazy wife and her showy husband have done portrays the cultural aspects of our society. Therefore it is unfanthomable for this senseless lady to expect people not to react. She must understand that there are alot of Malawian musicians who have achieved alot in the industry but none of their spounces has done this. Why? It is extremely worrisome that she is hitting back. May be they met in a bar. This is not Malawian. What do her fellow ladies say?

 80. AMalawi pepani ntundu wanga umbuli utipha Dan ndi wotchuka ndiye akupanga zinthu mogwirizana ndi ucerebrity wake inu simukumuziwa kuti ndiwoyimba kkkkkkkkjk

 81. Komatu Adapangisa Ukwat Mu Church More Over Bambo A Dan Lu Ndi Mbusa Ku Mangochi,, U See?? Thats Y I Dont Go Church Muslims Are Better

 82. Nsanje mipanje ndiyomwe inakula kuika mimba pa Internet ndikufuna kwake munthu ma celebrity ndimomwe achitira sizachilendo izi mind ur own business guys mungochedwa kukamba za mzanu apa salute Dan lu

 83. These kids they are full of nonsense alibe mwambo ana amasiku ano mwina anawauza choncho Ku u satanic kwawoko inoder to get rich

 84. Umwini ndi umene wavuta. I have been watching ma show for so many years but I have never seen a musician’s wife kumakakwera pa stage nkumakampukuta thukuta mwamuna wake akuyimba. Should we say oyimba ena onsewa ndi ma bachelor? Thats when I noted that something is wrong with this couple. Its either amayiwa amadzikayikira or palibe otsogolera mzake nzeru.

  1. Mayi aja amakhala kamoyo koopa kulandidwa poti nawonso anachita cholanda. Inu munazionako ku show zoterezo? Oyimba enawa we have never even seen their wives. Akuti marking the terrirory. What she should know is akabereka mwanayo, afune asafune, Dan akadyabe kunja basi

  2. iziso nde zabodzatu. kumpukuta mamunake thukuta ikhale nkhani ? amalawi mumangofuna zinthu ziziyambira kwa anthu ena tidzingotengera . shame Malawi

  3. MWIKHO is when you give a lift to a beautiful girl and she faints in your car. You take her to the hospital and the doctor says she is pregnant and congratulates you that you will soon be a father.
   .
   You shout that you are not the father but the girl insist that you are the father……
   .
   Things are now getting MWIKHOFUL you now require a DNA test to prove that you are not the father…
   .
   Things become MWIKHOSTIC when the doctor comes with results saying you cannot be the father because you are infertile…. You are relieved but on your way home you remember you are married with three kids at home!…..
   Now you are extremely MWIKHOUS
   .
   Now you begin to ask yourself who is the father to those three kids?… Now you get home to find out the father to those kids is your gateman…
   You are now MWIKHONED
   .
   YOu then decides to go to your mum to tell her the sad news… Your mum with tears running down her cheeks tells you ‘my son I’m so sorry….your dad isn’t your real dad’…. Then you know things are MWIKHOCATED
   .
   And if you dont LIKE this you are a MWIKHOCRIOSIS

  4. There could be something very wrong with this couple.The love being shown to the world may not even exist.Evidently,the love is stage-managed.

  5. Nkaziyi ife tinamvesedwa kuti ati ndi njinga yoti aliyese ali ndi pump akhoza kupopa ndi kukwera ngati yaphwa!. monga panopa sizingatheke kukwera nanga siyakhuta/mimbayi. koma akachira muthu akhoza kukwera kkkkkkkkk.

  6. Iv seen many shows in my life from all over the world, I don’t see anything strange with mayiwo kupukuta thukuta amunaawo. Ngati those other musicians wives don’t do it so what? Do what makes you happy not because other people are doing it or not doing it. Don’t live life to please other people, live it the way u feel is right. If they love each other and they wanna show it, let them. It’s called PDA public display of affection. Whether there love is fake or not it’s there business. There not hurting anyone

  7. Anthu omwe akuvomereza izizi osadabwa Malawi anazolowera kulambira munthu wachuma ndiodziwika olo awatukwane kusekelera kuli kupepera,,,,mayi wamimba akulu akulu amati “wodwala kapena wapakati” vulani chibwanacho chondee

  8. Anthu omwe akuvomereza izizi osadabwa Malawi anazolowera kulambira munthu wachuma ndiodziwika olo awatukwane kusekelera kuli kupepera,,,,mayi wamimba akulu akulu amati “wodwala kapena wapakati” vulani chibwanacho chondee

