Gaba, Nthara re-called

Advertisement
Gabadinho-Mhango

…Ng’ambi included

Malawi national football team  head coach Ernest Mtawali has released a final 20 man squad for 2018 FIFA World Cup preliminary first-leg qualifier against Tanzania on Wednesday next week at Benjamin Mukapa National Stadium.

The mentor has dropped four players who were part of the squad that travelled to Swaziland for the 2017 African Cup of Nations qualifier which ended 2-2.

Gabadinho-Mhango
Gabadinho-Mhango recalled.

Richard Chipuwa, Wonder Jeremani, Yamikani Chester and Chikoti Chirwa have been dropped, with Fisd Wizards captain Levison Maganizo and Big Bullets duo of Miracle Gabeya and Dalitso Sailesi being given their first national team call ups.

Surprisingly, Mtawali has re-called Simplex Nthara and Gabadinho Mhango who have been in-active for the past years.

Robert Ng’ambi is also included in the squad despite his public outburst when he was left to warm the bench in Swaziland.

Senior players who were dropped prior to the Swaziland game have not been re-called back.

Flames Full Squad list:

Goalkeepers:

Simplex Nthara -Brighton Munthali

Defenders -Limbikani Mzava -Stainley Sanudi -John Lanjesi -Miracle Gabeya -Pilirani Zonda -Yamikani Fodya

Midfielders -Levison Maganizo -Chimango Kayira -Robert Ng’ambi -Isaac Kaliyati -John Banda -Micium Mhone -Gerald Phiri Jnr -Dalitso Sailesi

Strikers -Manase Chiyesa -Gabadinho Mhango -Chawanangwa Kaonga -Robin Ngalande

Technical Panel Head Coach: Enerst Mtawali

Assistant Coach: Nsanzurwimo Ramadhan Team Doctor: Levison Mwale

Team Manager: Clement Kafwafwa

Goalkeeper’s Trainer: Swadick Sanudi

Head of Delegation: Paul Mzungu.

The team leaves the country for Tanzania on Sunday morning at exactly 7:30 am and will arrive in Dar es Salaam at exactly 10:30 am.

The Flames will return back into the country on 8 October to prepare for the return leg on 11 October at Kamuzu Stadium

Advertisement

398 Comments

 1. Am giving u last chance ndisanakuthile phuzo iwe enest.

 2. I wonder the argument that Mtawali gives. Looking at club level,Wanderers nditeam yoti sinachinyitse zigoli zambiri zambiri,,tinene kut coordination imakhala kuclub level kokha? Wat abt Brighton Munthali? Team yake ili pati? Abt Gaba,,ena munkawasiya sayin that they dnt hv game tym,,wat abt Gaba,,from injury straight to national team,,judging him becoz fellow coach has said akusewela bwino training–Mtawali ure not serious. And ure not a good coach.

 3. Mulungu inde amapereka kwa omwe apempha. Amtawali tawona tonse chomwe apempha apa kuchita kukokolola ndi wophulika amene. Kkkkkk! Koma yaaa

 4. i dont knw wat is happening to our coaches, kodi nthalayo cordination yake ndi madifenda ilibwino tikuwonerani momwe zithere and mukakawona kuti nthala sanagwilire bho muzasithenso malawi coaches eish

 5. A malawi kodi munatani tamusiyani Coach agwire Ntchito yake zokamba bweeee penanso mumasokoneza zithu ndi pakamwa panupo kodi ndani samakonda Ntchito yake? Tamusiyani musamusokoneze Coach mind your Bizness

 6. Tilibe timu yokhazikika ndi yodalilika apa auzeni makochi azisankha ma player amene akuchita bwino, aluso komanso a experience onsewo asewre limodzi tikatero tizakhala ndi timu yamphamvu. Osati lero tiona nkhope zina mawa nkhope zina ayi sizitithandiza!

 7. Zaoneka Kale Apa Kuti A Coach Awa Satithandiza ayi Bolaso Ena Aja Tere Ikabwerako Chabe Itazidzola Zigoli Kumeneko.Angochita Step Down Ngati Matengedwe Ama Players Ake Akhale Amenewa.

