Chakwera is not done with DPP yet, says Malawians have lost hope in the party

Advertisement
Lazarus Chakwera

Opposition leader in Malawi Lazarus Chakwera has claimed that Malawians have lost hope in the Democratic Progressive Party (DPP) led government following corruption scandals in the year 2016.

In his New Year message, Chakwera lamented corruption cases that have marred government departments in the country.

He cited the Malawi Energy Regulatory Authority (MERA) maize deal and reports of fraud at Malawi Electoral Commission (MEC) to be among the frustrating issues that have fuelled suffering.

Peter Mutharika and Lazarus Chakwera
Mutharika (L) has failed Malawi says Chakwera (R). (File)

“I have seen many of you losing hope because 2016 has been a year of corruption scandals, I understand your frustration as Malawians,” said Chakwera.

However government spokesperson Nicholas Dausi has faulted Chakwera arguing that he should give evidence on corruption reports in the country.

Recently, the DPP led government dressed down Chakwera following a national address speech the leader of opposition made.

Top government officials and party leaders accused Chakwera for what they said was misleading citizens on the state of affairs as he described President Peter Mutharika as a “failure.”

Advertisement

107 Comments

  1. Hehehe hahahaha ZILI PA MALAWI 24 kumangotukwana chakwela mmmmmmhuu mpilah ndi pa ground 90 minutes, TIONANSO 2019 KT WOTENGA BOMMA NDANI???

  2. Achakwela ur time is not yeat and simuzalamula kamba koti MCP is a party of full of blood mukanakhala kuchipani China mukanatolako kampando vuto lina kupoto,pakati ,simuzatenga Boma apeter avaye kunyumba ya abrother awo b4 go u should beaut stadium

  3. Kodi m’busa opanda mapantiyo angoyankhula koma osabweletsa maganizo othandidza bwanji?Akulira failure ndi chakwerayo chifukwatu paja analudza momvetsa chisoni.Munthu wadyera ngati chakwera sindinamuone.kusiya kutumikira Mulungu kuthamangila cashgate.Shame on chakwera he is a failure indeed…

  4. Mawu Anga Kwanyan Nose A Ddp Ngat Chakwera Alibe Polobulemu Ali Ndi Vuto Ndimunthu Opanda Mano Nkamwa Uja Ndye 2019 Tichotsa Mgogo Ameneyu Akafere Patali Ndmatenda Akewo Vindele Imwe

  5. we malawians are we happy kuvesera nkhani za ndalezo zopusazo inesazanditumiraso zankhanizanuzandalezo,angoti mitu mbwaa!!!!,pankhani anthu akufandinjara kuno nde akuyembekezera mmalawi wake yuti azavote chakwela asaa!!abwele kwathukuno azizapanga maganyu ophika mang’ina ankhuku,komaso sangawine bcz mulungu ananpasa mphasoya ubusa osati yolimbana ndi anthu zachipani ndizamulungu ndizosiyana,amadyabooo ali n’busa komalelo azadya nchenga akapusa,abwerere ku utumiki wa mulungu asamachite masewera ndimulunguyo,kuluzakuja ndi mulungu bcz iye afanana ndi yonah yemwa anatha utumiki wa chauta eesh!!!!!!!!,asandiyankhulise pambali timuona koma plz zitheza nkhaniza ndale muzilembako zina etiiiiiiiii

  6. Mbuzi zidzavoteranso mbuzi inzao, bola nkhosa ikupatsidwa ulemu.
    Zikuonekeratu kutidi utsogoleri wobera mavuto ache ndomwewo.
    Zinthu zibasokonekera Ku chipani cha DPP, popatsirana utsogoleri ndi nkulu wache popanda elective conference.
    Mu DPP muli anthu anzeru oyendetsera, dzxikoli, koma zinagwera wopanda mano.
    Mmalawi wanzeru zache zobadwa nazo angazasankhetso APM mu 2019, ndiye Ali ndi mwano.
    Wanzeru sangayang’anenso kwa Farao.

  7. Ndimaiko ochepa amene alibe mavuto azandale vuto: Tikulamulidwa ndi Maulamuliro ochokera kwa Satana. Believe me palibe boma limene lizayambe mpaka kumaliza opanda milandu. Malawi ndi wathu koma ndi dziko lomvetsa chisoni. Limakhala ngati munalowa nkhondo. Ndi dziko laling ‘ono anthu ndi achitukuko vuto ndi atsogoleri.

  8. Iwe chakwera,ngati ngati anthu ayamba kutuluka mumpingo wako bcoz of ur stupidity.Ungakhale president?azakuvotera amako.

  9. Man #kulima? Nkhaniyi sakuuza inu nokha ok olo ukanati usawelenge postyi panalibe chovuta ife akutiuza zomwe wanena#Chakwela don’t u fuck man mutu opowanyizikawo ngati maofozi

    1. Ku central region kwanuko mwinadi he z ur only hope but don’t forget here it z the majority who rule dis country . Ndye tizawona . Dilu ndfe akumwera

  10. pajatu ndimakonda kunena kvti chakwera ndi chitsiru! sayamikira munthu kwake mkunyoza! tiona 2019 ngati uwine ndi central region yakoyo! chitsiru iweyo! mbusa otembeleledwa iwe,galu wa munthu! ine sisangalala ndi speech yako.udadya ndalama za mpingo,pano ukulota utadya ndalama za boma,ulapaaa!.pomaliza,aliyese aike koment,no reply me!!