  9. Kuvala zovala kudabwera ndi azungu… Chikhalidwe chathu samkavala zovala an2.. Chifukwa chake magule a chikhalidwe anthu ovina amavala moperewera… Tidadziwa kut kuli zovala after colonisation

  10. Ayi ichi ndi chikuwawe kwa first wife paja sanabeleke naye mwana and nkhani yawo itapita ku court ankazi ananena kuti abambowa sanagule nawo chilichonse, everything was inherited from her parent kupatula fridge ndi screen ndi zimene anagula ali ndi bambowa nde ngati pali kugawana katundu agawane screen ndi fridge.

  11. Kuzolowera kupempha amalawi, mkaz yu akuona ngat aliyense amawerenga za ako mukut ka danlu ko..mwana amakhalako ndi mbalame iwowa ndi ndani? Anthu ali ndi ana leveni…

 85. We have hearld alot. Jst let them do what they want. Am not supporting them, neither am I against them. I think there are more better things u can b doing. We have financial/food crisis in this country. Why not talking abt these things? Plz, stop giving us updates about them. Let them read their life the they want

 86. kaya zawa izo, azionetse mimbayo ngati afuna, sindikuonapo vuto kwa ine Azimayi ndi atsikana onsewa akumaonetsa michombo pa mtunda town umu, ena akuonetsa matako nde mimba ndikachaniso,, plus mwangona pic yokha, tikuziona ndimaso anthuwa town atsikana akuonetsa ma pant ndi michombo, ndie mimba ya mkazi wa Dan lu isakhare nkhani ayi, za ziiii

 87. Asiyire generation yapanoyi zimenezi iyeyu ndi ife ndi m’bado wakale. Zikubwera mochedwa izi zikutioeza titakura kale chonde asiyireni ana amasiku ano ife zathu zinadutsa kale

 88. Waziyalusa yekha zobisika zaonedwa ndi mwana yemwe sangakulemekedze Emmie.iwe ndiye zintchito zako zija suzasiya ai ndimaona ngati wakula popedza uli pabanjatu,koma poti wachache ndi wachache ziziyalusa,poberekanso uwaitanise atola nkhani ajambule mwana akutuluka ku sanjika kwakoko.

 89. Zmenezo ziri m’malamulo astanic pamenepo akupanga boost fame times2..osasilira zopusazi iyeo ngat m’malaw apange manyaz

  1. Munthu osabeleka ndidelo mimbayi siyake Dan lu, za ena ixi mamuna weniweni sachitaphuma ndi mimba ngati ngati amagula

 90. taona akazi ife okongola,akhala nazo mimba sanapangepo izi,,,Olemela oyimba tawona ena tikuwadziwa,atenga ,aperekaso mimba sanapangepo izi.Izi zaonetsa Kut Danyele Lufani ndichitsilu chokumwa madzi aBibi.iyeso Mkazi ndichithaphwi chovomelezela ndi za ugalu zomwe.Ndamvela ka clip ka hule ameneyi komwe amati tisamulowe mu pant ndikumukoka kujeni kwacheko.kupusa mwana opa

 91. EMMIE KAMKWECHE & DANEL LUFAN koma makolo,ndiabale anu alipo koma???? akukondwa kuona mulamu or mpongozi wao chimimba pamtunda kuonetsa dziko??? mensa bambo a DAN LU ndim’busa kumangochi kotelo akupenya nyasi zotengelazi??

 92. Dziko lilironse lili ndi chikhalidwe chawo, akanachita ku Iceland kapena ku England even kuno ku RSA sikanakhala nkhani koma ku Malawi anthu amabisa mimba ya mzimayi awa sanachite zinthu zogwilizana ndi culture ya chi Malawi

  1. Point collection Mike juma,u mean in RSA they do that, England n iceland?In my life this is first time to see the musicians to do nonsense like this.even in South Africa I see women HV pregnant wear short but the pregnant is hide.

  2. Kuno mimba kukhala panja sizachelendo big, timakumana nawo mmiseu mu azimayi enaso ali ndi azimunawo michombo ili pa mtunda, point yeniyeni ndiyakuti kuonetsa mimba ya mkazi wako si culture ya chi Malawi

  3. Chifukwa chan magule a chikhalidwe chathu ovina samavala kubisa thupi lonse? Chimenechi ndiye chikhalidwe chathu mwamva kaya.. Colonisation idakupangitsani kutsata chikhalidwe… Chifukwa chake mukuziona zofoira..