 8. Team sitisintha ikamachita bwino koma ngati sikuchita bwino ndiye kuti coach ayenela kusintha kufikila team yathu kumawina. Mtawali ndi coach yekhayo ndamuona wolimba mtima akuyesa kufufuza ma player pamene ena amaopa kutenga risk yoyesa ma player atsopano .dziko ndi lalikulu gwilani ntchito a coach,

 9. The Ploblem Of Malawi Its Igiote And We Are Not Loving Each Other As Acountry, Enest Iz Anew Coach Dats y Iz Changing Players Every Game Let Us Give Him Atym And Encolagement Zamaplayer Enawo Amene Mukunewo Ngat Atusai, Kamwendo Even Bajo Amenya Zaka Zingat Kuflames What Iz Their Impact Amalimbikila Kujon Chifukwa Ndalama Ndizambili Shaa Find Me Inbox Ndikuuzen Tiyen Tiwalimbikitse Strike 50 Games 4goals Amuitane 4what?

 10. Very nice anawa akamenya mpira pa ground osati za pakamwa zanuzi apa.squad yabwino and very nyc combination ya ma player.my prediction iz TZ 0 mw 2…go flame go go go

 11. coach asinthe ee wasinthilanji eee,asasinthe eee ma club alindi maplayer abwino koma coach sakuwagwilitsa ntchito!koma nyama amaiti m’malawi sidzathekaso pliz!

 12. Ife ndiye tinasiya kusapota Mpira chifukwa National Team imangoluza. Tikuganiza M’malawi muno tisakhale ndi National team but makalabu chifukwa boma limaononga ndalama zambiri zoti akanatha kugula mwina Mankhwala.

 13. Ndiye kuti coach akangomva dzina la player adzisintha?goalkeeper wa surestream atha kukhala yemwe wachinyidwa kwambiri.bwanji sanatenge nthala ndi chipuwa.komanso gaba wangochoka ku injury kumene why cald him? Kodi ndi campain kapena chani?ndiye kuti kuti player akapanda kumenya bwino game imodzi ndiye kuti wagulitsa malo?this z nt buildn team bt dstroyn.nanga ng’ambi mwamutenga coz anakuuzani kuti h z nt a bench warmer? Selection ikuvutatu apa

 14. Ngati Ng’ambi muzamusiyenso panja,ndiye Mr coach muzangotuliratu ukochiwo mwantendere kusiyana kt muzamve ululu wathu chifukwa ulemu nkupasana.Ilov Flames mo dan u Mr Coach.

 15. Vuto si coach koma ma players amene tilinawo ifeyo,amat mwezi wuno asewere bwino mwenzi winawo phala lokhalokha ndiye mukuganiza kut coach angamatenge zimenezo.Ma player anthu ayenera kukhala consistency kuma club awo kut tikhale ndi national team yodalirika finish.

 16. Apa nde taluziratu,,,,,,,, akutengera maina coachyu eti? Thats y ndimakwera mbali inayop kusiya malawi,imandichitisa manyuazi kuyambira osankha timu

 17. Zalowa masanje,lero squard iyi,mawa squard iyo,mnkuja squard ina kkkkkk ziliko ku Mw nkumati national tm siikuchita bwino chitsebwe!

 18. Selection yabwino kungot walakwitsako kusiya Chipuwa. Coach koma ameneyu chifukwa ndi ambiri ma players amene amafuna atasewelako national team ndie zli bwino akumasithasitha aaaaa mpaka kumachita kuloweza squad yonse? Enafeso tidzamenyakoso flames akuchitiramu!!!

 19. Squad ilibwino koma kusinthasintha kumeneku sikutithandiza..Ndimaona ngat a Ntawali abwera ndinzeru zatsopano koma ndikuona ngat atengera makhalidwe aazimbuyawo amakocha m’mbuyomu,kusakhala ndi team yokhazikika.

 20. The inclusion of gaba is coming as a suprise hw can a player receive a national team call-up while he is not playing club football?,mr mtawali can u clarify the inclusion of this guy.

 21. The inclusion of gaba is coming as a suprise hw can a player receive a national team call-up while he is not playing club football?,mr mtawali can u clarify the inclusion of this guy.