  11. Iweyo bndi anthu akwanu mbali yakwanuyo oro iweyo utalowa Boma sikuti ungazasinthe zinthu .Waboza iwe usatinamizepo apa unalekeranji kuwina 2014 ukafuna zimenezo dikila 2024 ukaganiza za 2019 uwuponda ndithu uzingotokotabe basi .Achigawo chakwanucho nkumakuhirira macoments

  12. Enanu Mukutukana,but We Cnt Talk Abt The Troubles We Are Meeting In This Country Without Mentioning Dpp Cz It Is A Ruling Party Nw,wake Up! Malawi Must Change And Dnt Close Our Mouth While Nosense Are Happening W In This Government, We Are Government And Government Is People.

  13. iwe wa malawi 24 usamatinyase ndi chakwera wakoyo kd palibe nkhani zina zampindu zoti ukhoza kupanga post,dairy tikhalire za ndale kdi wakupasa ndalama zingati m’busa wadyera ngat ameneyo sindinamuonepo mawu a mulungu amati tsogoleri aliyese amakhala osakhidwa kuchokera kumwamba so iwowo akukhala ngat akususana ndi mulungu bwa?a chakwera asamale2 mkwiyo wa mulungu ukhoza kutsika pa moyo wawo even ku banja lawo!!adikile nthawi ya kapheni ikwane osat azingoyakhula zopusa apa!!!

    1. Oyamba kulangidwa atha kukhala mapwiya.do u tink Peter was chosen by God? Never.God can not choose a thief to rule us.das y sizikuenda…wakwiya Naye Yehova.

    2. I think goodwin supita ku church en even bible suwerenga amwene ndikuuzeni tsogoleri aliyese osati president yekha kma aliyesa otchulidwa kt tsogoleri amakhala osakhidwa from the above!!!

    1. Atleast Its Beta To Have Sm1 Who Knw How To Lead The Cogregation Cz He Knw The Needs Of The People,than To Have The Proffesor Who Lead Us Unproffesionaly,he Acts Like A Standard 4 Student Who Is Told To Go And Try Standard 5

    1. kkkkkk bwanji #Mastermind zina timafanana??andale sazasinthapo zinthu panzikoli coz dziko liti ndale ikuyenda bwino??ndimakhulupilila bible lomwe limanena zaufumu wa Mulungu kuti ndiumene uzathese mavuto basi,osati mwana wamunthu wochokela kufumbi.

  14. Amalawi mukauze kachakwerako kasamatnyase amalawife stifuna zopusa MCP iwere zolowa boma ife tambara tinamudya zaziiiii!

    1. Stamford who are you to call me frustrated? Clueless beings like you who trust politicians very much end up commit suicide after they let you down my advice to you is fix your eyes upon CHRIST He shall never let you down!

    2. Mwayamba Ubusa kulalika pano chifukwa chochita manyazi Mbuzi zanu zalephera kuyendesa Boma! kkkkkkk Mudakali kulalika ndi kumziwa Yesu! Frustrated you are indeed!

    3. A china dpp Kadetisi atamva kuti wawo ndi polofesa Americano, ali koma apa ndiye! Akanaziwa kuti ndi mphwepwa wotheratu sakanamukweza chonchija, lero izi manyazi madengu madengu kuti phwiiii….Munthu kulephera u minisitara nde u pulezidenti? Bwerani zili kuno ku Malawi muzazione kkkkkkkk!

  15. palibe president anayamikiradwapo mu dziko lathu lino.
    kamudzu wokupha
    bakili >>ati amapopa magazi
    ddp-bingu’s time>>chipani cha anthu azikwanje
    pp-cashgaters
    peter-corruption
    or tabwera prophet sazakondedwabe because aliyense ali ndi zofooka zake.
    *
    zonsezi ndi chizindikizo choti ndi Yesu yemwe azabweretse boma lenileni lopanda mavuto.
    or mutasankha ma president 100 pakamodzi,sizingathandize kathu.
    .
    look ati america,nigeria,mayiko a ndalama koma mavuto ndi osayamba
    MAY GOD HELP US

    1. Of course zeru uli nazo koma apapa nde sizikuchita fit.
      You don’t know what you are talking brother.
      Chakwera deliberately pays a cold attention to problems Malawi faces.

      To gain political marks, you will hear him making that noise.
      Then peter on the other side seem to be quite while some dogs are barking

    1. anthu ena ,ngati kuti anabadwa kwa agalu.Kuganiza ngati a galu ndithu.Ngati pali kape wa kape nde ndi Pitala,akusunga mbava poti iye ndi mbava kumene.

Comments are closed.