 93. A person who respects/recognises their culture in spite of modernisation,is full of wisdom because they abhorr enstranging themselves.

 94. Pali chiyembekezo choti patsogolopa Malawi akhala ataonongeka kuposa lero chifukwa ambiri zikuonetsa kuti akondwera nalo khalidweli,,,,,koma tipemphe mulungu mwini chifundo atitsekule maso tikathe kusiyanitsa pakati pachoipa ndichabwino!!

 95. iyaa she deserves it …what kinda reaction was she expecting? ku malawi tu kuno no one wants to be scrolling down theyr newsfeed just to see pics of pregnant women….kwa azungu komweko zimenezo

 96. Koma hule ameneyu amaona ngati ife timafuna kuona phuli yonyasayo….kodi mbuzi za matchalitchi zimamatcha nkhani za mathanyula zija zili kuti..zimumatche mmbale wawoyu chifukwa adapanga ukwati wamutchalitchi mapeto ake akutionesa nyasi…

  1. Iwenso ndi mbuzi bwanji…mesa anthuwa adapanga ukwati wapa tchalitchi….atchalitchi omwewo amamatcha magay ndi ochosa mimba….nyasi inzinso azimatche…kapena amaonetsa phuliyi kuti ubunyulilepo swazi wamkulu ngati iwe…

 97. Sultan ukamati amalawi kusayenda ukutanthauza chani? ndipo Malawi And U S A Zikugwilizana bwanji ? osamataya chikhalidwe coz mwayenda, nkuthekanso zakumeneko ndimaloto chabe sunapitekonso , koma zomaanika mimba pa mtundazi ayi, nyasi zimenezo ife ayi, ngati iwe zikukkusangalatsa usawangile zochita Amalawi. anzako ayenda osati zamanyazi ukunena iwezo vomelezani Lulu ndi mkazi wake walakwitsa Basi!

 98. Wapangira malo olakwika iwe usazikhululukire asangokankha komwe angavomereze zimenezo. Poterepo anthu oipa atha kulowerarepo. Society ya Ku Malawi waiwona wekha yakana. Uyaluka nazo. Osangogoja. Ulibe sense achuluka ndi matama ndi umbuli . Pamenepo osalephera kukhala ndi nthumazi.

  1. akazi Achina diamond chikhalidwe chawo mchanu zofanana,ndipo diamond ndi mkazache anatuluka magazine2 sizabule iyayi,za ulelezi tikuzionela man fb mu

  2. Inu chimidzi heavy, nde mutani? kakolope nyanja otherwise anzanu zikuchita kunyaditsa. Enanu mumayenda maliseche mutavala ma min, kuonetsa akatundu anu nde what is wrong with kuonetsa mimba. nde muisovatu

 99. Abale palibe alakwitsa anthuwa. kungoti tiri mu new world tsopano. Nde tiyeni nafeso tikhale ndi maganizo atsopano

 100. Ndinkadz opanda ULEMU ameneyi ,ndipo ngat iyeyu sihule ndiye kut ndichisilu cha nkadz, ndipo sindikukukhupilila kut nkadz ameneyi ali ndimakolo ake ndakaika ,kapena chimamunacho chili Ndi Makolo akenso ,zingakhalale zonvesa chison kunva kut Makolo awo awanthu amenewa angasangalasidwenazo zimenezo.

  1. Alinafe Mkwate anthu enawa kuwatengera antha kukutaitsa nthawi pachabe… Bola ukapeza nthawi ya ku toilet utha kumawaganizirako…

  2. Komatu agalu amenewa ngati amafuna kuziziritsa nkhani ya chimanga cha ku admarc apoila. Mitu yao yadzaza ndi mamina. kodi kapena mamumayu wachita kudyera ngunda kut chitsiru chimzakechi chikhale ndi mimba. apumbwa achabechabe. zitsiru muntondo. sidzidziwa kuti sidzidziwa.ndakwiya aliiiii

  3. Nonsenu simukudziwa… Amayiwa awa akupanga competition ndimunthu wina ndiye kujambulitsa zolaulaku amafuna kuti munthuyo ati amve kuwawa osadziwa kuti angozichotsela ulemu ngatinso anali nawo… Munthu wa nzeru zake zopanda uhule sangalole zopepelazi… Mimba ikulilenji kumapanga za usilu pa facebook pano..