 22. MISTAKE ILI PA GOLO,TAONA MMENE AKUCHITIRA MA KEEPER MU SUPER LIGI YATHUYI,BWANJI OSAPEREKA MWAYI KWA MA KIPA ENA? SIMPLEX NDI MBIRI TONSE TIKUDZIWA,Y HIM?KULI MA KEEPER KU SILVER,BULLETS,NOMA,MOYALE,BLUE EAGLES,Y NTHALA? MALAWI PLIZ,WE WANT CHANGE TO BETTER NOT TO WORSE.

 23. I thnk Ntawali z back 2 his senses dis tym & we cn av hop 4 a Win coz 2 say the fact h has selected good players wth experience & if h fields em well i c nothin stoppin us frm carryn the day next week.

 24. I thnk Ntawali z back 2 his senses dis tym & we cn av hop 4 a Win coz 2 say the fact h has selected good players wth experience & if h fields em well i c nothin stoppin us frm carryn the day next week.

 25. Kodi Gaba mpira amasewelera kuti? mpaka call up lu National team. Mtawali zploweza ku National Team ayi please

 26. You want us to ansa?wel if thts wat u want usatitole mkamwa mesa kochi ndiye akuziwa bwino who best?iweyo umaganiza bwanji?kwa ine, sanalakwise thts his best choice so let him be.

 27. squard iyi tailandira koma game ya flames ipangitsa kuti daby isakome coz players always sanasewera modzipereka poopa kuvulala.

 28. malawi why? ulendo ulionse kusitha team anyamata experience akaitengera kuti ma game awili kuwathamangisa,tinali McDonald harawa anangwira bwino ma game or ma penalty ,anangonyika one game kuthamangitsa mwatenga chipuwa wanyika mwathamangitsa,malo ofunika osamasitha nde goalkeeper ,simunaone cassilas atachinya zigoli zopusa ku world cup coach anati sanalibwino not saziwa kungwira,eish mungakhoze team game imodzi any way

 29. this is the last chance if it fails again let this team face government reform and replace it with jce which haz been disolved

 30. I dont knw ngat tiphulako kanthu,taifa stars ndi team yamphamvu nde squadyi yokaikisa bt wishng all the best flames hoyeeeeeeeeeeeeeeeeeeee!

 31. Koma ineyo ndikanakonda kuti Malawi ikhale ndi ‘squad’ yokhazikika. Monga achitira ma ‘club’. Koma Kantolatola akumachitikai tsiku lina adzatichitsa manyazi. ‘ Team’ ya dziko isakhale ngati ‘social’ ya pa msika. Don’t just do things for the sake of today only. Sindipepesa chifukwa nanenso ndi mMalawi. All de best my mother FLAMES woeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeeee

 32. Nde mwati Flames imeneyi ili pa number chani mu super league?

 33. asaaaaaaaaa inu mukuti akanatenga sulumba kusiya Gaba,what do u mean? Gaba mungafanizile ndi Sulumba?? take it or leave Sulumba z not a gud striker mwina kunyerere kwanu komweko

 34. Very impresssive striking force. Ana awa amathamangadi kusogolo, especially Chawanangwa uyu, I tell u ngat anawa sakachinya zgoli 5 muzandifunse or else ma penalty tikawapeza osaneneka. Coach, striking force mwandifikapo.

  1. amene mukuti anali injury mwanama ine ndi neba wanga alibe game time even training ,ndipo akuma user celtic yaing’ono Gaba ananenepa alimafuta pamtima kuthamanga kukumvuta akumatopa changu

  2. Nkhani ndiyakuti Gaba anali pa injury nsipo coach sadakhoze kumuitana chifukwa chake ndichoti sanachiritsitse,no matter how impressive he played for reserves but still its too early for national duty,mainly as his senior team is not playing him.Tiziona.

 35. Selection iliyonse ya Flames itha kuwina or kuluza. Nde hmm whatever, ife ndi a Malawi, we wil support the boys and Mtawali

 36. Ernest mtawali palibe chimene wachitapo apa kunena zoona olo akanatenga hard n tough squad palibe chimene chingasinthe coz its imposible malawi kut ipite ku world cup tisazivute a malawi yathu ndi super leugea yomwey bas i hope kut boma likusowa chochita nd ndalama koma zot mzipatalamu mulibe mankhwala likudziwa? ngat likudziwa chomalimbanirana ndi world cup mchan end yet tikudziwa kut afcon imatikanika so ngat afcon imatikanika do u think kut world cup ingatheke so amalawi amzanga do u have hope dat we wi’ll carry de day? Aah amalawi sitizathekaso ndaona chomcho

  1. Chipuwa can not perfom better than Thala – am tellng u bliv m not…..let hm sty. thats the bst squad fo the future of the team.

  1. vuto ndi phala la ma player yomwe tili nayo amat mwenzi uno asewere bwino bwenzi winawo phalalokhalokha ndiye coach amafuna ma players amane ali mu form thats wy amasithasitha.

  1. Sukunama, kumalawi kulibe timu yamphavu dats y timu yobwera 2 koloko izingotichinya,watengera history coachyu,anthu omwe ankasewera kale

 37. Attach a Photo · Mention Friends Levis Chigwembex Cashmere Go Keeper Samamandidalitsa End Wea Is Maunde? Like · Reply · Report · 2 minutes ago Tommy Hypa Elias Go Keepers I Dont Trust Them,,,,,difencing&midfilder Ilibwino Strikers Ndiye Timavuto Pang’ono Koma Tingokhulupilila Kuwina Nkotheka Like · Reply · Report · 6 minutes ago Francis Kanduwa Just hit like for Aheadmaster Yamikani Fodya Like · 5 · Reply · Report · 11 minutes ago Benja Newton Chikayenda tizayakhula akabwerako Like · 1 · Reply · Report · 10 minutes ago Ish Jame Phiri Best squad eva Like · Reply · Report · 3 minutes ago Tonny Kalupsa Chimangoyo Mmmm Ayi & Where Is J Chande Plz Like · Reply · Report · 6 minutes ago Emmanuel Tembo Gaba not fit Like · Reply · Report · 8 minutes ago William Dalo Jnr Diniwa i think this gonna help us mwamwina Like · Reply · Report · 9 minutes ago Wanangwa K Gondwe strikers zero (week) Like · Reply · Report · 10 minutes ago View next comments…

 38. Go Keepers I Dont Trust Them,,,,,difencing&midfilder Ilibwino Strikers Ndiye Timavuto Pang’ono Koma Tingokhulupilila Kuwina Nkotheka

 39. Gaba wakhala nthawi asakusewera mpira,Ngarande sali mwakare,akanayesapo achina Green,Bokosi,Chande,Kuwari kuti enawo azitolere kaye;so poti ndizaziko tiwafunira zabwino zonse.Ndimakhumudwa ikaluza Bullets yokha basi

 40. Zomwe wasankha coarch zimenezo.Koma uthenga wanga ndi woti: Akakangoluza,kochiyo komanso mapuleya onse akawone kofikira,osati ku Malaw kuno.IZIZI SIZOCHEZA!!!

 41. Koma pa Goal keeper sanalakwitse,,, zija tinapita nazo ku Swaziland zinali nyangwita ,, koma Nthala chonde osakamenyaso ref eti !!

 42. coach ameneyu akupanga phada watenga defense yonse ya bb ndiye nkumat sawapanga realese how?guys malamulo amat ngat team yapanga realese maplayer four sikuyenera game y bullets amene

 43. Ena ali busy kuwerengera mapoints pmene azawo akutenga zikho kenako adzthera zomwezo mpkna December kikikikikiki! Kupusa kwenikweni azanu akudya nyama inu mkumasungira mafupa ndye mkumati nyama ndkudyabe kikikikikikikiki!

 44. Bwanji anthu mumasokoneza,,,,Nkhani yili apa si ya Club,,,,,,Tikunena za National team osati Bullets,,,shame on you,,,,Go,,,,Flemes Never look back

 45. Kma zoona #Yamikan fodya amene amathandiziranso alendo kutichinya mpkna amtawali mwamutenganso kikikikikiki! Akatichinyanso ndthu kikikikikiki!

 46. LEVISON MAGANIZO NDI PLAYER OR TEAM DOCTOR? JUST NOTED WALEMBEDWA PAWIRI.

 47. My first choice 4:4:2 …..GK..Simplex ,DF… Fodya , Mzava , Lanjes , Zonda …….MF..Micium , Ngambi , Chimango , Banda …. FW….Robin , Mhango.