 101. Let them rot in hell but as malawians we are fed up of this photocopiers of bullshit trying to emulate satans from other planets.

 102. Amalawi kusayenda ife ku USA kuno tinatopa nazo izi.Taona zimimba ife ka Emmie ka nkachaninso ka.Taona mimba za Nicki Minaj,Beyonce,Kelly Rowland,Maddona ndi Jordan Sparks.Pali chani pa Emmie pa.

  1. koma samavurana mwanama ifeso ku americako takharako kwambiri kutopaso usanamize amalwi ngati zitsiru iwe ku america wakhalako liti? or nzungu amabisa izi usanamuze amalawi achina nickminaji wo amakhara avara chobisa mimbayo koma ikuoneka kuti ali ndi mimba osangovomereza kuti a dan lufan wo apanga zofoira bwanji ndi oimba anzake wo muno mu africa

  2. hahahaha kukhala ku America mwayesa choopsezera kapena kunyadila @ #Kalitera ? kkkkkkk koma zinazi abale kutamandila mimba za anthu otchuka zokuti nanunso mumazionera pa tv ngati ife tomwe ku malawi kuno!

  3. As a Malawian upeleke chitsanzo cha mkazi wako osatchula anthu ena, nkhaniyi ndi yokhunza chikhalidwe cha a Malawi not cha ma Americans. Ndipo usanamize anthu apa potchula anthu watchulawo bulutu.

  4. Nick minaj sanakhalepo ndi mimba,kelly Rowland nayenso alibe mwana ndiye iwe mimba zawo umazionera kuti? komanso anthu amenewa akabwera kono ku Africa kuzachita perfom amavala mwa chikhalidwe chathu.By the way Emmie kamkweche is a Slut.

  5. Ku Americako umakhala m’muzi mwake mwandani momwe ukumakumana ndi anthu ovuta kuwaona akungoyendayenda,evn ku show yawo ungakwanise kukalipira iwe?

  6. iwe ku joni uliko chinkhalidwe chinafe kalekale Ambiri kumeneko ndi ana anthu aja amagwira tchito mmigodi enaso ngati iweyo usiyako mimba kumabwera kuno kumudzi ndiye ukuona ngati kungakhale mtundu wolongosoka?

  7. Kodi Nick minaj ndi Jordan sparks adakhalapo ndi mimba? Abambo sultan shepherd kalitera mwangotchula anthuwa kamba kokuti mukuwaxiwa mayina awo eti? kkkkkk! ndikukaika ngatnso ku US A mukutchulako mudafikako

  8. Mmmmh kenako mutiuza kuti munaonaso mimba ya malemu 2pac tu abwana. Bodza kumachitako nalo manyazi mukuoneka kut ndinu munthu wachikulire mukanasiirako ana ndizidzukulu lusoli inu mkupanga retire

 103. klkkkkk walusa Chynna, penapake amalawi mumawaputa dala, mumakhala mukuziwa bwinobwino kuti if i do this, this is how people are going to react, nde mukatha muzisowa nazo ntendele nokhanso…. asatikwane

  1. hahaha eti eti? no ones is poking their nose into anyones bussines….iwowo why did they post it in the first place? akuona ngt ku america kuno …the reaction is totally reasonable…aliyense azipanga upload ma picture when theyr pregnant? ndye siikhalanso facebook tu ikhala martenitybook

  2. kk eti, rob and chynna wannabe’s, amayesa ngati amalawi asangalala kuti emmie wapanga za nyuwani, makape they thought that if they do that aoneka ku zindikila.

 104. Ma celebrity aku malawi, ali mbuuu…!! None of my business zowanyoza and zomwe wayankhazo its none of my concern

 105. if emmie was married to our own celebrity TYGRIN EEE!anakativuta ngat akuchita kutinyasa ndi poor man dan lu, ovala za mbelo. Chisomo was right we have many celebrities who have money osat izi zosatha english. Any way if you posted mimba yako on that you wanted people to see and comment positively but it wasnt as planned rather people were hitting with bad comments because emmie ndie wavulidwa mu chiwembemu wango flash zibwenzi zake za zii, dan let me tell u that mkazi wako ndiophweka sakana komaso ndiosaoneka bwino alibe formular nchifukwa uja unagwera uja amakudyera ma dolo umazimva koma ulibe kanthu, celebrity amayendera toyota allex? ma skin

Comments are closed.