 48. First and for most allow me to thank God and F.A.M that from this selection there is no “Lucky Malata” from this squad, tikanakalilaso nthawi yothayitha pa 90 minutes, this has the body of a defender but he lacks defending wisdom and skills he made me to cry when Malawi host Zimbabwe in a previous home game he made a rare blander which coast us 3 points…,mmmmh

 49. Nde mwati onsewa a bullets mwatengawa simuwapanga release mu camp pa durby ya surtaday? Nde akamenye ndindani mu bulletsimo?mwaganiza bwanji pamenepa a mtawali heee! Kapena mwapangira dala kutenga ochuluka a bullets kuti mukawasiye pa bench cholinga bullets iluze mu superleaqeu and kutenga ochepa a wanderous dala cholinga onse akakhale mom’mo .kodi zikukuwawani kuti bullets siidaluzepo eti.release them for superleaque

 50. 4-0 infavor of TZ coz mwatenga manyaka a Bibi bullets mpkna nkhalamba #Gaba zoona? Kma coach ameneyu amaganiza bwnobwno kma?

 51. Noma siyitha,ena anachalira kuti apita ku Tanzania,ng’ooooooo,coach wawabweza cause ndi mphwephwa.Bullets woyeeeeee!

 52. thats it,kaya..! Davie Kennedy Allan Kunkhanda Daud Chimaliro Winford S Picken Moses Mondokwa Steve Nthala Grey Linde Banda Kizito Cliford Phelatu Mathias Makinah Khumbo Nani Ngwira

 53. Can i get likes please for Head master Yamikani Fodya,Pilirani Maicon Zonda,Dalitso Di”Maria Sailesi,Robert Baggio Ng’ambi & king Frank Gabadinho Mhango ,Osaiwala Brackberry Chimango Kaila”TEAM BIG BULLETS kukagwira ntchito za Boma tsopano! !!!!”!”

  1. Kodi inu mukulimbikila za ayaya kodi FAM yakhala ikukulipilisa ma 450 000 kangati chifukwa chokavalira ku ntchire malo mokavalira ku dresroom coz u was using khin makape? Koma ife a noma sitimalimba ndi khani zopusa, ife ndi adola osati a maskin ngati a mahule

  2. Ayaya fc udolo wake ulipati? bwanji mukulepera kulipira achina kaliyati ku Tigers bwinotu bwino “ndife masikini ozindikira ndinu masikini pachikopa kkkkkkkkk

  3. ayaya fc idayaluka kale kale,,,,,,,ikadakhala trouser ikadakhala flair kkkkkkkkk!!!!!!!!!!!!oxamalimbana nd #TEAM_MAULE_AKA_Big_Giants_Bulets

  4. When u ask kuti ” udolo wanu uli pati? ” wat do u mean coz tinakumenya 2 kwa 1 mu final ya carsberg ndikutenga 9 mil pompo pompo maso muli gweee udolo upose pamemepo? Iwe chonsecho ukuti ndi oziwa mpira ndie kuziwa kwake kuli pati? Kkkkkk neba waduka mutu matama basi

  5. #chkutumbwe ukulimbana ndi ana ovuta pokamkha chkopa bb,,unayaluka neba coz u dnt fnsh yo balnce kwa agogo ako ayaya,,leav bb alone dats y mukungoluza coz mumangoziwa kunyoza osat ku player mxiiii

  6. Avoteredwaso chaka chamawa amenewo Noma sitha mpira koma pakamwa,,,,kodi mukamati muli ndichikho ndekuti chani?zimenezo muziuza omwe sadatengepo chikho koma kwa ife sizachilendo.

  1. what a vile submission???mr??? u’ll be take by supprise….because its a vice verser what u have predicted…malawi will win no matter what in jesus christ name!!!…

  1. Panali ma kape anzako amene amanyadila kuti ku Noma atumiza ma player ku national team ambiri than ku BB, nde sefa yasiyanisa yokha ma player okutha mpira pagulu la osatha. USOVA!!!!!!!

Comments are closed.